All the best on your trip. My request just as any ordinary citizen, Mr President can't you take an advantage when meeting president Nusi to discuss about Nsanje port. That even it failed for those big vessels but at least to open for small licensed boats for small scale business among Malawians and Mozambicans within that area. Not far as Indian Ocean NO but Zambezi-Shire only. And the two governments can create customs activities. Nsanje can benefit slightly positively.
Kuwafunila ulendo wabwino Mr President Chakwera ,komanso kubwelela kwabwino ,have a good journey ND health Returning Mr President we love you Mr President,And also you are only our president for now , wishing you all the best n success,
Maulendo Ako omaliza Amenewo ukamabwerako uzabe ndalama za Amalawi. Nthawi idzakwana udzayedzekedwa . Kalandireni degree ya umbava yo komanso degrees ya uchugawenga🔨🔨⚒️👹
Koma a Malawi simudzatheka ndipo minu mudzamva nkhwangwa ili mutu, ndinu opusa kwambiri, ochenjera ndi ochepa. whats funny there? you already forget what happened few months ago?????, Akukazingeni kaye ndiye mudzamva bwino,
This is using mother's dance always without thinking u can jst go don't pretend to be good reader bec Malawi we lost future with our readers who take advantage with people
Muyende bwino Abwana we love you Mr President
Long live our dear President! We love you!!
DONT SAY WE LOVE U GALU
@@cjaylucky wandiwaza😂😂😂😂
Good luck and the best
Nice travel Mr President.
Nice journey our own president, God bless you.
Wakulu Don Chakwera❤
All the best Mr President we love u
Why only questions from MBC what about others
All the best our president
All the best on your trip. My request just as any ordinary citizen, Mr President can't you take an advantage when meeting president Nusi to discuss about Nsanje port. That even it failed for those big vessels but at least to open for small licensed boats for small scale business among Malawians and Mozambicans within that area. Not far as Indian Ocean NO but Zambezi-Shire only. And the two governments can create customs activities. Nsanje can benefit slightly positively.
my vote 🗳 ❤❤❤❤❤❤
safe journey mr president
Nice journey Mr president
I'm just looking at Monica😂
Me tooo
Muyende bwino president ❤
Please also talking about Africa unite, we are tired of staying by fear while one continent
We want issue of one Africa,
Yendani bwino mr president chikangawa
Why only one question from one broadcasting station
A Malawi chonde tiyeni tilembe zothandiza dziko osati zonyoza zokha zokha
Masapusi
Kuwafunila ulendo wabwino Mr President Chakwera ,komanso kubwelela kwabwino ,have a good journey ND health Returning Mr President we love you Mr President,And also you are only our president for now , wishing you all the best n success,
Kkkkkk monica ngati chidole kkkkk amakupenta bwanji kodi
President Nyusi ask him what happened to his vice president till now we ask questions but he don't answer us .
Ku Harareko ukumanako ndi C .Ramaposa akufusa za Bushiri 😂😂😂😂
Za ku jerman ndi italy atolankhani simunatiuze tu 😂😂😂
Azere kuchikangawa atleast akaoneko pamene panafera our last hope we had😢
chitsiru cha presdant chongokhalira kupempha mayiko ena ich nditsiru kwa africa kuno mbuzi ya munthu
❤
Chakwela mpaka 2030
Why do you add back ground music to your Videos?
Muyende bwino bwanaaaa!
Dr Lazaro chalakwe chikangawa chakwera
😂😂😂😂😂
Zimfiti zikulu zikulu zkukambilana zasataniki apa akut kusazikana kut sala nzanga ine ndikupita koma mbuyo muno ngozi ndiy zchitika lero zkuchitikadi😢😢 ambuy bwerani muzikanthe mfiti zmenezi
Monica kodi omuphodawo amamupenta motani kkkkkkkkkkkk 😊
Angokhala okanika vuto siowaphodai😂😂😂
Endani bwino mtsogoleli wathu
Wosayenda pasi pa Mozambique pompa 😅😅 chifukwa ndege akukwelayo sabwelako
Ufananitsa ndi iwoyo lod? Iweyo ungakakumane ndi president was ku Mozambique osangopita ndi Iweyo bwa
@@kingsleyhopematchaya5184 who are you yourself bro i know is your brother and i don't care about chakwera bro who's him the killer
Umuwuze asabwerenso
Chikangawa pilot ameneyu osagoingwetsa bwanji amupange ngati samora
Far from that,musiye kuwafunila anthu zoipa
@@HassanJimmy-r1n inu mwadya chani Kodi?
Chingangawa
Makola chikangawa
Kma Monica iwe 😂😂😂😂😂
Talk about colonialism border to be borderless
Kma mai wafukoyu 😅😅😅 nd nkhan zina
Tithandize kuma passport iwe zithu zovuta kwambiri
zilibwino ❤
Muyende bwin tikufuna tizakuchosen nd zisankho osat chifunga 😂
Ayende bwino km tikudikilira mayakho andege yija yinagwa mwezi wa June ngati safuna kutiziwisa ife a Malawi nayeso akafele komweko .
Travelling Mercies from Our God Almighty. If God say YES who can say no! Nobody we Love your our dear President!
Chikangawa galu iwe almost to die mesa wayamba kukwera ndege you will see
Athu inuyo mumaphida Monica sakhanikoni powder wabwino yooooo even lipstick
Exactly my point 😂😂
Eish ndiponso ntchito akuyilephera saphoda bwino
Kkk😀😁😂
😂😂😂😂Ndipo inu eish kkkkk
Kkkkkkkk mwina ndi powder yemwe amamuko Ababa kkkkk
Kmso mukhazikitse ministry of thread chifukwa makampany akungopanga mitingo yao yao mopanda matha mutengeleko chitsazo thawi kamuzu katundu samakwela mitengo opanda boma kudziwa
CHAKWERA PANYO PAMAKO WAVA UKUTIONONGELA NDALAMA ZANTHU GALU IWE
Brazil tamuoneniko ndi imoz galu uyu kutumulani chifunga ku Mozambique
Haaaa ndikawona ndege chochi mmm mutumu ndimabalalika kapena ndege yoyipitsitsa ndiinja inatsakama mchikagawayi
Tamuoneni chayang'ana kumbuyoyo
Adakagwa ameyu Bwezi titabwelera kumudzi
Akafele komweko nayeso mesa samafuna kutifotokozela za ndege ija yinagwa
Bwanji muyendele Ku chikangawa njila yamadulila 😅😂
Ndamuwuza kale pilot kuti atelo😂😂😂😂
Zoona eti ngege yomwe anakwera Chakwera yagwa😭
Walakwisa ngat m'mene walakwisila malembedwe akowo their will return safely Sir ,please wish them well?
@HassanJimmy-r1n I cannot wish him well until we see report
Koma mbc mumakokomeza bwanji, fumsoli modzi koma mwalipanga kukhala mafumso 😂😂😂😂
Kufupika kwina ngati munalodzedwa 😂
Anthu onsewa amakatani kumeneku.amalawi khalidwe limeneli tidakasintha makhalidwe osiya ntchito mkumapita ku airport za nziiii
Popekeza apm uja amakatani ulibe zeru owe or makolo ako sanawaperekezepo kod
@@kingsleyhopematchaya5184 nmunthu wanzeru satangera khalidwe lonyasa.mudziyenfa mbuli inu.ndizopindilra dziko chiyani.mfumuu kupita kumeneko kapereka moni basi nosense.
Mukadutseso kuchikangawa mukamakabwera
Mukufunika mzimu oyela omwe umateteza kayankhulidwe
Chigawega
Kukakambirana zobera mavoti munya muona masatana inu mizimu ya anthu 9 ili pamutu pako chikangawa iwe
Bola mukanayenda pa galimoto chifukwa maputo salipatali ndi dziko lanthu after mukutionongela misonkho yanthu
Wakupha😢
Ndege imeneyi ikagwere kuchikangawa
mukusoweka mzimu oyela inu
@@chiletsokazembe-ri4ic mukhale zot muli ndi mzimu woyera bwezi muli kumwamba
Udutsile ku chikangawa wamva
Ndizokomera inu achakwera kuyenda pa ndege kubwera amoyo achilima ndi azawo akubwila dothi mtendere wanu mukhale amuyaya ndi banja lanu dzikoli mutenge muyike mnyumba mwanu anthu asamavote chilima awuse mumtendere tidakalira mpaka karekare.
Iyayi tikapuma mulungu akasatitengamo
Tiyezeka
Ayi mwawina podzola eletsa nomse
Black box ilimo koma?
Kaya😂😂😂😂😂😂
Degree yachani zasatanic basi
muzere kuchikangawa
Mizimu ya anthu 9 ija ilinawenawe ndipo sikusiyani apule
Sanje sumuna😀Akadalitsa wadalitsa
Mudzina la mulungu iyiso igwe mukharango isanafke komwe akupita
😂😂😂😂😂😂😂😂
Tsopano abwanawa analemba ntchito bodyguard wamkazi kapena ndi sing'anga wake? Koma ndiooneka olusa
Ulemu umapita kwa oyenelela ndiye muthu oipa sakuyenela kulandila ulemu m,fumu t
Yoipa isowe m tendele
Asakaguliseko nyanja yathu uko please tamuuzeni
😏😏😏😏😏😪
Eee koma anthu muli pano 😂
Kod kulibe chifunga kumeneko
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Wakafere Koko
Maulendo Ako omaliza Amenewo ukamabwerako uzabe ndalama za Amalawi.
Nthawi idzakwana udzayedzekedwa . Kalandireni degree ya umbava yo komanso degrees ya uchugawenga🔨🔨⚒️👹
Chonde bwana njira muzele ku chikangawa
Basi si dzikoli amusiyire comedian.🥰..muzangonva kuti museweroli munali.....😅
Koma a Malawi simudzatheka ndipo minu mudzamva nkhwangwa ili mutu,
ndinu opusa kwambiri, ochenjera ndi ochepa.
whats funny there?
you already forget what happened few months ago?????,
Akukazingeni kaye ndiye mudzamva bwino,
This is using mother's dance always without thinking u can jst go don't pretend to be good reader bec Malawi we lost future with our readers who take advantage with people
Kodi Za ndenge ATI zatani mu dzalanyama
🤣😂😂😂musatipalamilitse ife
Bwana chitani kothekera Mafuta a Galimoto ansike basi
Sangasike😂😂😂
We can't be happy with u bcoz u r going in 🇲🇿 with our misonkho thats rubbish nonsense mbava zokhazokha we know what u r going to do there
Mafuta agalimoto asike basi
Sangasike inu
We don't love you
Bola kumeneko mukakambe zopindulila ife misokho itsike kwambili osati zililimu ayi
Yendani bwino mr president chikangawa