Chonde musalore kukumana d Ndi munthu a Ntanyiwa ifetu aMalawi tikudalira inuyo you are our last hope. Ndipo ndimakupemphelerani daily kut mutipulumutse.osalodzedwa kulandila mphatso kapena kuonana ndi munthu
And this again can't be trusted could be saying this to look good and make him think he is good as well after getting in touch amupange chipongwe Maganizo anga
Ndikhupilira kuti wina aliyese wazimvera yekha. Madaliso anse apite kwa inu ndi mr mtanyiwa, born kalindo ndi wa bakili muluzi tv nonse akudaliseni zofuna za awo sizatheka mpaka atatuluka m boma
❤❤❤ May God blessed you bro man to another mother
Good advice
We love a ntanyiwa,Mr DC Born kalindo and bakili muluzi tv
Chonde musalore kukumana d
Ndi munthu a Ntanyiwa ifetu aMalawi tikudalira inuyo you are our last hope. Ndipo ndimakupemphelerani daily kut mutipulumutse.osalodzedwa kulandila mphatso kapena kuonana ndi munthu
Thx sir,,mukumvatu inu ma activisit God to keep yu all under HIS canopy
Mcp pano thawi yanu yatha sopano mulungu aliko mpaka mcp ichoke mulungu alipo mpaka crocodile achoke basi mulungu atimenyera khondo kuti zonse zimene akupanga mcp zisatheke
Tathokoza kwambiri pa malangizo anu bigup brother ❤❤
Uthenga wa bwino Bro Ambuye Akudalitse
Thanks for the message ur a star we will share to all the groups
Ameneo alipo mzimu amnthu ndi ophya.akanasowa.athu Akanazwa koma alipo ndithu myzna layesu
Keep it up the good work 💪💪
Mr inuyo ulemu wanu mulungu akudaliseni
Plz Ntanyiwa siyani kucheza ndi aliyese plz sitikufuna kuluza inu tikudalila pakampeniyi plz
Thanks very much brother for telling us
Zoona zake ndithu Bishop jemuse chowona anamutumiziranso paja wa army Ali mfridge
Atanyiwa please wakutsina khutu ndi mnasi
Achakwera your dys are numbered, 🤞
Ameneyo ndiye Mulungu wathu wamoyo apitilize kuwakantha anthu oipa amenewa
Good advice
Ine sindimaopa kumangidwa, ndipo unyolowo ndikuufuna bwanji simukundimangakoooo😂😂😂😂😂😂the DCcccccc . Kalindo ndikatunduuuuu
Ulemu wanu brother
Malawi wanga😂😂😂
Uyuuu ndiwachi lomwe🤟🤟🤟
❤❤❤❤❤❤
Mwayankhura momveka bwino kwambiri
Mudzenje lawolo agweramo wokhaaa vivaa
And this again can't be trusted could be saying this to look good and make him think he is good as well after getting in touch amupange chipongwe
Maganizo anga
God please protect Comrade Ntanyiwa ndipo mugonjetse oipa onse amen akufuna Moyo wake .Amen❤❤❤
Uthenga wavaka bro one luv
Zikomo kwambili chifukwa cha chikondi chanu Mulungu azikudalitsa
May our good lord protect all the activist
Uthenga ofunika kwambiri 🫲🫲🫲🦾🦾
Uncle plis,take care,uncle kalindo the DC,musakodwe mu nsamphamu choonde,we love you
Ngati pali ena omwe angakwanitse uthengau kuwupititsa Kuma Whatsapp group
Zikomo pamalangizo abwino
Chitsiru chamunthu iwe bodza lenileni
Well speak brother
Amene ali ndi phone yawo ua antanyiwa plz awuzeni
Its loud and clear
Good Advice
Antanyiwa chonde timadalira inu kutisekula maso uthengawu ugwilisen ntchito
Sindimaoka kalikose makape awawa pat
Truthfull wordz
Moti mumalandira ndalama eeet? Ndekuti mumatumidwa kuti muzingoyankhula zopanda nzeruzi?
Palibeso kukatenga mphatso kwa munthu wina aliyense wa Boma samalani nonse
Zikomo for the warning 🙏
God bless you sir
Keep it up brother Love each other
Auponda omwe anawapha aja akwana
Mulungu akudalize koma chakwela iweyo iweyo
Ineso ndine waku zomba nsilikali ameneyoyo timuchotsa zamkabudula
God bless
Ndende khadwe zilipafupi😢
😅😅😅😅😅😅 koma wanya komaso wasowatu ameneyo bwanji kod??
Ndipo zoona Ntanyiwa amakonda kupeleka number yake asiye zimenezo
Takunyadilani kwambiri brother pochenjedza
Samalanidi ma activity st athu ,we don't want to lose u ,no!!!!
Ndikhupilira kuti wina aliyese wazimvera yekha. Madaliso anse apite kwa inu ndi mr mtanyiwa, born kalindo ndi wa bakili muluzi tv nonse akudaliseni zofuna za awo sizatheka mpaka atatuluka m boma
Ntanyiwa saliyekha tili pambuyo pake
Nanga zipanga iwozi ndi chisankho chomwe chikukwera akumaganiza bwanji achipani chimenechi
Ndi zigawenga zoyipa kwambiri zi anthu zimenezi
My Allah protect mtanyiwa bm TV
Comrade ntanyiwa simunthu wamba, u can't get him. He refused 500ml already
Chakwera ndi nyelere zakezo zachepa ndipo sitikuopa auzane apwetekeka
Athe kumene kodi osamunokola uyoyo uyo wopha anzakeyo
Ndipo zosatheka ndipo sizizatheka.Chifukwa chake mulungu wazivumvurutsa kuchokera kwainuyo.mulungu amatikonda ndipo azapitilidza kutikonda ndi kutitetedza
Zofunika kumachenjezana
My bro otherwise no one will remain in this world better you find some ways to tell him
Anthu amenewa mulungu akuwasungiranji ndi moyo eeee
Mumakwana bigy takunyadilani potidziwitsa dza uthengawu cenjezo mwapeleka kale onse amene akufuna kupha ma activist asiyeni adziona chomwe chiwawonekelecho ndichomwecho sinanga ndizomwe akufuna.msilikali amenei sakudziwa munthu yemwe akusewela nae wangokhala msilikali koma akuchepa kwambiri tithana nae.
Kd galu chakwerayu amabwera kuzapha anthu kapena kuzalamulira dziko
Exactly
Noted just expose him.kumawachula maina anthu oyipawa kuti dziko liziwadziwa.Anga zolowele.
Zaboza basi adpp mwazolowela boza
abodza ndi amako
Tiyamike ambuye potimenyela khondo m, pakana titapambana mulungu si Lazaro
Zikomo kwambiri ndiuthenga wanu opambana ntanyawa wazungulilidwa nd anthu achitetezo.... wina apita mofulumila...
Uthenga wabwino zikomo ambuye akudaliseni bro tiyeni amalawi tipulumuse Malawi wanthu
Tathokoza mr man,ukhalise
Osaopa osatopa osafooka comrade
Abale timamukonda ntanyiwa zisatero ayi amfiti inu
Yesaya 29:15 zonse ziziululuka ndikukuuzani
Chakwela why why anapha chilima iwe lazaro mulungu akukathe
Thanks brother
chakwera watha mphamvu ndi nzeru
Mulungu akutetezelen antanyiwa plz plz
Ndipo nkhaniyo ndiyowona kwambiri akufunika kusamala kwambiri ntanyiwa samalani kwambiri nkhaniyi ndiyowona kwambiri
Ntanyiwa moto kuti buu
Inde inu anthuwa agwirizana zimenezo anthuwa
Ndipo akasipa atuluke atikwana agalu amenewa
Zikomo kwambiri tathokoza ntayuwa timamukonda Mlungu akudariseni
MCP INGOLANDIRA AWARD YAKUPHA ANTHU EEEEEH
Pokha zangoziwikapa Anya manyi
Zikangoululika chonchi basi filimu imathera pompo
Chakwela ndi president ochitisa manyazi kwambili akukhawulisa athu kwambili why why anapha chilima iwe lazaro mulungu akusende iwe panopa wayamba kulimbana ndiya sembe why kod mulibe manyazi. Mwawononga Malawi kugulisa mapiri. Nyanja. Mukusiya bwanj athu amene akudwala kuchipatala kuwasamala koma kupha basi iwe chakwela mbusa wonyenga iwe
Ok ndakumvan
Ma activists nose,musaope,awa tathana nawo kale,panopo sangamange munthu,sangapheso munthu aliyese, makona ose tatseka chitseko chapana,watsala mbuyawoyo soon akutsanzika
Koma izizi ndizoonadi uthengau ofunika uwafikile Antanyiwa, BMTV, Kalindo
Uthenga wabwino bwana
A NTANYIWA ASOWADI MASIKU AMENEWA KOMA ALIMOYO??
📦🙏🙏
zoonadi big
Zikomo
Nkhani yoona samalani amtanyiwa