Maganizo anga all the way from SA ,Vice achoke kwawo ku mcp chipani choipacho nanga tiphatikiza bwanji tiligu ndi nasongole let them finish there term so that when ADADI akamabwera asazaone khope pomanga zimbalangondo.
Fredo ndi wa chinyamata wanzeru angathe kulimbikitsa ndale za achinyamata ❤
Only kaliati m boma wakhalamo kwambili❤❤
Komanso vimitima Va anthu a MCP ndi voyipa ,mgwirizano unatha kale ,dziwani Kuti amene alole been vice president from UTM walowelathu MCP
Asiyeni a UTM awuse muntendere misozi siinathe yolira presdent wao,,mwachidule asankhane okha ku MCP komko
Akhare azikhare ng,oma nduna yachakwera mukufuna muphese ndani😢😢😢😢😢
Utm musalole muzigofa akhalere zikhale ng 'oma kumbukani ifa yachilima
Fredo🔥💪💪
Ifeyo tikufuna timuziwe yomwe anayikapo dzanja pokupha chilima ndicholinga akhale vice president
Penjani emweyo Ali 🔥🔥💪
Yeah ineso ndagwilizana nadzo zimenedzo Fredokiss akhoza kubwezeresa mabala omwe alirawo Amalawi pakadali pano 😢😢
Good advice
more fire Fredokriss
Mayi Kaliyati atenge utsogoleri basi ndipo tiwapanga support but we just want a strong and unified UTM party.
I wish Kariat❤
Mai kaliyati ndi mtondo amaiyu kunena zoona amadziwa ntchito yake wangokhala kuti ndi mkazi koma atakhala president sipangalakwike
Ndizoonad 💪💪
Tikusuna wachinyamata ndithu kubweresa achiyamba kale zioononga legacy
Asankhane okha koma mmm zikuopsatu is ladies and gentlemen
Kale fredokiss skc 👌🥰
Ndinali busy kuwelenga ma comments koma ndawona kt fans yambiri sikumvetsa SAM (Nkhani ndi yakuti UTM ndi bwino isankhe Fredokiss kukhala mulowa malo wa DR Chilima malinga ndi legacy yake ndipo ine nyamata wa ku Ntcheu Bawi ndagwilizana nazo or abwelere ku DPP basi...
Msiyeni fredo adyerere we're trust him kuthi we gotta future here Malawi from him nde ukumpereka kwadani a mcp no no no Fred plz take time to guess it about this fake ensures
Asankhe acakwela cifukwa Mikasa ndinu a utm akuphaso so kuti tikazingo kurila yai
Wachepa ameneyo ndiwachikoka kumaimbidwa km kuzandare ndimwana kwambiri 😅
Kudzadzitsa stadium ndi nyimbo ndi zosiyana ndi kupeza ma vote kapenanso kuyendetsa dziko, utsogoleri simungapatse munthu amene analephera u MP.
I think maganizo akowo ndi abwino but lets wait and see because mbali ina a president antha kufuna experience otherwise fredo alinso bhoo
Kanyimbo kakuvepa pasipasiko Kali bho
Ndiganizo lolakwika cz mumuphetsa munthu adakali mwana msiyeni munthuyu
let them finish there term asankhane okhaokha a mcp aziphana okhaokha
Komatu a mcp ndibwino kuti asankhane wokha, chifukwa or fredo atapasidwa udindowo palibe chimene angakanene a mcp angakamve, koma atasankhidwa kukhala president wa UTM zitha kukhala bwino kwambiri ndipo chaka chamawa atha kuzawina ndithu 😊
Amen
Mzotheka fredo kukhala replacement yabwana chilima kuzaima ngati president wa utm 2025,koma kwa panopa za u vice President zo ayii zisamukhudze asankhe ku mcp kwawo komko.
Asankhane okha akweni musalore chonde mufanso nanu ifeyo timakunyadilani mama,a mcp adalephera kumulemekeza chilima lero ulemuwo ukhalepo coz wafa zaziii.vice achoke ku mcp vice President
Imene mukunenayi ndi ndale si nyimbo udindowo ndi wawukulu wakhozeka kufela amalawi fredo
Inu anthu Fredo angakhale vice president zoona? Komainu mukkuonangati wafiapo ayi wachepa kwambiri
Asakhane okhaokha amcp Sinanga sakufuna kukhala bwino ndiazao mapeto ake autm atha ndikuphedwa
Mchana fredo asamale kwambili ife timakukonda sitikufuna usafe ngat chibudu
Komatu dzikoli tsiku likubwera tidzagawana ndinthu tilibe dzaka zambiri mwakanika airport ngati konyera ziwwto misewu zosankhara bwino tidurana limeneri
Za chibwana,mwasowa osakha eti,
Mukuona ngati VP udindo wa chibwana eti.
❤❤❤
Kodi mulitengela dzikoli zachibwana eti fredo ndimwana kwambili ndipo sanafike poti angalamulile dziko ameuja komaso sizoti vice Accokeek ku utmost asiyeni agalu akuphawa apange zomwe amafuna satiphela munthu wathu nde apangeno decision yawowo tiwaone
Mmmmm nkhani iyi ndyayikulu kwambili
Komanso ndikamaona fredokiss sanakhwime, ndimwana sangalimbe ndi mcp
Fredo❤❤
Musaphese mwana musiyen zimenezo komweko ku mcp konko akalowa wina amuphamso fredokriss sanadyelele muleken Akali mwana
tili nkati momulila chilima mu 2024 ndiye sizoyenela kuti ayiketso munthu wina wa mu utm osalola zimenezo 2024 ithe no vice president adadi akamabwela azawamange bwino onse wautali ku maula .
Ife Akunkhota Kota 2030 tidzilamurara patonkha tatopanazo kusefukira Madzi ma week awiri Boma sinabwere we don't have gavernment
Dr namadingo
Fredo angokhala reader of utm osati vice president wa ziko ngati analiri chilima coz a mcp apha mnthu ofunikila komaso msogolere wa utm ...asankhane okha amenewa
Akweni
Chilima anamuimika kwathawi yaitali amagwile ekha chakwela zivuta bwanji Kuti amalizeso ekha kwasalaku komaso kaliyati ndiwabwino kwambili koma kwathu Ku Malawi stinakozeke kusogoleledwa ndiadzimai ma
Fredo yomwe 🔥
Fredo 🔥🔥🔥🔥🔥
Aaah koma narrator wa video iyi sakuganiza bwino . Izi ndi ndale not music game . Ndiye kudzadzitsa anthu pa stadium doesn't mean kuti he got capability of winning running the government.
Kuimba ndi ndale ndizogwilizana??????
Musaphetse anthu asiyeni mfiti zizilamulura mfiti zokhazokha a UTM asalore ndi pusipusi akufuna kuwaphimba kumaso
Zimene mupangazo mukulowetsa chibwana. Ndale ndi kuyimba sizikugwilizana olo pang,ono. Komaso poti mukugofuna ndalama musankheni amaneyo muzigophana zigulitsani Moyo wo tione Ngati mukagule Moyo.
Kaliyati anali bwino chifukwa akuziwa goes ya chipan chawo fledo akadali mwana Atha kukanamizidwa ndi chakwela koma analiso boh fledo
He can make it
Iwenso ndiwe chitsiru umapanga ma program yako awo ukufuna umuphetse mwana wa eni ake asankhane okha agalu a MCP ine ndikuti machende ako pamozi ndi a MCP
Frend
Mayi kaliat ndi munthu wabwino kwambili
Misewu yomwe ija satsamunda takuyetsani mwakanika ma Brige tilibe kulibe dziko losauka anthu ndiwopanda chitukuko
Mukufuna mumuphese mwana WA eni?
We need a person who has vision
Mmmmmm inu siyani izi
Angakwanise udindowo ndi fredo komachonde asatiphereso amatimvetsa kukoma maganizo Anga fredo yomweyo amarawi tiyeni tipage sapoti nyamatayu mwina tiwonezina
Athese mugwirizano ndizakuyima pa wokha a utm azawina sure
Iyoyo sanankhwime pa ndale
Iwe kuyendesa ziko ndi kuyimba ndi zinthu ziwiri zosiyana ngati akulephera Abusa
Asiyeni a UTM apume cholakhula palibe .
Asakhane a MCP okha okha.Kapeni ayike a police ayimile mpandoo basi . Pompano tivota basi
Koma nde fredokis yo nde sangapangidwe chipongwe? Tiganizepo bwino pamenepo
Fredo wachepa nazo abaphunzira kaye ndale kuti Akhwimee
Sono pano tizikamba zamaganiz ako?!!?😊
Fredo akuyenera kukhala mmulowa malo a SKC
Ndithenga ine malo bg
Komano Samu yu mutu wake siukudyela zoona angamayelekeze Fredo ndi SKC
Kodi mukuzitengera zibwana zinthuzi eti?
Wachepa komanso athayambitsa nkhondo amalankhula zinthu zosapya
Iwetu iwe mwina akutumadi,upiteko iweyo akusankhe u VP,mmene wafera chilima alipo angakhumbileso zopusazo? Olo dyera landramalo kagwele uko
Manganya ndikape wa mcp ali mgulu lakupha chilima galu wachabe chabe
Maganizowo ndiabwino km akadalimwana mix akadalindizokhumba zochuluka
Maganizo akowo ndangwilizana nawoso ine
Mwaganiza bwanji nanunso?
Mukufuna mumuphetse mwana? Wa utm angalore zimenezo ndani? Asankhane konko ma evils
Fredo alibho km mwina kwaine ataimila kuyambira 2030
Mai Kaliyati sangalole zopusazo nthawi yatha kale abale anga a utm ndimveleni limbani mtima musangalala pompano
Fredo ndiwoyenela kukhala vice president
Fredo ndimwana kwambiri wachepa
Ukamabva kupusa nkumenekoo sam ndinudzitsiludi etii
Mwana wa chepa ,Music si ndale ,kupite Kaliati
Mxxx!
Mwaiwala fundo imodzi ndi handsome nso apanga replace mawalidwee
ndimaganizo abwino km asiyane ndi MCP
Maganizo yanga akanakhala Patricia kaliyati poti MCP ndiyakumpha azatiphelaso kulibwino asakhane wokha
IWE NDI OFOIRA KUIMBA NDIKUYENDETSA DZIKO ZIKUGWIRIZANA PATI
Kodi manganya amuchotsa ku utm😮😮😮
A MCP asankhane okha okha
Iwe nzeru ulibe .Chilima amayendedwa pansi
Ngat amupha chilima,tinato sitingalimbe azingopotokola...ngtvwayaka wawuwisi .....nanga mapesi..kuli achina chimwendo ndanzawo the tyrants
Amalawi Fred Kiss angopitiza kuyimba komweko chikoka chakecho agwele nacho uko, amalawi kupusa musanhkabe mbuzizo
Aaaaa fredokis sangamuike pamenepo
@@IsaqueFiniassezopangana😂😂😂😂😂😂eeeh anthuuu
😅😅