@@GraywellChirwa what is "sanje"? But if you mean "nsanje" then you're wrong coz munthu wa nsanje samapanga point pomwe sipali bwino or maybe you didn't watch it coz if you did you'd understand what I mean
@@jumakananjirazim ayi ndithu si chimidzi, koma show yoti DJ aziyika zima sound zake zokwela and voice ya host ndi guest izinvekela pansipansi zimabhowetsa show. Next time azapange Improve ma guy wa, ubwino wake ndi channel yawo awona ma comments wa
Mkulu uyu ayambe comedy. I am surprised, I am enjoying his interviews more than his songs
hahahahaahahahahaha akuti uli ndi matako koma si type koz ndimakonda ana eish koma eish kkkkkkkkkkkk
Eeee chi khalizma ndi chi vibe 🤣🤣🤣🤣
Umatha kucheza😂😂
Zani mwati chani😂😂
Program yose ili kumapeto 😁😁 real mijedo plus madness 🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Dislabada uyu palibens😅😅😅
Ayike ayambe kumbuyoko watching live from capetown paboma mijedo to the world 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Is tandifusire for me 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂nice koma
Koma Chariz aisee😂😂😂😂
Koma aixe. Uli ndi Chi vibe ✨️ 🎉🎉🎉
Nyau uyu.....size ya Aunt anga. Chipongwe choona sichabwino
Charisma😂
Pa eazy basi kuvera mijedo😂😂😂😂😂
Ili Bhobo adumbu
Nyauyu. Mamuna ndie olo kumuuza kuti buluzi owotsa kumudya shaft sichiphwela azidya abuluzi 😅😅😅😅
❤❤❤
Uli bhoooo nya uyu
Kma ya thelere siinathe bwino ayi mwatan kod Queen of Vilekeke 😂😂😂
Charisma ndichi vibe amwene😂😂😂😂😂
Enjoying
Charisma kucheza naye eeeh ndikupilira eish 🤣🤣🤣🤣🤣👋🤔🤔🤔🤔
ase mpaka tabweraso ku you tube 😂😂😂😂😂😂
Ruzma uchokela ku Ntchisi tininkheni T shirt chonde 😂😂😂
Tafikatuuu😂🎉
Fire
Donzo anaonjeza eeeh 😅😅😅
Wukutivetsa sugar watching live from south Africa
Ma sound effects kukwela kuposa mau a host .....nice interview..ma Dj mbola
More fire 🔥🔥🔥🔥
Atitonsefe tilibe zachita yoh😂
Watching live from Cape town table mountain
Voice ndiye ikuveka motsikatu koma... Takonzani pokhapo. But all in all zonsezi zili fayah 🔥🔥🔥🔥
Chikuopa agaluuu 😅😅😅😅😅😅
Kumapetoko nde fayaaa 🔥🔥🔥🔥🔥
Akazi aku Dubai avuta ku Lilongwe 😂
Fire
Namu nasuzgikila kuti nikusange nganya 😢😢
Hahahahaha phepani. Make sure you also like my page on Facebook and enjoy all the shows
@@FelistusNgwiraNyauyu napulika longosi
Km charisma 😅😅😅
Mulibo ccsta,it's Arthur Gondwe from Mpherembe
🎉🎉🎉 fanayu ndi dolo
So Malceba was @ Bunda?🙄
Meet bombshell grenade n collabo bwana chari
nya uyu amafira Charisma hvy
Watching live from chitipa
Charisma ndi swazi
Charisma my look alike
Berim ikupanga print ,photography and graphic designs here from blantyre
Watching from jhb vanozga
❤❤❤
charizzzz
Sound ikuveka pansi but zili bwino ❤
Ati gayika nyimbo ya mzeru shaaaa
I love you NyA
😂😂😂😂😂
Show ya char you should av playing his songs the whole show men
ATI Mmmmm cari
Madhala charisma
🔥🔥🔥🔥🔥🙌🙌🙌🙌
Live from Lilongwe area 50
Madala Khali🔥
Nyauyu Blantyre we here
Dzukani mubvine
Apopo mwafika team zeze
Taponya ma T- shirt wo mulongosi
Mmm from kasungu tigairekoni tchirt abale Berlim visions they do photography and videograhy
Mpaka mafuso 4 guest musanamuonetse
Chariz 🔥🔥👏🏻🤴
Live from dwangwa
Khali umakwana❤
Madala charisma
Volume kma
Uplifting she-gender. On fire nyauyu
❤
Mkazi iwe umakwana
Tifusileni koma
Nyauyu zakuno
A feli
chalisma ndi trapper wanyatwa 🔥🔥
Big up
Volume 😢
Kodi soundyo nde Kuti ilibe volume?... Otherwise show yabho
Kod ya jaa kev sipezeka bwanj ?
💪💪💪💪💪💪💪
❤❤🥳🥳🥳
Sound mixing nde mbolatu, it ruined the whole show
Sanje
@@GraywellChirwa what is "sanje"? But if you mean "nsanje" then you're wrong coz munthu wa nsanje samapanga point pomwe sipali bwino or maybe you didn't watch it coz if you did you'd understand what I mean
Zoona bro mbola
Ife nde timakomda mixing yii Kaya mchimiz Kaya chathu koma😂😂😂
@@jumakananjirazim ayi ndithu si chimidzi, koma show yoti DJ aziyika zima sound zake zokwela and voice ya host ndi guest izinvekela pansipansi zimabhowetsa show. Next time azapange Improve ma guy wa, ubwino wake ndi channel yawo awona ma comments wa
Nice 🔥🔥
Umatha kucheza nya uyu
😂😂😂
Umakwana iweyo usazafe uzangosowa
💥
😂
volume is too low sound engineer aipase moto
Uyu nd dolo
Nya_uyu umakwana
Kuyipasa moto Mesa
Blantyre lunzu
Umakwana iwe
Ifenso zanie ndi ma hope athu