zaululika!! Miracle Chinga amapanga uhule

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 10 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 223

  • @yohanebanda7537
    @yohanebanda7537 5 หลายเดือนก่อน +2

    Zinazi SI mbali yanu zisiyeni , nanga apa mukuti za uhule wa miracle zofotokoza zina 😢😢

  • @user-li3ym4cn5q
    @user-li3ym4cn5q 5 หลายเดือนก่อน +1

    Wakutsikabe Miracle go my girl thats the crying of a dying horse😅

  • @BrightNyoni-yd4ip
    @BrightNyoni-yd4ip 5 หลายเดือนก่อน +1

    Koma inu ndinu anyani zomwe mukukamba ndi zomwe mwalemba ndi zosemphana aaaaa amalawi pena musikhala siliyasi

  • @PreosTonour
    @PreosTonour หลายเดือนก่อน +2

    Anthu mumasowa zochita bwanji?osaphunzila kupanga zanu bwanji??? Za ziiii

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 5 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkk mulibe mfundo sir mukanangokhala chete osayankhulapo kanthu nanunso mwaonetsa moyo wachizimayi.

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga 5 หลายเดือนก่อน +1

    Miracle amapanga uhule anagonana ndibambo ako? Zaziiii

  • @AminaAgnessSaidi
    @AminaAgnessSaidi หลายเดือนก่อน +1

    Inu aliyense ali ndi zifukwa zake zokwanila kuthetsela banja ngati miracle samasangalala akhala bwanji ndimunthu yemwe sakumpatsa mtendere
    Phunzirani kupanga zanu komaso sibwino kuweluzana

  • @TamiweKalua
    @TamiweKalua หลายเดือนก่อน

    kusowa zochita eti ka gonani please 😂😂😂😂 musiyeni Miracle mulungu anamudalisa🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤

  • @BeatriceNahuwo
    @BeatriceNahuwo 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Khalani bzy kusaka chakudya chanu,ndinu akubanja kapena???

  • @patsonbanda3303
    @patsonbanda3303 5 หลายเดือนก่อน +2

    Yiweyo zabanja lako amafufuza ndani leave them alone

  • @user-vh5gp9is9r
    @user-vh5gp9is9r 5 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi banja loyamba kutha ndi limeneli mziko muno? Inu mwasowa zochita Kodi eti?😮😮😮

  • @RobertPhili-ib2tf
    @RobertPhili-ib2tf 5 หลายเดือนก่อน

    Mmmm okay chabwino APA ndiye mwati udzabwino AAA dzili ndiayiniyake dzimenezo Kaya abwerelana ❤

  • @EdithGoodson-tr2jq
    @EdithGoodson-tr2jq 5 หลายเดือนก่อน +2

    Guys b serious leave them and do ur own business, what's ur problem?

  • @DinnaHabonga
    @DinnaHabonga 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaaaa vutoo lakoo ndichaniii ,,,,,,ulibe zochitaaa etiii

  • @user-rv7tk8cv2q
    @user-rv7tk8cv2q 5 หลายเดือนก่อน +1

    Kungondithera bundle za ziiii.palichomwe ndamvapo apaa

  • @AlinafeSolomoni
    @AlinafeSolomoni หลายเดือนก่อน +1

    Iwe ndi londa wamoyo wa miracle?zantiiiii

  • @MAATPLUMBINGSERVICES
    @MAATPLUMBINGSERVICES 5 หลายเดือนก่อน +1

    Pezani anthu ena adzitha kufotokoza zomveka inu palibe chanzeru mwafotokozapoo

  • @user-lz4tj4zi3h
    @user-lz4tj4zi3h 5 หลายเดือนก่อน +1

    Osalimbana ndi banja la zanu.......... Zainu muzatiuza liti?

  • @Chisomochalamwendo
    @Chisomochalamwendo 5 หลายเดือนก่อน

    Nkhani ya Miracle Chinga simunayifotokezere momwe enafe timayembekezerera..mwina ndinene kuti
    'y͟o͟m͟w͟e͟ m͟w͟a͟y͟i͟y͟a͟m͟b͟a͟y͟o͟ s͟i͟m͟u͟n͟a͟y͟i͟k͟w͟a͟n͟i͟t͟s͟e͟ i͟n͟u͟y͟o͟ a͟N͟y͟a͟s͟a͟ H͟i͟t͟s͟,mwapanga palibe ngati mukuuza ana..
    ZA ZIIII

  • @PatriciaNyangulu
    @PatriciaNyangulu 5 หลายเดือนก่อน +1

    Kufotokoza kumakuvutani mpakana chaninchanichaninchani? 😂

  • @YohaneNapulu
    @YohaneNapulu 5 หลายเดือนก่อน +1

    Anthu Osauka amalimbana ndi banja la munthu wina tu...Iweyo Mkazi wako ali kutiko??

  • @user-rl1ye8ki2x
    @user-rl1ye8ki2x หลายเดือนก่อน +2

    Mwasowa nkhani hetti

  • @festusmhango
    @festusmhango 10 วันที่ผ่านมา

    Nde zachani zimenezo, zitaye usazalankhulenso ndiwe mwamuna

  • @user-vz4sn8mk1m
    @user-vz4sn8mk1m 4 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe tatolapo chazelu thawi yino siyomafufuza zamuthu pangani zina zosaka dola

  • @FieldMende
    @FieldMende 5 หลายเดือนก่อน

    Audio ndaimvetsera koma ndi mutu zikugwirizana guys?

  • @LalaNkhoma
    @LalaNkhoma หลายเดือนก่อน +1

    Musiyeni mulungu akhale mulungu

  • @MuhammadTennes-tx5ti
    @MuhammadTennes-tx5ti 5 หลายเดือนก่อน +1

    Awa amasowa zonenatu, iyi ndi nyasi hit not nyasa

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 5 หลายเดือนก่อน +1

    This is too much man,and mwayambazi ndizopusa simungafike pomunena munthu kuti ndi hule.ngati anakukanani musamuyalutse munthu munjila yake iyiyi and ine ndikanakhala miracle ndikanakakusumila, mbuzi ya munthu iwe

  • @RodrickLucious
    @RodrickLucious 19 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndichisilu kwambiri kodi kusokonezeka kwa banja ndiye kuti miracles ndi hule
    Sibwino kumayalusa anzanu please zilekeke

  • @EuritaDeric-fz3ds
    @EuritaDeric-fz3ds 5 หลายเดือนก่อน

    Mwasowa nkhan kodi iye amapanga zomwe wafuna vuto lanu nchani 🎉

  • @victoriamkandawire5469
    @victoriamkandawire5469 หลายเดือนก่อน +3

    Mind ur own business

  • @JackMlenga-j2t
    @JackMlenga-j2t หลายเดือนก่อน

    Musiyen miracle ndizofuna zakeka and mzabanja rake eeee km akuru ngat mukumufunas bwaa😅😅😅

  • @susanetaharrison7014
    @susanetaharrison7014 5 วันที่ผ่านมา

    Hall Joseph Clark Shirley Garcia Steven

  • @PhynessIshmael
    @PhynessIshmael 5 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤ komadeee asiyeni amenewa😮😮😮

  • @andrewkalima
    @andrewkalima 4 หลายเดือนก่อน +1

    Nobody is commenting on your side,sutha kulongosolanso nkhani,chilomwe chinakuthyolanso lilime lako ngakhale ndine mlomwe koma iwe waonjeza

  • @user-qc7fz1tk8q
    @user-qc7fz1tk8q 5 หลายเดือนก่อน +1

    tisakusiye wekha cholinga nafe tikhale amabodza ngati iwe

  • @CholapitsaSamson
    @CholapitsaSamson 5 หลายเดือนก่อน +1

    Zachamba ungodithera bundle mbuzi iwe

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 5 หลายเดือนก่อน +2

    Mwatelo et 😮😮

    • @brandinaphiri4728
      @brandinaphiri4728 5 หลายเดือนก่อน

      mwasowa zochita eyatu kodi zetu amanena ndani motimuzi paga ndalama zazi

    • @KhobasMaseko-yl2nw
      @KhobasMaseko-yl2nw 5 หลายเดือนก่อน

      waboza iwe galu

  • @noahtsamdoka1172
    @noahtsamdoka1172 5 หลายเดือนก่อน

    Koma mkuluwe school yomwe udapita ndikuti ndifuna ndikapase chibalo aphunzitsi ako l hope amakuchongela zolakwika or else umangolumphira ma class mbali yomwe wasankhayi si utolankhani tittle ndi story kusiyana stop nthano zakozi or ali ana kumazati padangokhala tilitonse avomela koyamba kwinako padangokhala no oyankha azangogona bax😊😊

  • @user-ei2yt3kf4x
    @user-ei2yt3kf4x 5 หลายเดือนก่อน +1

    Aliyese ndi ochimwa

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z 5 หลายเดือนก่อน +1

    Mutu wabkhani yanui ndizimene mukufotonoza sizikugwilizana ndipo lalibepo chimene tatolapo coz fundo zanu is fundoless

  • @MrMwambananji-tx8jt
    @MrMwambananji-tx8jt 5 หลายเดือนก่อน

    Kodi supeza nkhani zenizeni zoti ungafotokoze, imeneyo ndi nkhani?

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl 5 หลายเดือนก่อน

    prz Inu a hit mudzibweletsa nkhani zakupya musamabweletse nkhani zilizose plz

  • @MoyendaShumba
    @MoyendaShumba 27 วันที่ผ่านมา

    Kuyankhula nkhani za anzanu mumakonda ndinu mwaononga malawi inu ndi zaboza musaike muma midiya zinthu za anzanu ululani zanu ambuye akukhululukileni

  • @JaneMasikini
    @JaneMasikini 5 หลายเดือนก่อน +1

    Wasowa nkhani kape iwe ukulepheraso kuyankhula mmwxii

  • @monicatambala5615
    @monicatambala5615 5 หลายเดือนก่อน +1

    Bwanji muzikalima

  • @GraceMuvela
    @GraceMuvela 4 หลายเดือนก่อน

    Ngat amapanga uhule miracle amalekelanji kunena nthaw yonseyi
    Nosense tilibe nazo ntchito
    Azngopanga zake mamunayo ngt nd wanzeru,,,nosense🤧
    Miracle chinga,,u have to put up your socks show them🔥
    Tili kumbali yako

  • @katenyalayanayla2040
    @katenyalayanayla2040 หลายเดือนก่อน +1

    Zaziiii🤧🤧🤧🤧😂😂😂🤣

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op 5 หลายเดือนก่อน

    Mungotumiza zina osati zamabanja la adzanu please muzanu zake zikuyenda kuma inu zakambakamba ayi moyo umenewo siyani

  • @VictoriaHauli
    @VictoriaHauli 5 หลายเดือนก่อน +1

    Mpakana kufufuza mulibe zochita eti? Anzanu akusaka ndalama Inu muli busy kufufuza za ziiiii

  • @DorothyTamanga
    @DorothyTamanga 5 หลายเดือนก่อน

    Inu kagweleni ... Uhule amapanga amanu.. simunabwelese umbon bwa zaziii

  • @user-vg5wi9ww3p
    @user-vg5wi9ww3p 5 หลายเดือนก่อน

    Muzasiya liti kupanga zazanu ndiye mene mwachiziwa mwapindula chani

  • @AlnordMussa-p6b
    @AlnordMussa-p6b 18 วันที่ผ่านมา

    Inuyo chikukhudzani mchayani Kubanja la eni ake...zilimani man kkkkkk

  • @user-qg8ze3ru9b
    @user-qg8ze3ru9b 3 หลายเดือนก่อน +1

    Athuvena ngoipa mumalimbana naye chani miracle paganism zanu musiyeni

  • @user-ql8tv7wy2w
    @user-ql8tv7wy2w 5 หลายเดือนก่อน +1

    Come to the point. U don't know what u r saying. Waste of our time

  • @Jofra-pu7sm
    @Jofra-pu7sm หลายเดือนก่อน

    I don't understand Kodi ena akupanga uhulewo ndeno zikukhudzana bwanji ndi miracle wathu oimbayu guys khalan srs dzina la uhule mwalitenga kuti

  • @ModesterCheckcheck
    @ModesterCheckcheck 16 วันที่ผ่านมา

    Pangani zanu zoti zikuthandizeni

  • @lysonchipeya
    @lysonchipeya 5 หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaa akufotokozeleni Ngati ndani inuyo komwe ankafusilana anakuuzani a Pena gyz mumafalitsa zopusa ndisaname ayi

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 5 หลายเดือนก่อน

    Unamva kuti zoti court imathetsa kapena kumanga banja?😂😂😂😂😂

  • @RachelSiyani
    @RachelSiyani 4 หลายเดือนก่อน

    Mmakamba zaziii pedzan china chochita mukaphunzirenso kuwerenga zomveks bwino ,mulibe uiles

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 5 หลายเดือนก่อน

    Inunso ndiye mumangotiyisa anthu nthawi,ndangozindikira ndatsekula zazii izi mmmm my data

  • @user-mw8hr5fk2o
    @user-mw8hr5fk2o 5 หลายเดือนก่อน

    Iwe ndigaru kobas sumatha kupanga zako

  • @UpileChapita
    @UpileChapita 5 หลายเดือนก่อน +1

    Nde iweo chukhukhudza ndichani

  • @sophiebutao1758
    @sophiebutao1758 5 หลายเดือนก่อน

    Pezani zina zochita akulu 😂😂😂

  • @user-uf9us7xo5l
    @user-uf9us7xo5l 5 หลายเดือนก่อน

    Wachiziwa wekha nanga nanga apa ngat wafotokoza ngat ungoti mwakut mwakut kubisa zina umakamba mosabisa bwanji basi kutithela bundle zaziii

  • @GeorginaSAWAWA
    @GeorginaSAWAWA 4 หลายเดือนก่อน

    Nde mfundo yanu ndiyotan pamenepa?

  • @EvieZulukandulu-dz9bs
    @EvieZulukandulu-dz9bs 5 หลายเดือนก่อน

    Ndinu opusa kwambili miracle akumadya kwanu bwanji osapanga zanu apa uchitsilu ochita kuwowonekeratu uwu kupepela kwabwanji asiyeni asova okha awa ndima family issue kapena ndinu ankhoswe?
    Manyi

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di 5 หลายเดือนก่อน

    Munthu ungangochoka uko opanda chifukwa nkumumenya munthu nanunso inu
    Chenicheni chuchitika pa awiriwo akudziwana awiriwo sitinachidziwebe.
    Mamuna nzanu mamtani kodi? Mumadana Naye kale?
    Nkhanza kwa zibambonso ziliko
    Mamunayo is a smart boy mukachitidwe kazinthu
    Uhule wa nkazi ali wanu mumgatani?

  • @AlinafeSolomoni
    @AlinafeSolomoni หลายเดือนก่อน

    Wamwayi ndiwa mwati miracle sadzashilinkatu

  • @user-fz9oy6qc6i
    @user-fz9oy6qc6i 16 วันที่ผ่านมา

    Koma abale palibe zina zochita źoti zikhoza kusitha mayowu kusiyana mkumakamba za athu omwe akufalitsa uthenga wabwino, inuyo mwachitapo chani chopindulila dziko la Malawi? Pangani zanu

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 5 หลายเดือนก่อน

    Nkhani za m'banja sakamba poyera. Ndipo inu mulibe nazo ntchito. Osamakamba za eni. Pangani zanu Achimwene

  • @KelvinmosesBanda
    @KelvinmosesBanda 5 หลายเดือนก่อน +1

    Y are you boring with pple's business za banja lao zisakukhuzeni

  • @FumbaausoMafen-zd6kg
    @FumbaausoMafen-zd6kg 5 หลายเดือนก่อน

    Amwene munthu wanzeru sangamavutike ndizawina mwatumidwa nanga zabanja lako

  • @NaomiMwanza-n1v
    @NaomiMwanza-n1v หลายเดือนก่อน

    Live the girl alone place are you not ashamed of yourself o don't you have anything to do y can't of yourself,she will find another gud man who respect her wait and watch

  • @GanizaniGraldoFanuel
    @GanizaniGraldoFanuel 5 หลายเดือนก่อน

    Waziwapo chanipamenepa ngatizikukanika kufotokoza

  • @Jofra-pu7sm
    @Jofra-pu7sm หลายเดือนก่อน

    Osakamba uhule wakazanu ndi abale anu bwanji mwamuna wa miracle yo ndiwopusa ngat amalemba zimenezo pa social media akhala choncho bolan asadzabwere kudzapepesa zikamuvuta kut abwererane banja likatha mudzitha kusunga mau kut mukamadzabwerera musadzachite manyaz

  • @denndavie6041
    @denndavie6041 5 หลายเดือนก่อน

    Kodi ulibe nkhani zoyenela kupeleka kuntundu wa A Malawi zomwe zingapindulile anthu.

  • @user-tb7zu6lr3s
    @user-tb7zu6lr3s 5 หลายเดือนก่อน +1

    Mukunama

  • @user-xd2bs1td9r
    @user-xd2bs1td9r 5 หลายเดือนก่อน

    Iwe sudziwa zimene ykunena wava palibe cha nzeru chimene ukunena adakulenba ntchitoyi akuchinse wava

  • @IbraahPMenard
    @IbraahPMenard 5 หลายเดือนก่อน

    Zautsilu.bas menemwayambila munja kt mufoto kz zichani inu mwasowa sochita palib chomwe mukuziw

  • @bonwelllinyenga871
    @bonwelllinyenga871 5 หลายเดือนก่อน

    Anthu adzikhala busy ndi dzimenezi ndi abale ako 😮

  • @TrishBanda
    @TrishBanda 28 วันที่ผ่านมา

    Osapanga zako bwanj

  • @clementmahoka6287
    @clementmahoka6287 5 หลายเดือนก่อน

    Mbwerera zokhazokha palibe chanzeru ndatolapo, phunzirani kupanga zanu mkulu

  • @AgathaManda
    @AgathaManda หลายเดือนก่อน

    Ndiye za ihulezo zayamba bwanji zopanda sence

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 5 หลายเดือนก่อน

    Ziko ramarawi ndi rosauka chifukwa cha anthu ngat inu kutaya nthawi pazinthu zopanda phindu fuseki

  • @user-lj8ug5lq8c
    @user-lj8ug5lq8c 5 หลายเดือนก่อน

    Man mukutiuzazi mukufuna ife tikaziwa titani Mmene amafunsirana simunatiuze munalikuti?inu ndianthano man zongoyambira ntchito poti uncle amagwira komko kungolowa ndimutu

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od หลายเดือนก่อน

    Km zimene walemba apa ndi zomwe ukunena zosa gwilizanatu naweso chisilu iwe😂😂

  • @blessingbanda3369
    @blessingbanda3369 5 หลายเดือนก่อน

    Ndiwe mbuli ulibe nzeru,, galu iwe,, upeze zina zochita,, panyoopakoo,,

  • @JayKawereMw
    @JayKawereMw 5 หลายเดือนก่อน

    inu mumachulusa bonza kwambiri ndyeno inu munena bwanji kuti anapangayo uhule

  • @MariaAndrea-f9v
    @MariaAndrea-f9v 2 หลายเดือนก่อน

    Kodi mukupanga zammabanja yawanthu tsopano?

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 5 หลายเดือนก่อน

    Kod TV ya bwanji imeneyi yopanga za muthu ngt mwasowa khan osangoiseka zachamba bas

  • @lucymlendo7301
    @lucymlendo7301 5 หลายเดือนก่อน

    Nde ngati mwiniwake analephera kufotokoza pa social media iweyo mphanvu zimenezo ukuzitenga kuti zomalankhula za banja lamzako , uli ndi nthawi eti osakakweza kwacha ikugwayi bwanji

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 5 หลายเดือนก่อน

    Kodi mukuti chani kodi?komaso channel ichi nde manyakatu

  • @user-iv3xf7mf5p
    @user-iv3xf7mf5p 5 หลายเดือนก่อน

    Pezani zina zochita alekeni amzanu iiii

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 5 หลายเดือนก่อน

    Tchende lako mbabva osapanga zako bwanji amapangira uhule pako

  • @user-sl6fv7hc9f
    @user-sl6fv7hc9f 5 หลายเดือนก่อน

    Cholinga chako ndichani? Kazitape iwe

  • @AlinafeSolomoni
    @AlinafeSolomoni หลายเดือนก่อน

    Tsogolo lanu silaketu tayambani wafufudza vuto lanu umphawi wanu inu iyaa

  • @JailosFirston
    @JailosFirston 5 หลายเดือนก่อน

    Bro zolongosola zanu aaaa miracle saanafike potchuka mpaka mbili aaa km iwe

  • @user-yv1dq9bh2y
    @user-yv1dq9bh2y 16 วันที่ผ่านมา

    Do not judge

  • @AllessMoyo-uk4ke
    @AllessMoyo-uk4ke 5 หลายเดือนก่อน

    Zoonadi ndizayeni osalowerelapo amalawi ndichani chakuvutani banja silanu