LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA.23 JUNE 2024 SUNDAY

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 30 ก.ย. 2024
  • Dzuka Malawi

ความคิดเห็น • 353

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 หลายเดือนก่อน +22

    Mulungu wathu wa kumwamba timakudalirani muzonse tichitireni chifundo pa zomwe zikuchitika mu dziko la Malawi chonde. Pulumutsani abon kalindo ndi a kamulepo kaluwa komwe aliko Mulungu wathu chonde usalore kuti satana aambane tithandizeni kumenya nkhonoyi pathoka sitingate

  • @SamuelJohn-pc3ls
    @SamuelJohn-pc3ls 3 หลายเดือนก่อน +37

    A Malawi tiyeni tichitepo kanthu, apapa ndi nthawi ya zionetsero.......
    Let's protect our human rights
    Let's stand with our fighters.....

    • @EvanceSungani-cv9jk
      @EvanceSungani-cv9jk 3 หลายเดือนก่อน +4

      Exactly ndpo a opposition komaso a Malawi first amaenera kukhala pa top kutisogolera Ife athu wamba,,,,komano to be honest izizi 🇲🇼 zikundnyasa kowopsa,,,,,😢😢😢amene mulindkuthekera kukumana ND akulu akulu talumikizanani nao tisinthe znthu guys this is too much

    • @CassimMbalaka
      @CassimMbalaka 3 หลายเดือนก่อน +2

      Tidikire Monde ngati satuluka tipanga ximenezo

    • @triphoniasimbota116
      @triphoniasimbota116 3 หลายเดือนก่อน

      @@CassimMbalaka kumutulusa za mtendere sizingaatheke . Unless atamupanga something ....bcz anthuwa akuyesesa

  • @Stargahmelody-oi8bf
    @Stargahmelody-oi8bf 3 หลายเดือนก่อน +17

    Akulu akulu chonde ndikukupemphan chonde mudzina lamulungu chonde tatiyeni tigwilane manja tipange zoti Born kalindo atulutsidwe chonde nd munthu yekhayo yemwe akutionetsela zisinsi za momwe Boma likupangila nkhanza Amalawi

    • @GiftPhiri-tt7nn
      @GiftPhiri-tt7nn 3 หลายเดือนก่อน +2

      Exactly

    • @PaulDaka-dc3re
      @PaulDaka-dc3re 3 หลายเดือนก่อน

      And tisachedwepo akhonza kupanga ma plan awo achabe

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 3 หลายเดือนก่อน +18

    May the Almighty God be with Mr kalindo and all Malawians

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน +20

    Amalawi titeni tiyeni konko and tikaphwanye police pokhapokha atamututsa Bon Kalindo pls

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 หลายเดือนก่อน +18

    Lipopo FM number one ❤

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 3 หลายเดือนก่อน +32

    Chakwela waonjeza kodi munthu ameneyi bwanji akupanga mkhaza zimenezi very shame to u chakwela mulungu akulange munthu oipa iwe

  • @gilbertdamba7344
    @gilbertdamba7344 3 หลายเดือนก่อน +4

    Bon kalindo ndimunthu wabwino kuyambila momwe anali mphunzisi wanga pa nkolokoti primary School, I stand with him.

  • @ajudyaustine984
    @ajudyaustine984 3 หลายเดือนก่อน +14

    Komatu chakwera waposa satana amalawi tiyeni tisiye kumutenga president ngati mulungu ndipo azidziwa kuti no one is above the law nayenso wakhara miyezi yochepa bcz what goes round comes around dziko. Lamalawi chakwera silake ayiGod help us

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน +15

    Amalawi why tikungoyang'ana Bon Kalindo ndi Mr Kaluwa Kuti azidzudzika chonchi kudzudzikira ifeyo????😢😢😢😢😢 Kodi tikufuna tizizalira anthuwa ataphedwa ndi MCP?????😢😢 Why tisakupanga kanthu tikungoyang'ana?????😢😢😢😢😢😢

    • @chifunilojalasi2337
      @chifunilojalasi2337 3 หลายเดือนก่อน +2

      Tikuchitiranji mantha chonchi abale

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน +2

      @@chifunilojalasi2337 Ndipo big aaaaa chonsecho dziko lathu aaa

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 3 หลายเดือนก่อน

      Mukufuna dzikoli likhale losatsatira malamulo kod kut aliyense azingochita zomwe akufuna? Ndie likhalaso dziko lotetezeka? Ngat wapanga zosemphana ndi malamulo adziko Basi aziona, ifeso tazunzikaso titalakwira malamulo adziko amphwanga mwanva!!

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน

      @@isaacchiwaula731 Ukuyenera upite kusukulu adha, ukaphunzira Topic ya Human Rights, yomwe Muli freedom of expression. Tsegu maso pls inoyo sinthawi ya asamunda

    • @GremNyirenda-ej7wd
      @GremNyirenda-ej7wd 3 หลายเดือนก่อน

      Ambuye inu ndinu mulungu wamoyo woziwa kuyang'ana pena paripose mumenyereni nkhondo bon karinde kuti satana m' dyerekezi amugwire manyazi

  • @LucyLaisani
    @LucyLaisani 3 หลายเดือนก่อน +13

    Dziko lanthu lomwe kusowa nalo mtendere my Allah protect you bon kalindo 😢😢😢

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน

      Zovuta zedi Lu mmmmmm😢😢😢😢😢😢😢😢

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 3 หลายเดือนก่อน

      Aaa hahaha😅😅😅

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 3 หลายเดือนก่อน +7

    Ambuye Mulungu wanga kumwambako titakheni Ife tetedzerani Bon Kalindo kumene Ali tikulira pa maso panu mokupemphani Yehova nchitoreni chifundo

  • @ReginaHappy-kx9fl
    @ReginaHappy-kx9fl 3 หลายเดือนก่อน +7

    Mbuye timenyereni nkhondo chonde abale athu kumalawi akuxuzika dziko lokhala lawo,ndipemphero ndipembezero Kuti atuluke amoyo ambuye imvani kulila kwathu ananu Ife talema Ife ,km chomwe angaziwe ndichi muyezo omwe umamuyeza nzako naweso uzayezedwa omwe mulungu sangatisiye tokha

    • @JohnJohn-og8rt
      @JohnJohn-og8rt 3 หลายเดือนก่อน +1

      Sorry about Malawi kwa vuta kwambili kom akulukulu anane chomwe wakulu wayangu wolopatalichebe zimachitika cong les ndiyachabe chabe siizi ukuwona uvulu uli pati wa athu

  • @EvanceJimmy-e6c
    @EvanceJimmy-e6c 3 หลายเดือนก่อน +6

    Just loving what happened in Niger 🇳🇪 and Burkina Faso 🇧🇫. Army yachabe imene ija. Don't tolerate nonsense from President

  • @FunnyDimSum-hk1so
    @FunnyDimSum-hk1so 3 หลายเดือนก่อน +8

    Chakwera mulungu akukhululukire ukudzuza mizimu kom chmwe muziwe achakwera zanu zida mulibeso chaka

  • @CatherineKumwex
    @CatherineKumwex 3 หลายเดือนก่อน +10

    God protect Malawi

  • @PatrickLikole
    @PatrickLikole 3 หลายเดือนก่อน +8

    Limpopo ntchito mukugwira yotamandika

  • @KimDexonAdamson
    @KimDexonAdamson 3 หลายเดือนก่อน +5

    Where are you mr Namiwa?
    Can't you guide us?

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 3 หลายเดือนก่อน +4

    Daniele 6:16 sadileki ndi miseki ndi abitinego anaturuka mudede yagajo Yamato winiko atulukawamoyo

  • @EliasOdala
    @EliasOdala 3 หลายเดือนก่อน +5

    mcp yatha coz nkhaza akupangazi akudziwa kuti anthu awatuluka

    • @MarkMasangwa
      @MarkMasangwa 3 หลายเดือนก่อน

      Kkkkk zavuta

  • @ShadrechSapaluwa
    @ShadrechSapaluwa 3 หลายเดือนก่อน +7

    Palibe chobisika pamaso pa Mulungu. All the hidden treasures must out in Jesus Mighty Name🙏🙏

  • @CeciliaNkhoma-nz7uj
    @CeciliaNkhoma-nz7uj 3 หลายเดือนก่อน +5

    Kod chakwera ameneyo anabadwa ndi munthu kapena galu akanabadwa ku muntu bwenzi siku lina tikananva mawu amai ake akumuresa zomwe akuchitazi but one day is one day.

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere 3 หลายเดือนก่อน +7

    So if akumukaniza to go to toilet ndiye even food angamupatse may good Lord have mercy upon Kalindo's life 😢

  • @cephasSainet
    @cephasSainet 3 หลายเดือนก่อน +5

    Keep on rebuking them please

  • @CedrickBrighton
    @CedrickBrighton 3 หลายเดือนก่อน +6

    Your number one and only to be trusted

  • @MaryMakina-nh2eo
    @MaryMakina-nh2eo 3 หลายเดือนก่อน +1

    Guys apa ndiye wafikapo bwanji ameneyu Eeee chakwela umeneu ndiufiti.

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 3 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwera ndiye gwenembeyo coz anapha Vice wake chifukwa cha dyera

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 หลายเดือนก่อน +4

    Ambuye chitanipo kathu a Malawi tiyeni titengepo gawo kupempheraela akalindo ndi aka mlepo kalua

  • @GetrudMagwira
    @GetrudMagwira 3 หลายเดือนก่อน +3

    May the lord protect mr Bon kalindo in Jesus name

  • @blessingsbandah-pu3kw
    @blessingsbandah-pu3kw 3 หลายเดือนก่อน +5

    Mr mnthanyiwa tikukutsan ntchito mukuigwir kwmbr proud of u

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 หลายเดือนก่อน +4

    Kodi chakwela akuganiza bwanji ndizopatsa manyazi zomwe akuchita,koma amalawi tithadi ndikuphedwa komaaaaa???? Musamale kunja kuno kuli mulungu.

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos 3 หลายเดือนก่อน +3

    Nanga manganya Alibe udindo wowombola nzake winiko?

  • @AsifChacha-f3o
    @AsifChacha-f3o 3 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwale akuzitenga ngati wamuyaya ayi ndithu

  • @GeeGuu-zy4oi
    @GeeGuu-zy4oi 3 หลายเดือนก่อน +5

    Big up bravo

  • @KennethChagunda-gn8kg
    @KennethChagunda-gn8kg 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ndiyekuti iweyo ukunamaka cz sizimatheka munthu kumuletsa kuwonedwa komanso kupita ku chimbudzi.

  • @neemahkapatamoyo9563
    @neemahkapatamoyo9563 3 หลายเดือนก่อน +2

    Komatu Antanyiwa mukuyesetsa kwambiri mbari yanu komano vuto A Malawi ife sitimatha kugwilana manja komaso anthu omwe mukuti ndinu azipani bwanji mwangokhala chete osatuluka mesa munthu uyu amakulankhulilani? Tadzukani plz gwilanani manja pangani zothekera zowona zinthu izi zizichitika inu mukuona? Tadzukani apa tamuuzeni chakwelayo kut tili kunyengo ya Democracy timalankhula zakukhosi kwathu

  • @OweniMalokooweni
    @OweniMalokooweni 3 หลายเดือนก่อน +2

    Please koma akoro apolice anakunzani please musayese kuwachura ndipo munziwawunza popa kuti sindizakulurani ndipo munzindi unza zambili ena ofuna kukzani zambili alipo koma amawopa

  • @KINGSLEYDINIWA
    @KINGSLEYDINIWA 3 หลายเดือนก่อน +3

    Pepani bwana chonde tiuzeni choonadi zokhudza Magalimoto asilikali achilendo amene alowa dziko Muno more than 20 adusa pa Luzu Ku Blantyre atanyamula ma contena akudzatani plz #NTANYIWA tiuezeni...????

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 3 หลายเดือนก่อน +4

    Komatu anyamata amenewo asamale asangoti tili mwamba ndiye aziona ngati pansi palibe mame aziona akazasikamo mwambamo mpomwe azazione ndithu!!!!

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 3 หลายเดือนก่อน +3

    Falawo wawumisa mitima muziko la Malawi koma tisataye mutima Mulungu ali kumwamba akuona zose ikwana nthawi yoti falawo alangidwe
    Bon kalindo atetezedwa ndi Mulungu.

  • @FlossyAtupeleNyasulu
    @FlossyAtupeleNyasulu 3 หลายเดือนก่อน +4

    Zosakhala bwino... hmmmm

  • @innocentchirombo2073
    @innocentchirombo2073 3 หลายเดือนก่อน +2

    For the next generation yet unborn , whenever you come across this comment, just know that we were once alive this day to witness this masterpiece... Mtanyiwa the great man

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos 3 หลายเดือนก่อน +3

    Saíd m,bawa pa mkongo wamako, limozi ndi MCP yakoyo, munthu wankhaza ukumusekelera chakwela nonse ndi chakwela wako nyini za amayi anu

  • @juliusnjerengo2610
    @juliusnjerengo2610 3 หลายเดือนก่อน +1

    We worn you guys before 2019 election that this Chakwera guy you are about to vote him into power he will make you cry.
    Amalawi kusamva ndi umbuli komaso kususuka.

    • @MaryAaron-nn8ec
      @MaryAaron-nn8ec 3 หลายเดือนก่อน

      Even our parents warn us about the MCP leadership anthu kusanva now ndi izi we are no longer safe at all

  • @MusaWilliam-t8n
    @MusaWilliam-t8n 3 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwela akatula udindo choyambilila asazakhale kumalawiko chifukwa choti azayasidwa moto zuwa likuswa ntengo azaphedwa

  • @AlfredMandanda
    @AlfredMandanda 3 หลายเดือนก่อน +5

    Zosayenda

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet 3 หลายเดือนก่อน +3

    Zikufunika kupita kunja ndikuyamba mandemo paka watuluke bon kalindo walakwachani

  • @STARLIGHTGSM-cd8uv
    @STARLIGHTGSM-cd8uv 3 หลายเดือนก่อน +4

    Mavuto abale afuna apange chani

  • @NastonVickta
    @NastonVickta 3 หลายเดือนก่อน +1

    Office in charge yo anapanga rate munda wanga wa mizimbe, week ya mawa ndioti akubwera, so long time vampire tikamuthimisila komweko, ngati akufuna moyo andisiyila mzimbe.

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ambuye alowelerepo anatulusa Petro mundende tulusani boni kalindo

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mudziko.lapansi kuli athu ankhaza koma uyu ndie Ali special without any shame oooooo my God do something

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od 3 หลายเดือนก่อน +3

    Allah alipaliyatu amuteteza 😢😢😢😢

  • @hassansamsey1210
    @hassansamsey1210 3 หลายเดือนก่อน +3

    Allah will protect him

  • @OscarWesly-tn6kh
    @OscarWesly-tn6kh 3 หลายเดือนก่อน

    Malawi army overthrow chakwera government now if you really love your country.. .....coz your duty is to protect the country and its citizen......dont allow chakwera to bribe you see how many people are suffering.......where is your power MDF

  • @ContentCorgi-kx3tb
    @ContentCorgi-kx3tb 3 หลายเดือนก่อน

    Thanyiwa tumizilen number yanu please ndimakukondan kwambili❤❤❤❤❤❤

  • @innocenttasiziyo-rj3wr
    @innocenttasiziyo-rj3wr 3 หลายเดือนก่อน +3

    Come on Limpopo 💪💪💪

  • @emmanuelmukondia3568
    @emmanuelmukondia3568 8 วันที่ผ่านมา

    ZITSIRU CHIFUKWA CHA KUPUTSA KWANU LHOMWE. YOU THOUGHT THIS COUNTRY BELONGS TO YOU

  • @AhamdJafali
    @AhamdJafali 3 หลายเดือนก่อน +2

    Kodi kalindo akafuna kudzithandidzila adzichita kumuyimbila chakwela ndiye iyeyo chakwelayo amamuudza ndani

  • @OweniMalokooweni
    @OweniMalokooweni 3 หลายเดือนก่อน +2

    Sorry ana amu khonje tinachedwa ku timavanukukoma bother

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mumakwana pakanakuziwa kwamaveya koma ife tilipokupepela kuti akalido atetezeke dipoatulukako muzinalayesu masalimo 119:126

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 3 หลายเดือนก่อน +1

    Tiyeni tituluke abale anthu awa atikwana bwanji zoona munthu akuzizika ife tili pheee zoona Malawi tisala ndi anthu olimba tima ngati kalindo mulungu musalole choyipa chilichonse chimupeze bon kalindo

  • @AlbertoNgoma-kb9mb
    @AlbertoNgoma-kb9mb 3 หลายเดือนก่อน +1

    😮God will reveal everything done secretly

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 หลายเดือนก่อน +1

    Anthu akunkhotakota chonde onesani kukhuzidwa kwanu nanu pazimene boma lachakwelayu likuchita tisalole kuti bomali litizunze ife amalawi

  • @AgathaKaliwo
    @AgathaKaliwo 3 หลายเดือนก่อน

    May God protect Bon Kalindo wherever he z....

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera chilipo chikumusata MULUNGU si munthu khalani chete Let's pray for him.

  • @rashedzain6507
    @rashedzain6507 3 หลายเดือนก่อน

    Network ya NRB kulilongwe kokha
    Network ya ku immigration ku Lilongwe kokha
    Ayi zikomo ndithu tionana 2025

  • @wilsonali7890
    @wilsonali7890 3 หลายเดือนก่อน

    Why Malawians are not doing as the Kenyans are doing..... This is not good guys

  • @IbrahimPhiri-ky5jk
    @IbrahimPhiri-ky5jk 3 หลายเดือนก่อน +2

    Apapa ndiye zanyanya koma MOTi koma tiziti ikuchitika apayi ndi democrats olo bwanji kapena Mr chakwela asandukano mulungu mwina

    • @NastonVickta
      @NastonVickta 3 หลายเดือนก่อน

      Apa boma latengedwa ngati banja, osati democrany

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 หลายเดือนก่อน

    Yomweyooo Galu iweee, Yudasi Chakwera woyeeeee,wakuphayoooo thawani, thawani,uyooo Goliath,uyooo🎉🎉🎉

  • @EnthusiasticMountain-xd7vn
    @EnthusiasticMountain-xd7vn 3 หลายเดือนก่อน

    Ambuye mulungu kumwambako tioneni ife 😭😭😭mr chilima,mukadadziwa abale simukanakopa amalawife kulowesaso congress mb'oma 🥲

  • @blessingsbandah-pu3kw
    @blessingsbandah-pu3kw 3 หลายเดือนก่อน +1

    Plz alindi nyimbo yomwe ikuveka pasipai kumapeto kolankhura mr mthanyiwa anaimba ndna yandisangalatsa kwmbr

    • @PhillipAcquaron
      @PhillipAcquaron 3 หลายเดือนก่อน

      Anayimba nd a Mec uyiva 2025 osadanda

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 3 หลายเดือนก่อน

    May almighty Allah protect Bon kalindo 🤲

  • @charlesbanda7594
    @charlesbanda7594 3 หลายเดือนก่อน

    Tiyeni tipange ziwonetsero tisamangomvetsela Limpopo tiyeni tizuke Malawi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 หลายเดือนก่อน

    Amalawi, tiyeni tisawasekelele ang'aziwa, tiwachose b4 2025, palibenso reason yoti tifikile 2025 apaa, time to change is now!, achoke wagule ameneyu , mxiem

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 หลายเดือนก่อน

    MULUNGU ndi wa chifundo chosatha amuteteze Bon Kalindo.

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 หลายเดือนก่อน

    Iiiiii koma a MCP kupha kalindo utsayembekedzela zabwino dzikoli mulimva kuwawa chiwanda chakupha chili ndi MCP ukuko kumapeto nsono mwadzi wa chilima wakupengetsani mudzaliwona dziko kuwawa MULUNGU SIMUNTHU AKUWONA ZONSEDZI

  • @georgemponda
    @georgemponda 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera afa infa yopwetekeka mumuwuze kuti amalawi enafe sitikugona naye tulo... tell him to begin counting down his days of living. SITILOLA KUTI AWONONGE MALAWI WATHU OKONGOLA Just coz of his greedy and negligence.
    Kulibwino kadziko kamalawika tingogawanapo basi.

  • @ZakariasintidomathengaMathenga
    @ZakariasintidomathengaMathenga 3 หลายเดือนก่อน

    Zimene akupanga apulezidenti zikunyatsa zedi chifukwa palibe chimwene analakwa Koma azafa Ngati galu

  • @WysonAdamu
    @WysonAdamu 3 หลายเดือนก่อน

    asiyeni adzipanga dzimene akupangazo siku lachiweruzo lizabwela olo pachedwa

  • @RhodrickChauluka
    @RhodrickChauluka 3 หลายเดือนก่อน

    Ayi zikomo kwambiri chakwera koma chomwe ungaziwe kaya sindikumiziwa koma chomwe mungaziwe Bon kalindo kungofa ndikuti Bon kalindo kungofa tiziona

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi a tsogoleri osutsa boma bwanji ochitapo kanthu mophatikizana ndi a Human rights. Malawi is finished.

  • @MolosonMisitala
    @MolosonMisitala 3 หลายเดือนก่อน

    Pamenepatu pakufunika kukatchola policeyo komko ngat muja amkachitila iwo nthawi yamademo kwamsunde

  • @SimonMochede
    @SimonMochede 3 หลายเดือนก่อน

    But why chakwera? Kodi galu ameneyu akufuna chani Ku dziko la malawi?
    Kodi wapha aja sanakukwanire ?
    Usatilakwitss Ife , realise kalindo

  • @Imraanjafali
    @Imraanjafali 3 หลายเดือนก่อน

    Bola kukaocha moto police ya kumenekoyo ndalama anagwiritsa ntchito pomanga police sindalama ya chakwera

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 3 หลายเดือนก่อน

    Kmatu kungopha kalindo kuvuta coz zachilima sitidaiwale

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel 3 หลายเดือนก่อน

    Kutukwanidwa kwa chakwera sinkhaza kutengeka pachinthu chakut sukuchidziwa ndibwino kusachitsatira okay

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 3 หลายเดือนก่อน

    MCP AKUFUNA ASINTHE MALAMULO AZIKO AKUFUNA AWONGWEZELE ZAKA ZA PULEZ ASANAVONTENSO PHEKESELAZIKUNVEKA

  • @MadalitsoIbrahim
    @MadalitsoIbrahim 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwela sinthakoni nkhanza zanu chonde simoyo mukupangawo

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili1362 3 หลายเดือนก่อน

    Komatu ku bomaku uzanani chilungamo zinthu zalakwika kale and u continue kuwonongelawonongela why? And why mistreating Mr kalindo like that Ili ndiziko ndipo limazungulila musayiwale zimenezo. Remember that there's tomorrow

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 หลายเดือนก่อน

    Amabungwe owona za ufulu waanthu alikuti?, azibusa amipingo yosiyanasiyana alikuti

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od 3 หลายเดือนก่อน

    Kmatu tikadikila kut zifike povuta bwanji ndigoyambisa mademo

  • @christopherbanda4698
    @christopherbanda4698 3 หลายเดือนก่อน

    Dzikomo kwambiri munthu wa mulungu pitilizani ntchito yotamandika

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 หลายเดือนก่อน

    Bola lasatanikili la chakwela ng'ona ng'azi gule likufuna kuyambisa nkhondo mdziko muno ndizomwe akufuna asatana amenewa 😡👺👹👿😈👹👺

  • @AminahMussah
    @AminahMussah 3 หลายเดือนก่อน

    mpando ndiwosiilana umenewo usaiwale kt mwatsala ndi miyezi yochepa chabe

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 3 หลายเดือนก่อน

    Kalindo anachipeza chomwe ankachifuna paja anali patsogolo kufuna kongelesi lero ndi izi

  • @youngsmpevangelistchirambo4346
    @youngsmpevangelistchirambo4346 3 หลายเดือนก่อน +3

    Keep fire 🔥 Limpopo tilipompo nafeso

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 3 หลายเดือนก่อน

    Yehova tenganiponi mbali populumusa moyo was akalindo

  • @Happ2y
    @Happ2y 3 หลายเดือนก่อน

    Ine ndi kuti chakwera kupanga zosedzi chifukwa akuopa kuluza MA vote ndipo akudziwa kt adzafera kundende ndipo adzafera kundende ndithu

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 3 หลายเดือนก่อน

    Ndipo amene ataziwine 2025 azamuwonese mbonawona ameneyu mukuti president yu azawone zimene akuwawonesa amzakezi God is there watching as long as he didn't create himself

  • @LamequeSamuel-v6y
    @LamequeSamuel-v6y 3 หลายเดือนก่อน

    Taswela bwanji amalawi, pepani pepani masiku akudusa ndithu, Kodi ndi m'mene zikunvekelamu tikufuna tizazaze ku maliro malo mokasokha ku polici kiti atimasulire athuwa?