ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Pamene pandiwaza, ndipamene chisi amati akanva njala mandota aziyimba phone. Kkkkkkk
Che mandota ndikilani ndikuyimbileni nyimbo You never disappoint us You make funny every time for us
Thanks ambuye......nyimbo ibwele basi
kanyimboko kalibwino nditu
Nice video
Mumaita mani mupitilise nefa Gifi apu che mandota kkkkk we proud of you bru
Sakunva akubawa awotchedwe bas mmene ngini zimavutila kupeza wina angobwera ndkuba mophweka aaaaa ine kumugwira watha ameneyo
Moto bazi
Mwabebesa inuyo on top mw MAndota team 😃😃😃😃😃😃
Kuotcha basi cos akapita ku police mawa abweranso komanso katundu wako sapezeka ngakhale atamugwira
Ilibho bas
Chabwino zootcha tamva koma kwamenya tizamenya komanso kuzikhala kodesa khawa mpaka asiye tchitodwewu
Tisamenye olo kuotcha munthu tizipita naye ku police akamulange a police
Mtumbuka wakumana nazoo 🤣🤣
😂😂
Wakuba akangwilidwa alandile chilango nthawi yomweyo chifukwa kumusiya ku police akatuluka ndiye kuti kuba sikuzatha
🤣 🤣 🤣 che mandota apatu nde zakoma chifuka zili kwa nzanu, dzana simunadye nkulipira chitsamba? 🤣🤣
😂😂😂😂
Sharia basi kumangodula manja osamuwotcha
These comedians never disappoint 🔥🥳
Achisi keep up his very classic 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼😏😏
Amaitha achisi
Musawontche itanani police ndi amene ali ndimphamvu
Mpunga
Masha Allah
Fire 🔥🔥🔥🔥🔥
Mukagwira mbava ikong'ontheni.... Mpwai ndi tsoka iweee... Yosefe Mkaza
Very nice video
Wamenya bho, kma akuba ena samava or apite ku police cz akangotuluka ndi revenge kudzakuberaso.Taziwonako ife
Chapansana😃😃😃😃
kalividiyoko kalibwino nditu ndinayamba kuseka ndisanakaonele
😂😂😂
One day tidzabwera kudzadya mphunga.nafeso tidzatawa kkkkk
Ndisakulosani
@@CHEMANDOTACOMEDY ndinakwima kale ine kkkkkkkkkk ngagunda mwaune yeleyo
Keep it up
Good advice
Mumatiimilila madolo.
Ofunika kumakawapereka ku police
Tizikawapekeka ku Police akuba tikawagwra
Mesa umati ulibe foni kkkk
😂 😂 😂 😂 😂 Sizabho wakuba kumuotcha, the best sulushulu ndikuvaya naye ku police 🚨 mumantha che mandaota tili pano coz of u
Maganizo abwino ambuye azipita ku police basi.....thanks sir
This is gud,,,keep it up 😍😍😍😍😍
More fire Che Mandota
Wakumana nazo mtumbuka kkkk Che mandota inuyo ndi 1
Sikomo
Let Righteous be done as Water Covers the Sea.... 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Hahahaha 🤣 mumakwana guys
Kupita naye ku police bas
My guy mandota ulemu wanu
Vuto ndi loti akuba akumagwira ntchito limodzi ndi apolisi, nde nchifukwa chake anthu amalanga okha ngakhale kuti kutero si zinthu zoyenera.situations can transit the law into unsafe hands sometimes.
Ziona ambuye panopa ndi zovuta kudziwa amene akuchita chilungamo.....mapeto ake amapeza okubawo atulutsidwa
Koma njila ya bho, ndiyaku police Cox nkhani ikafika mmalamulo. Zimavutaxo omenya, maka amene.
Mutumbukawe😂😂😂😂
Osamuotchanso, kungomuika ma live wire nkamwa kkkkkkk. Umakwana mandota.
Hahaha wapusa mtumbuka
Eeeeeee ndimwalamwala aka I love this
Tiziwaotcha kuti azipunguka okubawa chifukwa akapita ku police amakabweraso ndi mangolomera hiya 😆😆😆😆
Azichepa basi😂😂😂
Mumatiyimilira inu
Achisi ndi mbafa🤣🤣🤣
Mbambandee
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 umaitha bg mn
Azimenyedwa uku tikupita naye kupolice
This is gud ......keep it up
Thanks
Inu malume supano
Mpunga 🔥🔥🔥
Kuli malusi
😂😂😂😂😂 che mandota plz ngati mungakwanise subtitle nanga sii ife tonkha timaonera ma video anu
That's it owez on fire 🔥 #Educative
Panado ur crazy 🤪
More 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 Mandota
Moto basi sakunva akubawa
Aziyaka 😂
Timakunyadila my brother
@@CHEMANDOTACOMEDY koma fasting ikuyenda bwanji brother
Tipite nao ku police
Chifukwa chani boss?!
Kumawaocha basi
Mpunga💥💥
More 🔥🔥🔥🔥🔥
Koma chipongwe osapilila ndalama kkkkkkkkkk kkkkkkkkk
ABWANA mumatha kuphika mpunga (masewero)😂 - akuba onse Ku Police.
Osati kuotcha?!
@@CHEMANDOTACOMEDY ayinso man. Mwinatu atabweza katunduyo koma ngati sanabweze akamve mb'emb'e Ku NDENDE
akuotche ndi petro kumwambanso ukapse eeee nyekhwe 😂
🔥🔥🔥 2 dabulo
Kkkkkkk koma
🔥🔥🔥🔥🔥
so the guy, afoto luteh, has been eating like for 30 minutes now 😂😂 amadyadi mpunga ameneyo?
Mpunga 😂📌
Boss mandota mumatha inuyo
Am the first to watch
Bulasa lero akudyeratu kkkk
😂😂😂😂 bg up guys 🙌🙌🙌
Koma mumatha 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Tatokosa
Keep it up!
💛 ulem wanu malume
💞💖💜🔥💦
Tizaotcha kkkk
che mandota keep it up
🔥🔥🔥❤️
🔥🔥🔥
Chuluchuni ya bwino ndi kungomufula chati nkupita naye ku polisi tu
Ozati kumufula talausa?!
ayi kumufula talausa ndi halam,chuluchuni yolakwika koma chati wawo 🤣
Pamene pandiwaza, ndipamene chisi amati akanva njala mandota aziyimba phone. Kkkkkkk
Che mandota ndikilani ndikuyimbileni nyimbo
You never disappoint us
You make funny every time for us
Thanks ambuye......nyimbo ibwele basi
kanyimboko kalibwino nditu
Nice video
Mumaita mani mupitilise nefa Gifi apu che mandota kkkkk we proud of you bru
Sakunva akubawa awotchedwe bas mmene ngini zimavutila kupeza wina angobwera ndkuba mophweka aaaaa ine kumugwira watha ameneyo
Moto bazi
Mwabebesa inuyo on top mw MAndota team 😃😃😃😃😃😃
Kuotcha basi cos akapita ku police mawa abweranso komanso katundu wako sapezeka ngakhale atamugwira
Ilibho bas
Chabwino zootcha tamva koma kwamenya tizamenya komanso kuzikhala kodesa khawa mpaka asiye tchitodwewu
Tisamenye olo kuotcha munthu tizipita naye ku police akamulange a police
Mtumbuka wakumana nazoo 🤣🤣
😂😂
Wakuba akangwilidwa alandile chilango nthawi yomweyo chifukwa kumusiya ku police akatuluka ndiye kuti kuba sikuzatha
🤣 🤣 🤣 che mandota apatu nde zakoma chifuka zili kwa nzanu, dzana simunadye nkulipira chitsamba? 🤣🤣
😂😂😂😂
Sharia basi kumangodula manja osamuwotcha
These comedians never disappoint 🔥🥳
Achisi keep up his very classic 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼😏😏
Amaitha achisi
Musawontche itanani police ndi amene ali ndimphamvu
Mpunga
Masha Allah
Fire 🔥🔥🔥🔥🔥
Mukagwira mbava ikong'ontheni.... Mpwai ndi tsoka iweee... Yosefe Mkaza
Very nice video
Wamenya bho, kma akuba ena samava or apite ku police cz akangotuluka ndi revenge kudzakuberaso.
Taziwonako ife
Chapansana😃😃😃😃
kalividiyoko kalibwino nditu ndinayamba kuseka ndisanakaonele
😂😂😂
One day tidzabwera kudzadya mphunga.nafeso tidzatawa kkkkk
Ndisakulosani
@@CHEMANDOTACOMEDY ndinakwima kale ine kkkkkkkkkk ngagunda mwaune yeleyo
Keep it up
Good advice
Mumatiimilila madolo.
Ofunika kumakawapereka ku police
Tizikawapekeka ku Police akuba tikawagwra
Mesa umati ulibe foni kkkk
😂 😂 😂 😂 😂 Sizabho wakuba kumuotcha, the best sulushulu ndikuvaya naye ku police 🚨 mumantha che mandaota tili pano coz of u
Maganizo abwino ambuye azipita ku police basi.....thanks sir
This is gud,,,keep it up 😍😍😍😍😍
More fire Che Mandota
Wakumana nazo mtumbuka kkkk Che mandota inuyo ndi 1
Sikomo
Let Righteous be done as Water Covers the Sea....
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Hahahaha 🤣 mumakwana guys
Kupita naye ku police bas
My guy mandota ulemu wanu
Vuto ndi loti akuba akumagwira ntchito limodzi ndi apolisi, nde nchifukwa chake anthu amalanga okha ngakhale kuti kutero si zinthu zoyenera.situations can transit the law into unsafe hands sometimes.
Ziona ambuye panopa ndi zovuta kudziwa amene akuchita chilungamo.....mapeto ake amapeza okubawo atulutsidwa
Koma njila ya bho, ndiyaku police Cox nkhani ikafika mmalamulo. Zimavutaxo omenya, maka amene.
Mutumbukawe😂😂😂😂
Osamuotchanso, kungomuika ma live wire nkamwa kkkkkkk. Umakwana mandota.
Hahaha wapusa mtumbuka
Eeeeeee ndimwalamwala aka I love this
Tiziwaotcha kuti azipunguka okubawa chifukwa akapita ku police amakabweraso ndi mangolomera hiya 😆😆😆😆
Azichepa basi😂😂😂
Mumatiyimilira inu
Achisi ndi mbafa🤣🤣🤣
Mbambandee
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 umaitha bg mn
Azimenyedwa uku tikupita naye kupolice
😂😂😂😂
This is gud ......keep it up
Thanks
Inu malume supano
Mpunga 🔥🔥🔥
Kuli malusi
😂😂😂😂😂 che mandota plz ngati mungakwanise subtitle nanga sii ife tonkha timaonera ma video anu
That's it owez on fire 🔥 #Educative
Panado ur crazy 🤪
More 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 Mandota
Moto basi sakunva akubawa
Aziyaka 😂
Timakunyadila my brother
Sikomo
@@CHEMANDOTACOMEDY koma fasting ikuyenda bwanji brother
Tipite nao ku police
Chifukwa chani boss?!
Kumawaocha basi
Mpunga💥💥
More 🔥🔥🔥🔥🔥
Koma chipongwe osapilila ndalama kkkkkkkkkk kkkkkkkkk
ABWANA mumatha kuphika mpunga (masewero)😂
- akuba onse Ku Police.
Osati kuotcha?!
@@CHEMANDOTACOMEDY
ayinso man. Mwinatu atabweza katunduyo koma ngati sanabweze akamve mb'emb'e Ku NDENDE