A Malawi Musadandaule Nyanja Ilipo - Country Man & Uncle

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 25

  • @MntinjafjrgrdtHdbydh
    @MntinjafjrgrdtHdbydh 6 วันที่ผ่านมา

    Achakwera mwatinyasa zochita zanu😊mubusa wakuba ndi kupha soka munatenga pa chilima osanamizana munaphandinu ngatimuli ndi mawu mundiyakhe ndipo muzafa ifa yosaziwika bwino

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 10 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂😂❤❤ bullets ija osazaiphwekesa

  • @JonaKanyangalamakondetsa
    @JonaKanyangalamakondetsa 7 วันที่ผ่านมา

    Koma ngati ndi kampeni kufuna kuti anthu akukondeni,mwaphonya khomo lolowera. Timadziwa kuti ndale za pa Malawi ndiko kuipitsiran mbiri. Ana a njoka,mukuchita monga state anu amachita, popeza dzungu silibala mphonda.

  • @JumaStambuli-w2i
    @JumaStambuli-w2i 10 วันที่ผ่านมา +2

    Koditu malire amaiko tonsefe tinawapeza anatigaila tonse ndi atsamunda ndiye malire amalawi akhalapo kuyambira kale n malamulo adziko lonse analiposo n tanzania ikudziwa kuyambira kale malire adziko lawo kusintha kwa map adziko lawo ndikungofuna kubweresa zisokonezo

    • @AthumaniAolo
      @AthumaniAolo 6 วันที่ผ่านมา +2

      Tanzania tuna maziwa makubwa matatu ziwa Tanganyika na ziwa Victoria yote mipaka ipo kati kati iweje nyiny mtake ziwa lote liwe lenu, sasa tunawaambia kuwa nusaunya lake Nyasa ni letu, na hamuwezi kufanya chochote kile

    • @kakawamashariki8978
      @kakawamashariki8978 วันที่ผ่านมา

      ​Salaam ziwafikie toka Nyerere land.umetoa uchambuzi yakinifu ndugu.​@@AthumaniAolo

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 10 วันที่ผ่านมา +2

    AMALAWI IFE TISAMASANKHE PRESIDENT WOSAUKA .CHIFUKWA WOSAUKAYO AMATHAMANGIRA KUMABA NDALAMA OLO CHUMA CHA NZIKA..SO LET US MALAWIANS NOT ELECT POOR PEOPLE TO BE OUR LEADERS.OK FELLAS !!

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 10 วันที่ผ่านมา +2

    Ndipo ameneyi watikwana bwanji

  • @RAJABSTYLESTYLE-yi1el
    @RAJABSTYLESTYLE-yi1el 8 วันที่ผ่านมา +1

    akongoti walanda mumuze kut achoke kumalawi iyeyo chikangawayo

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 9 วันที่ผ่านมา

    Sindingavele zopusazo ndizovela mazoba

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 10 วันที่ผ่านมา

    PAC inapanga chisankho chogwila ntchito ndi boma full stop

  • @NephtaliKumsenjere
    @NephtaliKumsenjere 2 วันที่ผ่านมา

    Nosense

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 10 วันที่ผ่านมา

    ACHOKE PA MPANDO CHAKWERA MWACHANGU..CHANGU..AKUZUNZA A MALAWI.@ ONSE A PAC ADZACHOTSEDWE MMAUDINDO AO.NAWO ADZIMUKA MMAKWAO MOSAUKAMO.

  • @FidelisKumwenda
    @FidelisKumwenda 10 วันที่ผ่านมา

    Osanamiza anthu, chonde. Malamulo a padziko lapansi amanena kuti malire nthawi zonse amadutsa pakati pa nyanja.
    Mzaka za kale kwambiri, Germany imafuna kumenyana ndi Britain chifukwa cha chilumba cha Heligoland. Pa zifukwa zosawakhuza anthu Aku Tanzania, a Britain anagwirizana ndi Germany kuti Britain ibweze Heligoland Ku Germany. Germany kumbali yake, ipereke nyanja yonse plus Zanzibar Ku Nyasaland.
    Atalandira ufulu, anthu a Ku Tanzania anangouzidwa kuti nyanja yapita Ku Malawi, pa zifukwa zosawakhuza anthu a Ku Tanzania. Izi wina aliyense sangavomere. Ife tonse Amalawi okonda chilungamo, tisavomereze kuti Malawi izikakamira kuba, kuwabera anthu a Ku Tanzania nyanja imene inali yawo. Za Heligoland ife ndi abale athu a Ku Tanzania zisatikhuze.
    Titsatire pakhota nyani mchira ndi pamene tingamapange ziganizo zolondola.

    • @PeterMorgen-k4b
      @PeterMorgen-k4b 10 วันที่ผ่านมา

      You are insane

    • @jackmambo2638
      @jackmambo2638 10 วันที่ผ่านมา +1

      Malamulo a kunyumba kwako Ameneo ndikuchipinda kwako

    • @mayesojameskatete
      @mayesojameskatete 10 วันที่ผ่านมา

      Go back to school and read more about this story my friend the lake belong to Malawi from the first map ma Tanzania akugwilisa map achiwili 😂😂😂

    • @MiddayDeleza
      @MiddayDeleza 9 วันที่ผ่านมา

      Lake Malawi belongs to Malawians not Tanzanian history imanena cbonchi

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 9 วันที่ผ่านมา

      Genesis to Chivumbuluso eeeee mwalembatu