Theresa Phondo - Zambezi (Audio)

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024
  • Zoti kunja kuwala
    Palibe angatsutse
    Kuwona madzi mu khwawa ooh
    Palibe angafunse
    Kunja kuwala yeay-yeah
    Palibe angatsute
    Kuwona madzi mu khwawa oooh
    Ndendende ndi mmene
    The way that I feel for you
    Palibe chimene
    I wouldn’t do for you
    Zoti ndimakukonda
    Sizovuta kuwona
    Chikondi changa pa iwe ndichokuya
    Ndendende Zambezi
    Awh yeah
    Ndendende Zambezi
    Ooohhhh
    Ndendende Zambezi
    Ayayayayaya ohhh
    Ndendende Zambezi
    Ayayayayaya oohhh
    Dzuwa saalozelana
    Zamumtima saauzilana
    Koma zoti ine ndimakukonda iwe wekha
    Palibe angatsutse
    See my actions revealing
    The way that I’m feeling
    Na chikondi chokachi palibepo oleletsa
    Ndendende ndi mmene
    The way that I feel for you
    Palibe chimene
    I wouldn’t do for you
    Zoti ndimakukonda
    Sizovuta kuwona
    Chikondi changa pa iwe ndichokuya
    Ndendende Zambezi
    Awh yeah
    Ndendende Zambezi
    Ooohhhh
    Ndendende Zambezi
    Ayayayayaya ohhh
    Ndendende Zambezi
    Ayayayayaya oohhh
    Zoti ndimakukonda
    Sizobvuta kuwona
    Chikondi changa pa iwe ndi chokuya
    Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah x3
    Ndendende Zambezi
    Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah x3
    Ndendende Zambezi

ความคิดเห็น • 57