Makendulo aziyatsidwa pakuti sakuyatsidwila pamyumba ya munthu,, Koma munthu amene angaletse kuyayatsa makendulo pitani kunyumba kwake makendulo akayake kunyumba Kwa amene akuletsayo , komaso dziwani Kuti amene akuletsa kuyatsa makendulo mufufuzeni pa ifa ya chilima ndi anthu ena ndakuti anali nawo kokapha chilima ndi anthu ena aja
@@FocusGeresom-hj3os iwe sukuona kt ndi kampeni palibe amakonda saulosi apa ndipo mnkutheka ali pamenepawa ndiomwe anapanga chipongwe america ikulimbana ndi German Russia sinkalowerera imakana koma America inapanga ndege ndikuika zindindo za German kukagwetsa ma bomba ku Russia kenako Russia inaona kt aaa a German ikupanga za ife ndikuyamba kuthandiza America ndiye malirowa ena apeza chida chopangira kampeni koma amalawi ambiri tinazindikira akuchedwapo apa
🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Will owez miss this voice,a voice with authority chilima why ???
Amen 🙏 🙏
ALUTA CONTINUAWA !!!!!!!!!!!! SKC❤❤❤❤❤
Kuyatsa MA kandulo kupitilire mpaka Tonse Alliance idzachoke m'boma
Omwe zikuwanyasa asamapite koma ndipemphe kuti Mwambo oyatsa makandulo udzichitikanso ku Madera a kumudzi kweni kweni
Osaopa!!!!!!
Osafoka!!!!!!
Osasiya Kuyatsa makandulo!!!!!!!!
Continue kuyatsa ma candle kt mzimu wa SKC uzigona kmnso kt chakwera ayamba kubwebweta yekha za imfa imeneyo,Osaopa ..from Cape town
Kodi kansonda ndikachani?
❤❤❤kulibe kuletsana kuyatsa makandulo akamuphelanji chilima
Ngat a mcp zikuwanyasa nawonso ayambitse Tembo candle lighting
Musasiye kupañga zimenezi lusifala chakwera ndi ana ake achite manyazi
Aaa MCP anaying'alula pokupha chilima bolani akanangotsiyana otse ali moyo apa 2025 zamvuta dzedi
Mbambande Benjani kaluwa
SKC lolani mzimu wanu utsogolelebe UTM Mwa ife tokha sungathe , Rest in peace
More fire UTM. God bless
Yomweyo galu iwe kumene uliko sonda uli kt kodi tayelekeza kutimisa anthu akupondele koko
Makendulo aziyatsidwa pakuti sakuyatsidwila pamyumba ya munthu,, Koma munthu amene angaletse kuyayatsa makendulo pitani kunyumba kwake makendulo akayake kunyumba Kwa amene akuletsayo , komaso dziwani Kuti amene akuletsa kuyatsa makendulo mufufuzeni pa ifa ya chilima ndi anthu ena ndakuti anali nawo kokapha chilima ndi anthu ena aja
Kuyankhula nde tikuyankhula koma kubanso.
Amen
Amen ❤❤❤❤
Tisiya mwambo wa ma candle zitafa mfiti
❤❤
Komatu ka clip akaa aaaaaa ndikawawa 😂😂 Moto Kuti buuuuuuu
Continue guys ❤❤❤
SKC ❤ UTM ❤
Msonda ndi chitsilu chamunthu, osamvela zomwe kamanena, ndi kahule ka ndale kamenekaja kamangolowa chipani chilichonse.
Continue Resting well
Osaopa osatopa osa fooka nde khaniyake asonda mutuwanu
Msonda kamutu kadataya uku apita uku apita kamunthu kosokoneza kwabasi
Nsonda machende ake inu hiv yamuswa uko
Osasiya
Alikuti a nsonda?
Aluta continue 🔥
Yomweyo utm.
Who is sonda mwambo woyasa ma candle 🕯️ usutha afune asafune
Moto motoóooooooopp
Ken sonda tipha ndimbama
Mpaka wina asegule mmimba basi😂😂😂😂
Amen 🙏🙏🙏🙏
Galu msonda panthako pake
Kampen imeneyo kkkkk koma malilo amenewa!!
Nanuso inu maliro ndi kampeni zugwilizana bwanj
Inunso yambanipo kampeniyo
Ndiwe Galu kwabas
@@FocusGeresom-hj3os iwe sukuona kt ndi kampeni palibe amakonda saulosi apa ndipo mnkutheka ali pamenepawa ndiomwe anapanga chipongwe america ikulimbana ndi German Russia sinkalowerera imakana koma America inapanga ndege ndikuika zindindo za German kukagwetsa ma bomba ku Russia kenako Russia inaona kt aaa a German ikupanga za ife ndikuyamba kuthandiza America ndiye malirowa ena apeza chida chopangira kampeni koma amalawi ambiri tinazindikira akuchedwapo apa
Nsonda munyapo ndi chipani chanu Ana anjoka inu please guys keep going to burn candles 🕯please please
UTM ku buuuu
Amen amen 👏🌎💓
Fredokis
Moto utm palibe kusiya ai
SKC kufera mbendera😢
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen ❤