Welcome my bru u still look nice
Nyimboyi amene sayikonda ndiwopanda mzelu chifukwa muli langizo nditu lambavu❤❤
Guys too nice song 🎵 keep it up
oh my words great job
Amsako ntchito mukugwila ❤❤❤❤❤❤ keep it up
Charles Nsaku mulikuti ndikupaseni Bonas panyimbo yomwe mwayimbayi Lave you❤❤❤❤
Welcome Mr Nsaku muli bwino mwapanga ft yo aaaa akuononga nyimbo
You are talented braz,more fire ❤❤❤
Fire mabomba reggae machine
Umakwana m'bale wamu Extension 6. Chi-Hit chako chili bhoo heavy!! Tikumane pa Jehova witness-pa Pali uwiri achimwne. Mumakwana zedi❤️❤️❤️❤️🤌🏻🤌🏻🤌🏻🤌🏻🤌🏻🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Zili bwino, Mr nsaku munasowa kwambiri, timakunyadirani kwambiri, from cape town
Welcome back
U remind me mzuzu legend those day
Keep the fire burning 🔥
Amene akunyodza nyimboyi ndiwopanda mzelu kobasi muli langizo nditu
Welcome back chris Charles nsako akatundu
Mr nsako ur a legend koma guy winayo waipisa nyimbo
Charles Msaku please bwelerani muzizayimba, you are missed
This is the real sounds ❤ the touch remains super
Great tune
Video plus message all good nice collabo 🔥🔥💯
The legend, welcome back. Dzina mudapanga kale.
Nice song mr charles nsaku keep the fire burning watching it in cosmo city extension 4 Johannesburg south africa
Yapendekeka nyimbo ya bwino kwambiri 🙏
Welcome back mr Charle❤❤
Tsache lakale kudziwa kusesa makona😮
Namandwa wa live performance Msaku umatha kuimba we've bn waiting for your comeback
Nice one big we will teach us
Life ya safulila
Welcome back big man
Ansaku mumakwana big, timakunyadirani more fire
This is massive
Powerful this song Mr Charles nsaku ur welcome.
Charles ❤that is true chabwino palibe pa jozz
❤🎉 alibwino awa amatha
Nsaku wanga sadzagonja please bwerani tasowa ma live show anu my reggae machine.
Respected sir ❤
😊 back in action
Mwasowa na pa Cosmo City
Yapemdekeka official ija yafika basi tionele 🎉🎉❤
Nyimboyi mwayikazinga abigi❤❤❤😂😂😂
So powerful ❤
Good song indeed full of advise
Njanji ya reggae is back moto kuti buuuuu 🔥
Zoona big man ❤
Nkhani ya zoona iyi more fire ❤❤❤
Legend never die 🖖
Chihit mesa nsaku forever give up🔥🔥🔥🙌
Nice tune biggy
Nice song big
Big tune
Good song
Welcome back Mr nsaku
Koma akulu awa 🙌🙌🙌
Malawian music legend
more fire 🔥🔥🔥😁
Still the best star
Nice track
Or atasowa kwazaka koma akatulusa nyimbibo imakhala bomba
Nice song charles
Who remember this......
Charle! Charle! Charle! Charle! Charle! Charle! Charle!
Fire mabomba mesa
Koma mumakhala ndimilandu akulu,,,,, mwatiyalutsatu.......
Iwe wananga nyimbo iwe MJ manyi iwe, but our Sanku is the best always, MJ wawonjeza mphuma munyimbo and jokes iyaa
Respect
Machine charles nsaku Mbambande song yapendekeka
Machine opangira machine anzake
Welcome back nsaku
Powerful
Ndakunyadilani big❤😂❤😂
Inuyo ndi machine... Ulemu wanu
Machine machine
chipheeee chadzaaa
Munthu wa nkulu ali pa black label 😅..uthenga ndi wabwino.,❤
Chi hit cha bho heavy ndipo ndachikonda
Power
Welcome charles nsako
Good job Nsaku
inu ndadala bigi man ❤❤❤
Nice one
Zoona yapendekeka simomwe zinalili kale
awuze siunama bg mn
Nyimbo yabwino nditu❤❤❤
More fire💥💥💥
Yapendekekaaaaa
Muthu wamkulu kwambili sanathe
Salute saku❤
Nsaku🎉
More 🔥 Cosmo city
More 🔥
Ndipo simukunama Mr Charles yapendama
Mwayìmba bho koma mukokele kathipipo
Wabwera boh Nsaku
Very nice song
Zoona sanathe Charles nsaku
Tivineno beautiful song
Charles Nsaku mulikuti ndikupaseni bonas
Love your music from zambia