Satana Chokele ndife magulu Ayesu. Chakwera wachita chotawa ku CCAP akusekedwa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 57

  • @user-mi1rr6wq7o
    @user-mi1rr6wq7o หลายเดือนก่อน +5

    Komande atsekuratu mimba yoooo

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +3

    Ndipo tiye nayeni sazaupeza m, tendele muthu opanda manyazi wamanga m,busa wa CCP lelolo akupita komweko umuthu alibe ndithu satana ameneu

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน

      Ndiopepera Zedi ujaa😂😂😂

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน +2

    Mizimu yakwiya, waganiza zokapemphela lero, zaululika basi kuti black box yili ku state house., wanya.

    • @user-tk6qh9zs7h
      @user-tk6qh9zs7h หลายเดือนก่อน

      Bodza ilo.
      Mudziwerenga nkhani nokha ndi chifukwa chake ndinu a Misala

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y หลายเดือนก่อน

    I support UTM and always i will miss SKC. Besides LUZ is the only president that malawi is currently having he deserves respect. If God can allow it that he should be distracted then we should know that the whole nation will be distracted. Rather let's pray that God should give great wisdom to those surrounding him because he is not a self decision maker.
    Am not condemning the song but comments that are flowing.

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน +4

    Kkkkkkk koma kumeneko mulungu akhale nanu

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td หลายเดือนก่อน +1

    Agonthi tilipo kumalawi CCAP sipanganawo zaukape mukamuona otelo nansongole ameneyo nyimbo yandale chuni chandale kuikamo yesu zipita kwina akhilisitu tisamale zandale ndiza yesu tiyense kupeza mayimbidwe athuathu

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 หลายเดือนก่อน

    Its just asong nyimbo iyi ndiyakale imayimbidwa mostry in churches ostati chifukwa cha ndege no no no

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 หลายเดือนก่อน +4

    Amen

  • @AnnieJutta
    @AnnieJutta หลายเดือนก่อน +1

    Umunthu ngofunikadi munthu kumanga m busa wa CCAP lero mkumati mkupemphera komwe koma mzimu wa chilima uzuzadi anthu ndatha kuona tiyeni tipitilize kuyatsa makandulo mpakana Ambuye atiyankhe basi

  • @ChrispinKashosha
    @ChrispinKashosha หลายเดือนก่อน

    Nyimboy ikugwirizama bwanji ndi chakwera sikukamba kalikose za chakwela mbuzi ukungofuna kuononga ma data aanthu

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh หลายเดือนก่อน

    Kulikonse angapite kopephera nyimbo yake izikhala yoteroyo kuchitila kuti satana oyipayo azichita manyazi

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 หลายเดือนก่อน +2

    Isshhh abwana alimavhuto ndithu

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i หลายเดือนก่อน +1

    Bwanji osangowalola ena akaimire ku convention!😅😅😅😅😅😅

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i หลายเดือนก่อน +1

    Koma ndikuona ngati munthuyu akhonza kungothawa!😅😅😅😅😅😅😅

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk....komatu achewa apa mwafika pena..😅😅😅😅😅😅...ndiye amanga ndani pamenepa? 😅😅😅😅😅😅😅

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂 Yomweyo Chikangawa sunati uzimangilira

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v หลายเดือนก่อน +3

    Koma nde ayalukatu satana chokeledi akamwe magazi anthu 9 aja devil

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e หลายเดือนก่อน

    Amen 🙏 🙏

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o หลายเดือนก่อน +1

    Nde mumafuna kut ayimbe kuti yesu tichokere koma muli pa ntchito chakwera Ali phee

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef หลายเดือนก่อน +2

    Mwamuchita bwino kumuimba satana opha anthu 9 amu Ndege

  • @user-tk6qh9zs7h
    @user-tk6qh9zs7h หลายเดือนก่อน

    Ubwino wake mulibe dzina la munthu.
    Komanso Chakwera sanachoke chothawa izo mwanama ife timali komweko.
    Namizani a Misala enawa

  • @user-gj6gc3cc2j
    @user-gj6gc3cc2j หลายเดือนก่อน

    Mulungu amuone agalu am kumumpha chilima Inu mulungu sangalole kuti muwine agaluiunu assatana

  • @MaryNyalapa-u2t
    @MaryNyalapa-u2t หลายเดือนก่อน +1

    Munthu ukachita tchimo umakhala kapolo watchimolo.

  • @JessyChidanzi
    @JessyChidanzi หลายเดือนก่อน

    M'zanu mukulimbana nayeyo sakukuyankhani zomwe mukupangazi mukupangitsa kt anthu mukuwanyozawa azingodalitsika bansi osachita mwanyazi kt palibe akukuyankha kd mukunjenjemete simunati

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw หลายเดือนก่อน +1

    before 2025 General Election nkuruyu akhara atazimangilira

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 หลายเดือนก่อน +1

    Anyanayo chakwera azipha ndithu

  • @collesTambala
    @collesTambala หลายเดือนก่อน

    Mmmm zabodza koma athu eish

  • @WilliamKawina-y7d
    @WilliamKawina-y7d หลายเดือนก่อน

    Sakudziwa kuti akutumikira satana yemweyo

  • @ChimzyBatson
    @ChimzyBatson หลายเดือนก่อน +3

    Koma muli ndiganyutu kkkkk

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira หลายเดือนก่อน +3

    Kkkkk km athu mwakwiya

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma หลายเดือนก่อน

    Eyetu kwake kupha kuononga chikangawayo

  • @user-ng6ku3lh1r
    @user-ng6ku3lh1r หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkk Koma kumeneko 😂😂

  • @user-hx2nq4pq3l
    @user-hx2nq4pq3l หลายเดือนก่อน +2

    Koma zovuta kwabasi

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน

    Kkkķkk Chakwela ukuva bwanji?

  • @JumaKachala
    @JumaKachala หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkk athawa sanatiii

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂Koma yaaah zoziputa 😂😂😂

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 หลายเดือนก่อน +1

    Azimangilile satanayi

  • @MtendereKamwiri-re7yr
    @MtendereKamwiri-re7yr หลายเดือนก่อน +1

    I think dis song it's not new one! It was present before

    • @user-pn7cj9hb3t
      @user-pn7cj9hb3t หลายเดือนก่อน

      Funso ndiloti pa nyimbo zonse bwanji kungosankha iyiyi?

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 หลายเดือนก่อน

    Yoo ziliko zafika pa mwana Akana phara ndithu bwanji manyazi

  • @BawulenLuka
    @BawulenLuka หลายเดือนก่อน

    Wangwilo ndani?

  • @user-ey6in8is5h
    @user-ey6in8is5h หลายเดือนก่อน

    Mbuzi za anthu aMCP kwathu Pena pake timati'agaru kunyindaa!"

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk koma wina azipha chaka chake chino

  • @mosysi324
    @mosysi324 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂 eeeish no comment on this hahahahahah

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน

    Amen ❤

  • @RachealPongolani
    @RachealPongolani หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂

  • @captainsisitomalawi1548
    @captainsisitomalawi1548 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂

  • @user-eh1gn1nj9d
    @user-eh1gn1nj9d หลายเดือนก่อน +1

    Muchedwa nazo izi

    • @LuciusLungu
      @LuciusLungu หลายเดือนก่อน +1

      Zitizo zotchedwesa?

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂