MOMWE ANTHU AYANKHILA MFUNDO YA A CHAKWERA_19 December 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 19 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 46

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Kunena chilungamo Chakwera ndimunthu woyipitsitsa kwambiri bola akanangokhala chete osalankhulanso chitsilu cheni cheni

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Kkkkkk koma chakwera 😢😢😢😢kumvetsa chisoni kwake ai zikomo

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Munthu ukamalandira chakudya cha ulele siuziwa Kuti anthu akuvutika ndiye achakwera pano ali bwino zedi zoti anthu akuvutika sangaziwone olo

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Chitsilu cha tsogoreli chakwela mbuzi ya munthu alibe chisoni kwambiri....😢😢😢😢

  • @TherryApasta
    @TherryApasta 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Achewa akwiya chakwera ali m'madzi, chimwendo wamputsitsa wadyapo dziro kkkkkkkkk 😂

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    President womvetsa chitsoni pa dziko lampasi chakwela

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 21 นาทีที่ผ่านมา

    Mizimu ya Soulos yikukana sanati chakwera

  • @ChikuCharlie-r9u
    @ChikuCharlie-r9u 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ine ndikuwona ngati Chakwera akudwala matenda amubongo

  • @KhaifaMdala
    @KhaifaMdala 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    😂😂😂😂 Km chakwela

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    😭😭😭 ndilibe mau ndithu Bola alemera

  • @WilsonMbendela
    @WilsonMbendela 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mtolankhani iwe ndie uti

  • @ThomWatsopanoMW
    @ThomWatsopanoMW 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwera mulungu akukhululukire

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwera achoke basi 😂😂😂 sikuyakha kwabwino

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Next kumakhala program on radios yoti kulondoloza za imfa ya saulos chilima and ena 8,

  • @SimionDmtande-z8v
    @SimionDmtande-z8v 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nanga kwa amene salima amangwila ntchito ndipo amalandila 100,000 apanga bwanji galu wa munthu chakwera wanva

  • @LovelyCookingApron-ok9ql
    @LovelyCookingApron-ok9ql 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Please mr. President, pangani zotheka kuti feteleza atsike kotelo nacho chimanga chitsika ntengo chifukwa kuno kumudzi ,timadalila ulimi

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera mmm ndimangova kupanda zelu koman ,uyu ayi ndituu

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chilungamotu chomwe akunena

  • @chisomokotamu7563
    @chisomokotamu7563 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ntolankhani wamantha ngati uyu sinamuone guys

  • @DavisSeyani
    @DavisSeyani 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuyipa mtima kwa president

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera wayamba kupenga misala

  • @TakalaniGlenda
    @TakalaniGlenda 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koditu apa zili ngati kugulitsa nkhuku ziwiri nkugula dzira limodzi nkhani iyi njobvuta kwambiri koma chakwera ndi osamvetsa mmaganizo

  • @DavisSeyani
    @DavisSeyani 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mtola nkhani iwenso ndi ofoila mafunso ako ukutanthauza chani ? Uli mbali iti ukudya ndikukhuta eti?

  • @festonmpombwe9462
    @festonmpombwe9462 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbuzi yeniyeni😂

  • @AubreyKammwamba-to7uv
    @AubreyKammwamba-to7uv 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela prazdent opusa kwambli galu wamunthu

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma Apule amanamudzidwa kwambiri. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Asanduka zgete Naye wosadzindikira zinthu

  • @JoãoChirwa-n3l
    @JoãoChirwa-n3l 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kd tu chakwela mutu mwake muli mamina ndiposo pakunya pamache ndithu

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pepani tinazolowera zinthu zolandira ndipo timati Pali bwino kugula kulekana ndi kulima ndiye lero wolima wasowa

  • @phindiswatshibo7101
    @phindiswatshibo7101 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Anasuta chamba 😂😂

  • @alexpetros4021
    @alexpetros4021 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma chakwelayu akudya chamba

  • @ResterKabudura
    @ResterKabudura 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kd chakwerayu amalima kut azit matumba 2achimanga agagule feteleza

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela anamuononga ndi chimwendo

  • @veronicagullo9373
    @veronicagullo9373 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukatukwana mmapeza chani

  • @PeterRabson-z3w
    @PeterRabson-z3w 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera mmutu mwake n manyi okhaokha

  • @EmmanuelkpPraise
    @EmmanuelkpPraise ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A president adalengeza okha kuti mdziko muno mulinjala ndipo maboma 23 out of 28 amene zavutilatu,ndipo boma likupempha thandizo kwa mayiko akufuna kwabwino,komanso boma likuganiza zogula chimanga,ndiye funso ndilakuti anthu chimamnga achitenga kuti choti agulitse ngati mudzikomo mulinjala? Ndiye sindikudziwa kuti chimanga chakecho chichokera kuti

  • @KondwaniChumula-h8s
    @KondwaniChumula-h8s 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achakwera sakunama akunena zoona kungulisa matumba 2 achimanga ndy kt mwapata one bag of fertilizer

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chuma cha dziko lino chiri mu nthaka ndiye titenge ulimi Ngati bizinesi

  • @rexphiri6951
    @rexphiri6951 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A chakwera pilizi

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😮😮😮😮😭😭😭😭💔💔💔💔

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkk km chekwe?

  • @raymondsamsung5264
    @raymondsamsung5264 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mwati akulu amenewa bwanji?😂😂😂😂

  • @GiftZuze-ge1ne
    @GiftZuze-ge1ne 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimangacho chikupezeka

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uchitsilu chimanga chimene angamagulitse amalawi chichoka kuti poti fetireza otsika mntengo kulibenso chakwera ndimunthu onvetsa chisoni

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela bolo yake 😂 climinal killed chilima