Welcome and we'll done Mr DC kalindo chilungamo chikhale chilungamo or if tiling kuno ku RSA watikwana Chakwela ndi mcp yake fertilizer sanafike mmene chakwela wapangila mgodi wamalawi ndiulimi mcp ipite enough is enough
Kuchita celebrate ngongole ya 100 billion koma ogwira ntchito mboma omwe anapuma kuyambira 2022 ena 2023 ena 2024 uno osawapasa ndalama zawo boma la mtundu wanji ili
Ndipo live baba chakwela akufuna kapeni kkkkkkkkk warepela ndithu 💪🔥 Mangochi oyeee zomba oyeeee 💪💪💪
Ulemu wanu Dr dc born kalindo❤❤
Long live our own freedom fighter ❤
The DC timakunyadirani ulemu wanu ife tikukusatirani bwino bwino
Welcome back our very own president
Ulemu Wanu mumatiyimilira ❤❤❤
All the best Mr DC
Boni kalindoo zangongore .........
Boooon !!!!!! Kalindooooo!!!! You. are. the greatest !
machine Bon kalindo mumakwana bwana president
Mulungu akutimenyera nkhondo yeriko kwawo
Azibusa oputsa muziwantchula Maina awo Kuti ayaluke
I wish mukanaima nao presidential
😅😅😅🤣 ndipo tell them DC m'we Ni m'we vakusyausya and Mangochi don't try to come
MY president 🎉🎉🎉🎉❤
Your welcome back the dc
Ntchito akulembana okha okha a congress MMA department onse,tinatopa nkulembera vacancy,tiwona a 2025
Ndipo mimba mumatseguka ngat sitinva mau anu bwana DC
Well come the dc
Our true freedom fighter in malawi ❤😂❤😂😅.
Akakhala ben longwe anagwilira mwana wake omupedza kusouth Africa 😂😂😂😂, anayenda cha uyu uyo 😂😂😂😂anathawanso chifukwa chakuba magalimoto poopseza ndimfuti 😂😂😂😂, kodi amatuwatu 😂😂😂
Timakunyadilani bwana kalindo ndipo timalimbikisidwa
Born kalindo mwana oopsya kwmbr welcm bk my president
The deceeee more 🔥
The group leaders for NIF would be New branded branch chairmen to be used during elections in 2025
Indeeee zitsiru za china Chakwera
Welcome and we'll done Mr DC kalindo chilungamo chikhale chilungamo or if tiling kuno ku RSA watikwana Chakwela ndi mcp yake fertilizer sanafike mmene chakwela wapangila mgodi wamalawi ndiulimi mcp ipite enough is enough
The DC 💪 always with you 💕
Palibeso wina ngati inu a DC
Kalindo iwe ndiye anapanga😂😂
Manganya alibe mfundo mbava
DC ....fire umakhwanaaaa
Pamenepo mosemuja ndalama akaponye lero kwadzaka 4 😂😂😂😂 ayalukadi
God bless you and protect you Booooni! Kalindo
Kuchita celebrate ngongole ya 100 billion koma ogwira ntchito mboma omwe anapuma kuyambira 2022 ena 2023 ena 2024 uno osawapasa ndalama zawo boma la mtundu wanji ili
U can say that again
Kkkkk inadzadza empty palipose 😂😂😂😂😂
Boooooon kalindoooooo the DC mumakwana ❤
THE DC MORE FIRE
Wlcme back the dc
Tang'alula iwe bro the DR
Koma inu ndinu munthu wa chilungamo even ogontha ayi aseguka
Zoonadi komano mutilangizile makolo akalewo chifukwa ndiomwe amavotera mcp kutengela history
Adc mumakwana, pitilizani kutipasira uthenga wabwino wotidziwisa Zomwe zikuchitkka mdziko muno, God bless you mr dc
Ulemu wanu a DC
Ngalura owe Dc
Wulemu wanu Mr Kalindi your are standing on the truth ♥️♥️
😂😂😂😂 kom DC paka a tiphikila eyoo popedza 🇲🇼 aiwala km ndikukaikilaso kuti tiiwaladi aaa
Anyanayo amenewa sazaona voti mu 2025
Apa DC waing'alula zeni zeni 😅
Boooooooon Kalindoooóoooo Mwana Wakwathu Ku Mulanjeeeeeee mmatiimilira mulungu azikutetezani nthawi zonse
Umakwanila DC❤
Muuzeni manganya azikapanga tikufelanji alibe mfundo
Manganya alibe mfundo
The DC
More fire the DC timanyadira Mulungu akutetezereni
Ulemu wanu 👍👍👍👍👍
Welcome back Mr DC
Ulemu Kwa Mr kalindo Moto kt buuuuuu
Landilani ndalamayo yachuluka the DC
Respect to the DC
The DC 🔥🔥🔥
MR DC more fire kma ndimafuna number yanu bwana president
Maro mopeleka makhwala dzipatala kukwedza malipiro kusisa ndalama yaonongekayi ati km apange celebrities machendawo bs
Bwana munasowatu musamasowe chocho Dc ❤
Welcome back dc
Continue mwanawe wa panjeza
Zikatipeza ndalamazo mdidzilandila koma sitingavoteleso mcp nanji sitimkaifuna kale tinavotela chifukwa cha chilima
The DC mwana oopsa kwambiri
The Dc❤❤❤❤
Well come back
❤❤❤ DC
The DC we love alot
Galu iwe ukhalira yomweyo yomangobwebwetukayo chitsiru iwe
Andipeze kuno pa shop panga naneso plz😂😂😂😂
Size zoona mphwanga pitiliza
Welcome the DC
Allah must protect you
Our legend
The Dc bon kalindo 🎉🎉
The Dc inuyo ndi one kkkkk timakunyasirani ife mademo aja achitike mcp madz akhaula tilandira sitiwavotera agalu waw
I'm listening from Zambia powerful speech your a man without fear .
The DC!!! Ng'alula ng'alula
Ulemu wako pambuyo panu Mr p
🔥🔥🔥🔥👍
Campaign yavutad
Tnakusowanid timakunyadilan THE DC ❤❤❤❤
Welcome back mr DC ndimakunyadira mwana wakwathu🫡
❤❤❤❤❤
More fire DC
big mani kuwa ng.alula achina nama nchende a mcp
The DC the one I know your so great may Allah guide you all the time
Kalindo 😂😂😂
Kkkkkkkkkkkkkkk koma Mr DC, akut Stadium inadzadza Empty😂😂😂😂
Akhaula amenewo DC osadanda
Munthu wamkulu kwambiri the DCeeeee, nyaduuu
Kkkkk inenso ndayamba kuumba njelwa pano abwele machende ameneyo azandithandize 😂😂😂 akuvutik amene uja
Chibwana kumalawi😂😂😂😂
Ndipo Campaign yayambikapo anthu ayamba kuzidya pano ndalama kkk Tuesday yiso achita manyaz kwa mmbaluku kuno tivotere kaye khansara ndithutu
The D.C. ❤❤❤😂😂🎉
Vilombo vina vili against the DC.. Valemba against the DC.
Mbuyanga timakusimbwilani kwambiri ❤❤
Akunana kuti mr kalindo wamisala ndiyeyo mwina ndiwe wemwe ngulu limodzi koma nyiye mukhaula simunati mupsa moto