A Chakwera Mwalola Nyanja Ipite? - Bon Kalindo

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 3

  • @MustapherMulumbe
    @MustapherMulumbe 13 วันที่ผ่านมา

    Inu awa ndiiwopepela 😢😢😢😢

  • @JacogloryMwafulirwa
    @JacogloryMwafulirwa 10 วันที่ผ่านมา

    Uchitsilu was chakwera we have more backing point

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 13 วันที่ผ่านมา

    Nyanja yokhayo
    Akanatisiira chonde.
    Tizunzeni.
    Mutha kugwetsa kwacha osatiuza
    Njala itha kukhalako
    Titha kudya chitedze...
    Koma Na Nyanjayi Lake Malawi tisiire aaaaaaa...nanga tikagulitsa nyanja titsala ndi chani Apule...
    Talakwanji Amalawi yehova.
    Timvereni chisoni ana anu.
    Pamene tinalakwitsapo tikhululukireni.....tikumva kuwawa yehova
    Moyo ukuwawa kale uwu....ana akubwezedwa mma xul kamba ka fees kusowa...ma drop out a kuchuluka mma xul phala mulibemo..
    Mpaka tiyambe kusowanso chamber zoona chifukwa choti nyanja tilibe....izi zokha timvereni chisoni...kwasala tidzamva kuti ka Malawi kagulitsidwanso kwa azungu aaaa koma MCP.....??????????
    God Have Mercy on us
    God Have Mercy on Malawi..
    Tikuvutika ife....😭😭😭😭😭😭😭😭