Racheal Dumakude Watondeka Satana
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 10 ก.พ. 2025
- Satana walephera ndipo ndi olephera nthawi zonse.
Watondeka satana ndi nyimbo yachilimbikiso angakhale kuti oyipayo angakuphinje motani koma Mulungu amakhalabe mbali yako.
Ambuye akudaliseni pomwe mukumvera uthengawu.