Cas Bwoy3119 Koma Mukanabwera Official Video Pro By Admin-Foxxy

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ก.พ. 2025

ความคิดเห็น • 32

  • @JaphethJumbe
    @JaphethJumbe 6 หลายเดือนก่อน +2

    Japheth lilongwe area 25
    1. Eya. Nyimboyi ndi kulira kwa zimayi yemwe Sakulandila attention kwa mamuna wake. Ikuyamba ndi kudandaula and ikutha ndi pempho.
    2. Afro dancehall
    3. Akufuna attention kuchokera kwa amuna ake.
    4. Amunawo akulakwitsa coz ngati akaziwo analakwitsa anakangowauza ndikukambirana.
    5. Mafunso 5.

  • @PatrickKaitano-f8z
    @PatrickKaitano-f8z 6 หลายเดือนก่อน +1

    🎉🎉🎉ur flowers ma men❤nice tune💙💪

  • @CasBwoy3119
    @CasBwoy3119 6 หลายเดือนก่อน +1

    Live and direct you deserve your flowers my gee stuff on fire

  • @preciouskaunda7162
    @preciouskaunda7162 6 หลายเดือนก่อน +1

    Nice Track King Cas. 🎉

  • @TrinketTeeChannel
    @TrinketTeeChannel 6 หลายเดือนก่อน +1

    Arasi tsopano❤️❤️❤️

  • @truminemw
    @truminemw 6 หลายเดือนก่อน

    Tune🔥🔥

  • @SlyZaza
    @SlyZaza 6 หลายเดือนก่อน +1

    Mesa 🔥❤️

  • @Thelastkings-s2c
    @Thelastkings-s2c 5 หลายเดือนก่อน

    More fireee monga Rasta

  • @TCEEMEDAH
    @TCEEMEDAH 6 หลายเดือนก่อน

    My katswili❤❤❤❤

  • @IshavinBilliat
    @IshavinBilliat 5 หลายเดือนก่อน

    Nice track kig cas🎉🔥🔥🔥🔥

  • @LayLeefrancisco
    @LayLeefrancisco 6 หลายเดือนก่อน

    Mn mulibho mukutiphunzisa ,kutisangalasa and kutilimbikisa

  • @PaulManondoh
    @PaulManondoh 6 หลายเดือนก่อน

    Mmakwana inuy mesa bro,🔥🔥🔥🔥💪

  • @FlossieMaguwa
    @FlossieMaguwa 5 หลายเดือนก่อน

    My favourite 🔥

  • @ceciliachikondinjoka2604
    @ceciliachikondinjoka2604 6 หลายเดือนก่อน

    Great Malawi beat

  • @RazantDIHBaderer
    @RazantDIHBaderer 6 หลายเดือนก่อน +1

    🔥🔥nice tune

  • @AhmigoOg
    @AhmigoOg 6 หลายเดือนก่อน +1

    Mwadza1

  • @LucySichali
    @LucySichali 6 หลายเดือนก่อน +1

    Nice

  • @Shack-D1
    @Shack-D1 6 หลายเดือนก่อน

    Dolo katatu owe
    1. Production
    2. Vocals
    3. Umatha kucheza

  • @bikmw
    @bikmw 6 หลายเดือนก่อน

    🔥🔥🔥

  • @Lemuel-t5p
    @Lemuel-t5p 6 หลายเดือนก่อน +1

    4Ine ndi kingpin Kaundah, kuno ku 25 , sector 5
    1 Ili ndi chiyambi chomwe amayiwa akuwauza ana kut bambo awo anasintha khaldwe lawo lokonda banja lawo. Mathero aliponso pomwe amay akupempha amuna awo kt asinthe, abwelele mwakale
    2 nyimbo yaimbidwa mu chamba cha afro dancehall
    3 bambo anali lakhomopo km iyeyo samapereka chinthandizo momwe achitila bambo wapakhomo, nchifukwa chake amay amanena zokt abwelele.
    4 ndi mmene nkhani yakambidwila zaoneka ngt bambo wo ndi olakwa ndipo akuyenela kpanga zokt azipereka attention ndi chisamalilo.
    5 pali mafunso 7

  • @CasBwoy3119
    @CasBwoy3119 6 หลายเดือนก่อน +2

    GAWO LAMAFUSO PA KOMA MUKANABWERA
    01: Kodi munkaganizidwe kanu nyimboyi iri ndi chiyambi ndi mathero ? Fotokozerani yanko lanulo
    02 Kod nyimboyi yaimbidwa muchamba chanji?
    03 Ndichifukwa chani amayiwa amafuna amunawo abwerere kunyumba chonsecho amunawo anali ali kunyumbako ndikale?
    04 Kodi mutakhala oweluza nkhaniyi mungaweluze motani?
    GAWO LOMALIZA CHENJERANI NDI FUNSO LOMALIZALI CHIFUKWA NDILONGOFUNA KUPIMA MAGANIZIDWW ANU🤣
    05 Kodi mukaonetsetsa mwafusidwa mafuso angati?

    • @JaphethJumbe
      @JaphethJumbe 6 หลายเดือนก่อน +1

      Japheth lilongwe area 25
      1. Eya. Nyimboyi ndi kulira kwa zimayi yemwe Sakulandila attention kwa mamuna wake. Ikuyamba ndi kudandaula and ikutha ndi pempho.
      2. Afro dancehall
      3. Akufuna attention kuchokera kwa amuna ake.
      4. Amunawo akulakwitsa coz ngati akaziwo analakwitsa anakangowauza ndikukambirana.
      5. Mafunso 5.

    • @CasBwoy3119
      @CasBwoy3119 6 หลายเดือนก่อน

      Thanks for participating mudzdkira announcement apapa tione Kaye kut Ena ayankha motan

    • @Lemuel-t5p
      @Lemuel-t5p 6 หลายเดือนก่อน

      Ine ndi kingpin Kaundah, kuno ku 25 , sector 5
      1 Ili ndi chiyambi chomwe amayiwa akuwauza ana kut bambo awo anasintha khaldwe lawo lokonda banja lawo. Mathero aliponso pomwe amay akupempha amuna awo kt asinthe, abwelele mwakale
      2 nyimbo yaimbidwa mu chamba cha afro dancehall
      3 bambo anali lakhomopo km iyeyo samapereka chinthandizo momwe achitila bambo wapakhomo, nchifukwa chake amay amanena zokt abwelele.
      4 ndi mmene nkhani yakambidwila zaoneka ngt bambo wo ndi olakwa ndipo akuyenela kpanga zokt azipereka attention ndi chisamalilo.
      5 pali mafunso 7

    • @SpeCia-j1q
      @SpeCia-j1q 5 หลายเดือนก่อน

      @@CasBwoy3119 chiyambi ili nachoko km mathero ayi

    • @SpeCia-j1q
      @SpeCia-j1q 5 หลายเดือนก่อน

      2 Triple t chamba chake and inaimbidwa mofatsa

  • @CasBwoy3119
    @CasBwoy3119 6 หลายเดือนก่อน

    Thanks bro tidikire kut Ena ayankhapo motan then tdzapereka zotsatira