TANVANI ZOMWE WAYAMKHULA BENEDICTOR MBEWE ZOKHUDZA PETER MUNTHALIKA NDI DPP

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น •

  • @AxelCarl-v7k
    @AxelCarl-v7k 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +19

    Don't simply retire from something; have something to retire to. Start saving, keep saving, and stick to investments.

    • @KingsleyAfingi-q5v
      @KingsleyAfingi-q5v 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      It's really heartbreaking to see how inflation and recession impact low-income families. The cost of living keeps rising, and many struggle just to meet basic needs, let alone save or invest.
      It's a reminder of the importance of finding ways to create financial opportunities. You've helped me a lot Noahavamia!
      Imagine i invested $50,000 and received $190,500 after 9 weeks

    • @SandraBullocks-d7e
      @SandraBullocks-d7e 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      I can still remember the exact feeling on my biggest payday in the market. Imagine taking home $407k just from 12k initial deposit. For the newbies I'll encourage anyone to embrace copytrade as the best approach especially when you're a newbie

    • @QewOpe
      @QewOpe 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      🙏 *12k to 407k is significant increase. My first copytrade wasn't profitable. Please share who you copy trade*

    • @SandraBullocks-d7e
      @SandraBullocks-d7e 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      SHE'S MOSTLY ON TELEGRAMS APPS WITH THE BELOW NAME

    • @SandraBullocks-d7e
      @SandraBullocks-d7e 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      @Noahavamia

  • @ShadreckKambazithe
    @ShadreckKambazithe 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Exactly APM my vote

  • @IssahBwanali-i8w
    @IssahBwanali-i8w 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    I like u bro God blessing you

  • @collengoma6542
    @collengoma6542 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Malawi linari dziko la mtendele koma tinakana utsogoleri wabwino ndikusankha utsogoleri wa satana mudyelekezi chilima anali ndi nsanje ndi muntharika ndi chifukwa anaphatikana ndi chakwera munthu oyipa koposa lero chilima kulibe chifukwa chakusaziwa

    • @GeorgeMphande-le6kl
      @GeorgeMphande-le6kl 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      true chilima is the coz this

  • @ThomasShuga-z5p
    @ThomasShuga-z5p 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Wakumva wamva wosamva sanamve God bless you Mr Mbewe 👏👏

  • @LuckyKalengo
    @LuckyKalengo 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    You are speaking the truth. Keep on telling the people the plain truth.

  • @alinanehauya
    @alinanehauya 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Even Peter anayankhula ku times zama project amene aja. Peter ndiwozindikira osati tikuonazi

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    kumayankhula ngati chitete cha manyi nkhosi kumati BOMA NDI LOMWELI mwanyi eni eni

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Mau apose apa ndie kuli khutukuve zosauka angozitengera ma lorry misokhano

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mbuzi za wanthu

    • @spargomw
      @spargomw 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      😂😂😂😂

  • @TanazioBanda-i9y
    @TanazioBanda-i9y 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Man wa alankhula mwanzeru modzichepetsa ndipo 100% true

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God bless you my beloved brother

  • @DzalimbaChimkango-b7h
    @DzalimbaChimkango-b7h 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Nsogoleli ozozedwa muthalika

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Dream media tiyakhulileni tikufatu Ife or mvula mulungu watikwiyila chifukwa cha president opanda mzeru chakwela

  • @BrownMatonyola-xi3lb
    @BrownMatonyola-xi3lb 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Amalephera kunena zoipa za APM

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Perfect 👍 said brother man DPP ibwerere boma fuel tiguleso K600 ndi APM ndizotheka 💪💪

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Zoona Ambuye akudalisen ndithu Peter 2025 Boma 🙏🙏

  • @georgemdachi9054
    @georgemdachi9054 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Well spoken Benedictor mbewe....I'm behind you

  • @ChejaliChirwa
    @ChejaliChirwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Don't give up my brother🎉🎉🎉

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    PANO A MALAWI MUKUTI BOMA NDILOMWELI MUKAMUVOTERANSO CHAKWERA THATS THE END OF MALAWI, MUDZALIRA NYOOOOOO

  • @alicemalika677
    @alicemalika677 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo you are a man of God who believes in Him the God I know who is sited in the throne and the earth is His footstool never fails. Emmanuel

  • @JamuMailosi
    @JamuMailosi 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Munthu ameneyu ndagwirizana naye 100% mwayakhula chilungamo

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Integrity bro,,,,🎉 perfect said I love it

  • @TechZaketa
    @TechZaketa 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    DPP ndimene ili ndi ukadaulo oyendetsa dziko

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    ATUPELE MULUZI ADANENA POYERA ZOTI A CHAKWERA SANGALAMULIRE DZIKO LERO TAZIONA SI IZI

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Well spoken.Koma nkhani ya Biyeni imene idzaoneke mutu wake.

  • @EsnartTione
    @EsnartTione 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    A Mbewe Mulungu wolenga akudalitseni chimene mukunena ndi chilungamo chokha chokha adad my vote

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Amen Yona 1vs1 Mutu wakhani kuzemba yehova

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kumbukirani mawu a Atupele Muluzi zokhudza Chakwera

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwela ndimbuzi yamuthu kwambili thupa lachimanga panopa ndi 60,000mk thawi ya Peter ndima gula 6.000 chakwela kwake ndi kupha basi

  • @HaroonMaundala-lg5lg
    @HaroonMaundala-lg5lg 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ambuye akudalise polankhula izi. Athu aphuzilapo ndithu. Chakwela ndi mcp yakeyi ndi zithu zomwe zawononga dziko la Malawi. Tikulilatu midzimu athufe. Adadi zosezi sanachiteyi. Nde agalu ena nde kumati boma ndilomweli aaaaaa mbolizanu ndi ambuyanu achakwelawo.

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Tinazinyenga ndichala ndithu Malawi tikusawuka lero chekwela wapha amalawi basi 😢😢

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Perfect speech 🤝🤝🤝

  • @InacioCement-t7n
    @InacioCement-t7n 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kuyakhulatu komveka ndipo your true mafuno ophikira panopa eshhh

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Dpp my vote 🗳 ❤❤

  • @SanudJafari
    @SanudJafari 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Uthenga wabwino wakuva wava winawe nde uziti boma ndilomweli ukugona nayo njala😢😢😢

    • @ThomasShuga-z5p
      @ThomasShuga-z5p 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ufiti basi br

    • @JafarWiati
      @JafarWiati 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo inu

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwela anakana mulungu kuti iye sanali busi ndipo mulungu amuyendele padeladela ndithu

  • @GiftMathewe-fr3kn
    @GiftMathewe-fr3kn 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Good massage💙💙

  • @MableMwavu
    @MableMwavu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    I agree with you my brother DPP never did much wrong to deserve outage

  • @DzunguBenson-m4g
    @DzunguBenson-m4g 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Wonderful speaking

  • @GeorgeTambala-j1m
    @GeorgeTambala-j1m 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Listening from Johannesburg in south Africa but from machinga I agree with you my brother

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Please continue fighting for us malawians tikuvutikatu Ife😢😢😢😢

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo kwambili ndichikwiya boti mcp ndiyakhaza kwambili

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ineyo ndimalemela 85kgs koma pano 35kgs ndikufanana ndi mbuzi kulemela kwanga.zomsezi zachitika chifukwa cha achakwela ndi boma lawo la MCP ukapita ku chimbudzi ndi thomvu basi chifukwa cha MCP.

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God bless you brother,,, well spoken

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zoona bro sanje inatipwetekesa ❤❤❤

  • @EmmanuelSambani
    @EmmanuelSambani 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    You are speaking the truth magesi akudzimadzima kuno BT Chemussa.

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Perfect speech brother 👏

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mcp sizasintha ndi ya nkhaza

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Nkhan iyi ndi yoona chakwera alibe utsogoleri wabwno wativutitsa amalawi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    💯 %talk brother ❤❤

  • @FlorenceNjilagoma
    @FlorenceNjilagoma 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    You are talking realty,,,chakwera waliononga dzikoli kwambiri

  • @alelabana7257
    @alelabana7257 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    keep it up bro God bless you

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo iweyo ukuyakhulawe ukunena zoonadi chakwela ndkhuku yamuthu

  • @dorothymosimbwa3638
    @dorothymosimbwa3638 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma zoona Chakwera asazamangidwe??

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwela sibusa ndichigawenga chokupha ndithu

  • @malishimajidurajabu
    @malishimajidurajabu 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    zoonadi bro mavuto Alipo koma mulungu atisogolele kuti mcp yichoke

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Well Said mr B Kondowe 🔥 🔥 ❤❤❤

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Boss man thank you

  • @kalimahTarcisious
    @kalimahTarcisious 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    tell us more big up madala

  • @GeorgeMphande-le6kl
    @GeorgeMphande-le6kl 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nice speaking bro silute

  • @PhilbertoChaimah-l4p
    @PhilbertoChaimah-l4p 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    I agree with you pastor but chakwera azangobweza ndalama zomwe akuba pamodzi ndi nduna zake zonse

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂😂 Or Chilima samadziwa moyo wa chakwera...........ndipo chakwera samatha kupanga zithu payekha

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ndipo ndikugwilizana nazokwambili anthu awa anachosa DPP chifukwachachikulu inalinsanje %

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    akuti muzigulitsa matumba awiri a chimanga kuti mugule thumba limodzi la fertilizer eeetu mmaso muli gwaa

    • @spargomw
      @spargomw 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Munthu akusowa ufa oti adye so Chimanga choti agulitse achitenga kuti kut agule Feteleza? Chakwera pansana pake ndithu😂😂😂😂

  • @cosmaskadzanja1633
    @cosmaskadzanja1633 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ambuye akudalitseni ..tikuvutikadi it's true

  • @FrankBanda-w4f
    @FrankBanda-w4f 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Brother u say truth god be with u

  • @ElijahWilson-z7f
    @ElijahWilson-z7f 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Listening from KwaZulu-Natal

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    TSONO ADZAWASIYE NANGA ZAKU CHIKANGAWA?

  • @PhilbertoChaimah-l4p
    @PhilbertoChaimah-l4p 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Apm my vote 2025

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Adzamangidwa nkhani yopha Chilima ndi ena 8.

  • @harrisonwadinda6342
    @harrisonwadinda6342 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Perfect said neba

  • @CHARLESNdalam
    @CHARLESNdalam 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Iwe ndie munthu iwe🎉

  • @giftevans2957
    @giftevans2957 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nice 👍👍👍

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Listening from cape town u get point

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tumizileni # yanu ponyereni kenakake mumwe madz

  • @collinsmaganga8569
    @collinsmaganga8569 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ..
    .
    Powerful

  • @EvansEgra
    @EvansEgra 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Malangalanga admarc anatichotsa ntchito anthu 31,the time of Peter muthalika in 2015, Nena zina wosati za admarc ai

  • @noahkalima5294
    @noahkalima5294 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndpo mukunamalo sibozaaa,,koma chilungamo ndthu,

  • @ThomsonChipwele
    @ThomsonChipwele 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Please Pangani zimenezo boma lithe la mcp

  • @georgemponda
    @georgemponda 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Well said za nzeru izi

  • @FatimaKhan-i5p
    @FatimaKhan-i5p 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Brother Ben mwayankhulatu momveka bwino tiyankhulireni moto wayakatu uwu sizinaonkenso anthu osalakwa Akufa mosayembekezera Kodiak tipita kuti kwathu ndiku malawi kuno tipita kuti?

  • @GibohSize-s9c
    @GibohSize-s9c 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    A chikulile zabwino saphimba ulemu wanu bigy wakuva Ave osava ankhale choncho

  • @IsmailTambula-g1k
    @IsmailTambula-g1k 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwayankhule mophizisa kwawina aliyeze koma amalawi ndioveza chison kwamene amafuna chakwela ife kujon kut tikulila chifukwa chaulamulo wachakwela

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iweyo dream media we love you

  • @JoshTech-h4r
    @JoshTech-h4r 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thanks boss

  • @JoyceKasongo-s8k
    @JoyceKasongo-s8k 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Wanenabwino Ben

  • @naphymothiwa3791
    @naphymothiwa3791 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    More fire

  • @EvelynMaston
    @EvelynMaston 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ambuye akutetezeni brother

  • @noahkalima5294
    @noahkalima5294 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kulankhula izi munasala kudya masiku angati abwana,,chifukwatu mwalankhula monga munthu wanzeru

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Olo chimanga akugawa chija chinabeela ndi mayi Joice Banda , koma akuzitukumula ngati abweletsa iwowo , Crocodiles

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiye galu wins mkumati Boma ndi lomwelo , chamba

  • @WilsomNyirenda
    @WilsomNyirenda 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zauchitsilu ngachopereka chikuchepa ku Church ife zisatikhuze bwanji ma albino sakuphedwaso ma cyclone ose aja Anna, Fred, edai, covid, Cholere dpp ikanazitha ngati inachosedwa izi kulibe zikanawachitikira iwowo kukanakhara bwanji, ndiye anzanu asesa mukufunamduse moyera, sizitheka maloto achumba

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iweyo ndiwe mbewe kwanu komweko Dpp no more mukhalitsako ku oppositioniko limbani ntima utsogoleri si mafuta ayi

  • @LovmoMwanxa
    @LovmoMwanxa 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ambewe ndizoona zonse zambiri mukukambazi,,,,,,,,,,,,,,,, koma chomwe chingatithandize si ma demonstration ay tamemezani tililire kwa MULUNGU OONA basi,,,,,,,,,,,,memezani chonde chonde awawa akufunikira MULUNGU ndipo nduziwa kuti uthengawu akuva nawo kuwawa koma ana ake si ife,,,,,,,,,,,ife ndife ana a MULUNGU OONA ndipo awawa akugwa ndithu zomwe mwayankhula a Mbewe ndizofunika tamemezani tiwatengere ma fasting AMBUYE MULUNGU OONA ativera ndi zomwe MULUNGU amafuna zimenezo amenya ekha nkhondo koma ife tigwrane manja mmapemphero nzotheka(idalipo third term idalephereka ndi pemphero tiyeni)

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    BINGU mafuta amkavuta kwambri chakwera more fire ife pa central region fertilizer sitimkalandila

  • @NoelChipeta-q2h
    @NoelChipeta-q2h 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    More 🔥

  • @DaeyangSonon
    @DaeyangSonon 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuli dzuwa kunjaku ndipo simasewera, kaya mmabanjamu zikutha bwanji ndikukwera kwa zinthu uku😌

  • @PeterRabson-z3w
    @PeterRabson-z3w 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thank you

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Athu oweluza milandu akumalawi michilayao anatipweteka kwambili komaso chilima ause ndi thendele muthu oipa ose zamawo

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela watepelera dziko lathu lamalawi chifukwa anakana mulungu kuti iye anali nyamata wothamangathamanga kuchalichi osati busi ai