Palibe chazelu icho Malawi 🇲🇼 yipindulengepo apo iwe Lazaro osatipusisa pano ngati ndise Ana ako ayi achina Nicki wakhala Kuja kwa sabata yose iwe ndiwe west president ever in Malawi kungoyendayenda basi
Kose uko mwayenda bwana nthena fetereza mundagule nyengo iyi yamala Sono APA mbwenu vula yayamba mukuyowoya mwenkha kuti nyengo yasitha mususkanenge vinyake ivi ngemundaruteko Ku sukulu aaaaa
koma president uyu amalawi atinthandiza tawoni wayenda mayiko 4 pakamodzi koma munthu uyu atinthandiza akungoononga ndalama za mbili malawi zovuta kwambili
Abwerako kogulitsa dziko lino.kwa azungu .osatipatsa ife report ya ngozi yandege ija kuchikangawa .@ Ndiponso .malawi kugwirizana ndi imf or world bank ife amalawi takana ma devaluation awo..chakwerayo wabwerako asaphenso anthu ena ife tatopa kutigulitsa kwa azungu
Nkhani ya ndege ndiyomwe mukuidziwa kwambiri? Kusiyana ndi njara matenda komaso chitukuko zomwe a president akulimbana nazo kut zithe; koma inu mukukongoti ndege ndege kod ndikuyamba kuva kut ndege yagwa? komasotu inuyo m'mene mwakulila apa ndege simunaionere pafupi mumangoiona pa mwamba kapena mu magazine abasi
Amoyenda afika,,kokapinyolitsa dziko.
Komandiye eee first Lady wapa Rumphi nyagondwe
My vote mcp basi watembenuza Lilongwe as capital city
Useless president ever
Osakhara iweyo bwanji mudzapikisane tidzaone ngati ungawine or mp iweyo sungakhale
Welcome back Mr President
Kumene umakakwera njinga kkkkkkk osamanamatu ama achikangawa inu
welcome back our leader
Kodi zimayi ang,opa mbambalipo ndindan
Welcome back Mr president
My President and my vote
Me chikangawa
@@SuzgoMkandawire-ss4khiwe ufuna WA MA albino uja kod
Home is the best my president welcome back
Welcome Mr chikangawa
nkhuku yamunthu iwe
Welcome back my President
Inetu ndimangodandaula saulosi chilima chifukwatu ndamene anapasidwa ma mvote agalu ameneyo popanda chilima iweyo ndege siukanayidziwa kukwera kwake iyaaaa
Wapindula kukwera mnjinga the worst president ever,Koma kujambulisa ndi azungu
Takulandilani bwana president,nthawi zonse timayamika ntchito zabwino mumagwira kutula ziko lathu la malawi.2025 mukuwinanso chisankho bwana,mulungu ali mbali yanu bwana ❤❤❤❤❤❤❤
zigawenga
Kapolo wa ntchimo 😎🇲🇼
Ine angondiwaza ndi a fist left ledy mene akwayang'anila amuna awowo 😂😂😂😂😂
Palibe chazelu icho Malawi 🇲🇼 yipindulengepo apo iwe Lazaro osatipusisa pano ngati ndise Ana ako ayi achina Nicki wakhala Kuja kwa sabata yose iwe ndiwe west president ever in Malawi kungoyendayenda basi
Bola chakwela akuyendela zothandiza dziko Kusiyana ndi PITALA kudwala nyamakazi mpaka kwa merika
Lero onse abvala ma glass ofanana ziliko ku malawi😂,
😅😅😅
Pamtumbo pako galu chakwela
😂😂😂😂
Kkkkkkkk😂😂
Iwe ndiwe chitsilu nkhani zake zomwezomwezooo Chilima, Mia mizimu yawo iuse muntendele
Kodi bwanji salemekeza chiyankhulo chake.akuuza nzungu wake uti pamenepo.vuto la nyasaland losalemekeza chikhalidwe chowo.yankhulani chichewa kumayambirilo mkulu
Osangoyankhula chichewa bwanji
Ofusayo anafusa mchizungu or Chichewa?
@@williamsalexmbonga ndikuti Chakwera adzilemekeza cjiyankhulo chathu.Malawians first.adziyankhula chichewa otanthauzirayo mchizungu
😂😂😂 m'mesa wayakhula chizungu ndi chichewa. Mwina siminamve zimwene waziyakhula m'munchizingu zinja ndizomwezo wayakhula mu chichewazo
@@PociahMack ndikuti adziyamba chichewa. Malawians first chifukwa speech yo akufuna kuti timve ife.
God bless you my president
Which God should bless me chikangawa
@@SuzgoMkandawire-ss4kh don't judge any one it's only God knows
😅 Madamuwo kubisa maso akulu akulu 😅😅
Kaya mawandiye ukhala wakutiko kaya😂😂
Not on MBC ?
Kose uko mwayenda bwana nthena fetereza mundagule nyengo iyi yamala Sono APA mbwenu vula yayamba mukuyowoya mwenkha kuti nyengo yasitha mususkanenge vinyake ivi ngemundaruteko Ku sukulu aaaaa
Impoxyo unapita kwa azunguŵo kuti uphenso a malawi magazi ake muzikamwa .nkumagulitsa
Mulungu awakhululukile sakudziwa chomwe akuchita
Chakupha icho
Zitsili ndife posokha misokho kuti ayende galu ameneyu…….. ku Mozambique 🇲🇿 ubale wa anthu andale okha okha umenewo
Mr presidency want about za ndege ku Chikangawa results...?
Awa andichimwitsa pls,
Fuso ndirachichewa maboza wonkha kuyankha muchizungu
Nonsense 😮😮
Kom namaphodayo amayitha 😂😂😂😂
Madamuo dzulo anavalaso zomwezo ku jereman leloso sana sithe
Sanasambeko
Kkkkkkkkk
Nzomwe ndikuona inezi kkkkk@@SigereAckren
Koma uyu spresident ot angathandize malawi
Kuchibwano kopanda ndevuko
Athu osawuka kkkk koma Lazaro zilemerani ife tikumwalira mutchuke ndinu tikakumana kumwamba komweko
koma president uyu amalawi atinthandiza tawoni wayenda mayiko 4 pakamodzi koma munthu uyu atinthandiza akungoononga ndalama za mbili malawi zovuta kwambili
Look the face zikusiyana zomwe akunena ndizomwe amakachita
Za report ya ndege yakuchikangawa zili pati ndizomwe amalawi akudikila kuti amve.
Koma mutopa simunati
Akuti chani Koma?
😂😂😂😂😂 tamawawuza zanzeru ana umapita kukalapa kwa pape mizimu yathu akufa ikukunzunza iwe
Kodi azazi awowomesa adakasunthapo kaye pakamelapo
Galu uyu zaziwa chimene akuchitha
Zamanyi
Madock achani anthu akutha tikut
Usatipusise galu iwe mesa unapita kokwera jinga !!!
Chindere iwe mr chikangawa
Atolankhaninso mumafunsa zopusa kwambiri kumatha nthawi ndi chitsiruchi
Azungu Adandaula Poona kuti chidole cha wa chokera
Akanakhala achitukuko sibwez akuenda chonchi chisilu
Mtundu wa Malawi uvutika ndi Chakwera
Zaziiiiiiiiiiiiiiii
Agalu inu atolankhani oputsa za Report ya ndege simungamufunse chilima mulibenaye ntchito?
Iwe chakwele ndiwe galu kwa bas
Ndiwe galu kwabasi
Zaziiiiiii
Kupusa umakakwela njinga zachani this time we must drum about bicycle are serious
Mmmmmmm
Zazii
Kkkkkk
Gulu uyu
Nde kujelemaniko munawauza kuti amalawi simunawauzebe zakafukufuku wandege
Monse mwayambira zamages mpaka zaka zinai mukupempha mages za ziii munthu opusa iwe
I think sometimes quite is the best solution rather than speaking dzithu zomwe sizingasithe kalikonse
Kokabisa lipoti landengeko
Mbole yako chakwera
Mbuzi ya munthu ya mano kusi iyiiiiii
Mmmm, zamnyanzi.
MACHENDE AKO CHAKWERA
Nosense
Mfiti
Iwe chakwera udziyankhula chiçewa osati chizungu .kodi iwe siobvina guĝtetee? Ndiye ngutetee amalankhula chizungu .kunyada mnanu.a gutetee
Nafwaaaa kma zilikooo