Amayi mhmmmm, Mumatha ndipo Mulungu anakudalitsani. Mwanditengera malo ena ake. Ndatsitsa nsozi chifukwa cha uthenga olamitsa. God bless you abundantly Mayi. Have been listening this pa repeat from Springfield - Virginia to Baltimore Maryland. ❤️🎻🤗🤗🙏🙏🙏
Chemwaaa anga Farai mmmmmmmm Ambuye akudaliseni koopsa zedi Amen mmmmmm mwapha ndipo mukuswa mwanva 🙏🏿
Nyimbo Ngati izizi kuimba kwabwinoku ndikomwe kumafunika kumatenga ma award osakhala zina timadziwona mudziko mwathumu mmmm, zikomo kwambiri Farai Chazima Soko🙏🏿🙏🏿
Asis mumatha glory to God for the talent,we enjoyed your performance at abundant life assembly Lansdowne Capetown
Very beautiful song my sister Farai Chazima
this hit imandisuntha zeedi
I love this Song very powerful
I really like this song alot
very powwrful song indeed
Amayi mhmmmm,
Mumatha ndipo Mulungu anakudalitsani. Mwanditengera malo ena ake. Ndatsitsa nsozi chifukwa cha uthenga olamitsa. God bless you abundantly Mayi. Have been listening this pa repeat from Springfield - Virginia to Baltimore Maryland. ❤️🎻🤗🤗🙏🙏🙏
Mulungu apilize kukudalitsa
Amen
great job in saving the nation
Nyimbo 😊✍️✍️
Amen!
Zilibwino
Amen
Amen
Amen
Wow wow wow nyc one