Powerful skefa. You can't hate your leaders and say you love your nation. Respect to skefa for taking part to spice up this event, one love, peace for mother Malawi. I love you Mr President
Anyone who is against skefa for singing ku convention you are probably faulty in thinking,he sings as business,so he can not fail to go for it because some Malawian who is anti MCP will hate it😂😂😂😂😂😂
Koma ndalama😢😢😢 ayi zikomo SKC what people are doing now in front of your grave? Ambuye imvani kulira kwathu ife a Malawi chifukwa cha imfa yowawa ya abale athu ku Chikangawa kuja, tikudziwa kuti sizatisiya tokha pa ballot paper paja, zaimeni ndi mMalawi aliyense patsiku lachitsankho
MCP yanyamukadi apa pa social media pano timapusitsidwa go pa ground anthu ayambaso kuchikonda Chipani cha Mcp Kaya mukufuna Kaya titukwana bwanji koma Chakwera alamulliraso mpaka 2030, pa social media pano pakutipusitsa amalawi Kkkkkk kooomaaaaaa!!!!!!!!!
Don't blame him it's part of spicing this event... Sanapite kumeneku ngati wandale km as artist amene anapatsidwa ndalama kuti akayimbe ukuku... Eee olo ndili ine man ndipita
Bola Chakwera ndi anyamata anzake atambala titha kuti mzachidziwikire kuti akunva kuotcha ,koma sindikudziwa Kuti achina , Nankhumwa,change golo,Ken msonda,Dausi ndi ena aja anachotsedwa muchipani chokoma cha DPP aja akunva bwanji kumeneko aliko😂😂😂😂
Kodi mesa ankati siwandale?gays let's listen again the Grace chinga's speach,just praying malawi gays🙏🙏🙏uti ndi nkhondo ya kuthupi tiyeni timenye ya uzimu
Powerful skefa. You can't hate your leaders and say you love your nation. Respect to skefa for taking part to spice up this event, one love, peace for mother Malawi. I love you Mr President
Skefa wachita bwino ndalamazo ndizaife amalawi osazisiira mphavazo ay udyenawo aise umakwana zkatuluka nboma uzaimbeso nyimbo yowaseka agaluo❤
This is end of beautiful talent my brother Skeffa
Go and ask Nkasa kuti anatha bwanji
How,....? Music is business boss and obviously he was paid handsomely
Thus the End of Talent watch out skeffa
Skeffa akusokola cash mmati akhala bwanji pa Malawi 😂😂😂❤❤
Anyone who is against skefa for singing ku convention you are probably faulty in thinking,he sings as business,so he can not fail to go for it because some Malawian who is anti MCP will hate it😂😂😂😂😂😂
Amalawi muli ndi vuto yamikirani chabe skeffa akuyimbira ziko la malawi kuwonesa chikondi basi amalawi ma jealous ndi ufiti wachuluka
mukubera nyimbo za DDP a Skefa chimoto aaah ndakutulukan basi
Ife timakonda luso la skeffayo💕💕 osati zinazo
Ndakutulukani a skeffa
Dan Lu ndiye tsogolo lake lilipo poti amayimbila Dpp? Inu kodi ndi Mulungu? Tsogolo la Skeffa ili mmanja mwa Mulungu, osati mwa munthu
Koma zowona Muthu ungamamusapote fumu yoyipa Mmmm
Ma biggey kusungunula mafuta mthupi 😂😂mimba kugwelela muja motie kotooooooo😂😂😂😂😂
Wakwiya ndi kamanjekete wagwanayo ndalama ndizomwe waonongazo 😂
Skeffa ndi machine
Skeffa my artist, apa mwabesa ma fans anu, uziona
Ndipo kwambiri
Koma ndalama😢😢😢 ayi zikomo SKC what people are doing now in front of your grave? Ambuye imvani kulira kwathu ife a Malawi chifukwa cha imfa yowawa ya abale athu ku Chikangawa kuja, tikudziwa kuti sizatisiya tokha pa ballot paper paja, zaimeni ndi mMalawi aliyense patsiku lachitsankho
MCP yanyamukadi apa pa social media pano timapusitsidwa go pa ground anthu ayambaso kuchikonda Chipani cha Mcp Kaya mukufuna Kaya titukwana bwanji koma Chakwera alamulliraso mpaka 2030, pa social media pano pakutipusitsa amalawi Kkkkkk kooomaaaaaa!!!!!!!!!
Skeffa ndakutuluka ndiwe chikangawa part 2
Kkkkkkkkkk a Skeffa Chikangawa
Don't blame him it's part of spicing this event... Sanapite kumeneku ngati wandale km as artist amene anapatsidwa ndalama kuti akayimbe ukuku... Eee olo ndili ine man ndipita
Nyimbo siyachipani Nanu kkkkkkk koma anthu ena awa
Koma amene anaganidza za ndalama anakonza Mmmm where do you think you are ending Skeffa?.
Everyone has got a right tu du wat he/she wants...ndi mene wazionela skeffa minding his own biznes.....
Ambuye Muwapatse moyo adani anga osewo, Mcp boma😂😂😂
Skeffa ndiwe Kaini basi,timakukondani koma izizi mwayambazi ,ndalama yoopysadi inapha yesu
Brother skeffa malowa ndale u know meaning ya ndale wait koma osazauza anthu osapupuluma posaka ndalama
Koma ndalama.., inaphadi yesu .
Skeffa wabwino bwino uja wapenga.😅
Bola Chakwera ndi anyamata anzake atambala titha kuti mzachidziwikire kuti akunva kuotcha ,koma sindikudziwa Kuti achina , Nankhumwa,change golo,Ken msonda,Dausi ndi ena aja anachotsedwa muchipani chokoma cha DPP aja akunva bwanji kumeneko aliko😂😂😂😂
Mmmmm kma dziko lamalawi kuvetsa chisoni
Skeffa u r finished I'm watching you...
Ine or skeffa atadzasiya kuyimba koma ndidzaMkondabe chifukwa nyimbo zimene wayimba iyeyo zasintha moyo kwambr
Mesa anayambira kutulutsa nyimbo yodandawura chilima ameneyu koma ndalama anakonza😂
Woyimba alibe mbali ❤❤
Safuna ndalama ndindan inu..
Olo muli bread winner mungatan..
Ana atupe ma offers alipo?
Nzanu ali mu office mwake,azisake basi
Kukagwira Dala mabaterry a Mkango utagona uku kkkkkkkkkk
Askeffa be careful zandale zimagwetsa career yamunthu
Kd skeffa wa ndi wa mcp?iye akugoimba basi kusangalatsa anthu,ndemwat bwa??
Eeeee ndalama ndisatana yoo
Kodi mesa ankati siwandale?gays let's listen again the Grace chinga's speach,just praying malawi gays🙏🙏🙏uti ndi nkhondo ya kuthupi tiyeni timenye ya uzimu
Skeffa this skeffa that aaa inu mwatan kod. .. are u gonna pay his bills? Everyone is hunting for salt
Bartimeus wa ku CHIKANGAWA
NSANJE SIZINTHU KKKKKKKK ZAWAWATU KKKKK MUNYA MUWONA SIMUNATI😅😂
Ndimaona ngati nkasa yekhatu
Mmmmmm mukuzinamiza
In jesus name , 😢😢😢😢
Inu uyu siwoyamba kumakayimba mmisokhano ya ndale kunali a Lucious Banda komalizila kwake akut akuyimila UDF a Joseph Tembo nawo ndikuyimila DPP naye uyu skeffa
Muva nayeso ndufuna kuyima pa MP sizachilendo fanz izi
Musiyeni muthu akusokola chakudya cha banjalake
Luso ligwire ntchito malipilo ake ndi money basitu
ndale zapamalawi,umavina ngakhale sukufuna, akuti kusangalasa abwana kkkkkkkkk bwana amakhala munthu akulipilidwa ndinuyo?
Nsanje ndi yomwe ikukuvutani, olo mutamutuluka sadziwanso kuti mwamutuluka
Oyimba odalirika ndi Billy komanso mlaka malito basi , achoka kutali koma olo za ndale amayimbanso mwandale
Odalilika chifukwa amatumikila DPP 😂😂😂😂 nsanje adakonza
Don't think that anthu mukamawapanga follow aziganiza zomwe mukukaniza amalawi chonde. Skeffa still has followers just like Dan Lu😅😅😅
Km ndrama tiona zinthu 2024🙌
Or ndili ine nkanaimba nkhani ndi chakwaza
Mmmmmm plz skeffa don'tsupport chakwera plz 😢
Ndamutuluka
Kutha kwa luso asikefa 😂😂
Komatu penapake eti skefa azikhala serious,,chakwera waBeBa patipo pamenepo???
Wakwiya ndindani?
Paja skeffa ndi wa satanic musaiware abale wapita kwao kwa chakwera Joyce Banda onseo Ali gulu limodzi ndiye musiyen chimene akuchita etu grace chinga nzimu wako uuse muntendere
Zoonaaaaaaa!Mcp yomweyo
mwayamba kuyimba mundale ofuna musamale mutha ngati makatan khaya simutiva
Sikefa nyimbo zako ndazitulukabas sidzamvelaso ndinkakuona ngat umaganiza km hoooo
Kkkkkk
Sikefa nyimbo zako ndazitulukabas
Koma ndalama tiona zithu mu 2024
Skeffa chimoto ndichisilu pano zoba sure
TAMADYANI NDALAMA ZAKUBAZO,AZIKUMBUKA AGALU AMENEO SKEFA ZILANDILE
Eish very disspoint oyimba wanga u have money why now u join there
Musaononge mbiri yanu ndi MCP a skeffa muyedzekedwako kumeneko
Cassandra Dale
Basi band yoidalila panopa ndi ma blacks
Ma blacks amapitaso kuzipani iwe nawe,,,,tingovomerezaamalawi ndife okonda ndara komwe kuli ndarama ndikomwe tikupita tikupita
Mpakana apa Askeffa muli pati pati makamaka eeeeeeeeee ndalama ili paminga
Walakwa chani skeffa...???
Mpaka Skeffa, useless
Skeffa uja
Skeffa wakwela yakuphwa 2025 mcp ikutuluka m boma
Zaziiiii😂😂😂😂
Tiwamvetsetse anthu they just need money umphawi wavuta kumalawi.izo ndi nyimbo zomwe anamutuma kut akaimba amupatsa zindalama
Utsiru wakula nsinkhu pa malawi
Sikefa kuthatu uku utha ngati sofiya umayiwonatso pano Sofia iweso utha chotcho
Akunjoyayo ndani zachamba
Chiyambi chakutha man basi 4:07
opanda kumvako kuti nkhaninyazinthu zodulazi atithandiza bwanji
Alibe ma plan awa
Ife tinachituluka kale chisikefacho
Zaufiti basi
Fitsi uyuuu tilibeso naye ntchito wakupha
Skeffa like crsly
This is the End of skeffa
You are totally finished for ever
Kuwapusisa anthu bas
mwayamba so izi akulu kuthatu uku
Pano awa anaonetseratu kuti nda mcp
Koma kungiziyakusa uku
Ndalama anakonza😢
Iwe siwandare
Am so disappointed with my artist nw
Chakwera boma
Chiyambi chakutha man basi
U re finished