GWEDEGWEDE LERO PA 27 AUGUST 2024 |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 42

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d 17 วันที่ผ่านมา +5

    Za zii mukufuna kubera zisankho zinachitikapo kuti kuyesera mavoti a zipani zotsutsa plz musalore tikudalira inuyo akukavoteltsatu ana aja awa plz abale azipani zotsutsa tamachangamukani Inu abale

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 15 วันที่ผ่านมา

    Zazii mukufuna kubera basi koma next year simukutenga boma akhaza inu mcp nonse chikangawa ndi manganya

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 17 วันที่ผ่านมา +1

    Khani imeneyo ndi yabwino kuno ku south Africa amachita zomwezo ineyo ndinagula botolo limodzi la 750ml ndinatuluka mu botolo sitolo ndi kuyamba kumwa ndinameza kamodzi akufika wa traffic anandiranda botolo namatsila pamsi ndinafusa bwanji wapanga zimenezi anati public drinking ukumwa mowa makiyi agalimoto ali m'manja,anapita nane ku police ,ndisankhe kukhala mundende kwa miyezi itatu kapena ndiripire ndalama yokwana R350:00 ndipo ndinalipira ndikunena izi sibwino kumwa mowa ukudziwa Kuti uyendetsa galimoto ayi tiyeni tivomeleze mwambo wa pamseu,moyowu ndi wathu ndikudziwa kuti ena ainu munditukwana ndi kundinyoza koma ineyo ndiribe nazo kanthu ndi makukondani basi.

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 16 วันที่ผ่านมา

    AKaliat makwana 🙏🙏🙏🫂🫂🫂💪💪💪💪💪

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 16 วันที่ผ่านมา

    chikangawa yomweyo kkkkk zavuta pamalawi mmm !!!! koma zobela mavotizo mno tizaphanapo amalawi chakwela ndimanganya ife c tikuwafuna apa tizalolela kufa za chamba basi

  • @EzekielWakudyanaye
    @EzekielWakudyanaye 16 วันที่ผ่านมา +1

    In Europe, people are fond of feasting: dining and wining. However, when we go out for wining and dining, we take taxis to the pubs and back home to avoid road accidents. This means that pub and restaurant owners and taxi drivers, will make profits, but the only loser is the one who takes alcohol….kkkkk

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 16 วันที่ผ่านมา

    Mmmm Steve musapusise anthu

  • @EmilyBanjachikwatula
    @EmilyBanjachikwatula 16 วันที่ผ่านมา

    Kodi bwanji apolice omwewo amayendetsa galimoto atakedzela tawaona ife ambilimbili.

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 9 วันที่ผ่านมา

    Khani yabwino

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 17 วันที่ผ่านมา +1

    Km kukhwimaku 😂😂😂😂😂 chikangawa bomalake likuchita zinthu ndithu 😂😂😂😂

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 17 วันที่ผ่านมา +1

    Usi ndiyemwe akupangisa kt mwoyo ya athu a utm axifa ,coz akufuna kugulisa chipan

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 16 วันที่ผ่านมา

    Kma abale anzanga tikangolora kt akalembera akaetsele makina amenewa tidziwe kt mavote sazaenda bwno cifukwa iyi ndi njira imodzi yomwe yakonzedwa pofuna kuzabela zisankho za nxt yr plz ndipemphe kwa omwe mungakwanitse kutsusa izi chonde tithandizeni omwe sitingathe kukafikitsa uthenga wathu koyenera kutero mabungwe osiyana siana omwe siaboma tithandizeni 🙏

  • @raphaelnamukhoyo1268
    @raphaelnamukhoyo1268 16 วันที่ผ่านมา

    Mwaziyambazi i don't think mukwanisa kuzimaliza

  • @AndrewChirombo
    @AndrewChirombo 17 วันที่ผ่านมา +1

    Mozipasanako mpata polankhula kuti tizinva nao

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 17 วันที่ผ่านมา +2

    Dziko la dramma

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 16 วันที่ผ่านมา

    Za machine ama votes 🗳 paunikileni palowa chinyengo pamenepo

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 16 วันที่ผ่านมา

    Ayi isathe chifukwa ikuteteza umoyo wa athu,ndipo mowa omwa paka kunja kuche mowa wanji

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 17 วันที่ผ่านมา

    Manganya mthera kuwiri,nzeru zake zofuna kupha UTM.angotenga chipani chake apange mgwirizano ndi MCP..asaphe nzeru za chilima.komanso NEC imupange recall sayenera kukhala President ameneyu.

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 17 วันที่ผ่านมา +1

    INU NDIZITSIRU KWAMBIRI,MWATUMIDWA NDITHU NDI MICHAEL USI KAPENA,NANGA TIZITI INU SIMUKUZDIWA KUTI ANTHU AMENE AKUMAVALA MAKAKA A UTM KUMISONKHANO YA MCP KAPENA KUKUYENDA MANGANYA AMAKHALA A MCP OMWE AJA ,AMANGOWAGULIRA MAKAKA A UTM CHOLINGA ATSOKONEZE OTSATIRA UTM

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 16 วันที่ผ่านมา

    Zakeyu akufuna kupha chipani Cha Utm

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 16 วันที่ผ่านมา

    Palibe kuyetselera mavote kulibe komwe anapangapp izi.

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 16 วันที่ผ่านมา

    Plz chikangawa lipot😢😢

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 17 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤

  • @vincentbarnes5872
    @vincentbarnes5872 16 วันที่ผ่านมา

    Ngati Secretary General ndi NEC yonse ya UTM yalengeza kuti yatuluka mumugwirizanu inuyo pomwe simukumveza ndi pati a Gwegwede? UTM is well mannered party. Ananena kuti popeza anatuluka mumugwirizano ndeye makaka a UTM asamavalidwe Ku misonkhano ya Boma very clear. Ngati Michael Usi sakuwawuza anthu chifukwa akufuna kukondaeresa Chakwera akulakwila ma lamulo a chipani. Koma ngati inuyo a Gwedegwede mukuti simukudziwa kuti which is which the you are also very wrong as same as Michael Usi. If he keeps on mocking the death of Dr Saulos Klaus Chilima by showing his stupidity then he will soon pay back as those who killed Dr Saulos Klaus Chilima

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 17 วันที่ผ่านมา

    Akunama osalora zoteserazo zinayamba zachitika kuti zoyesera zisankho munyatu simuzabera agalu inu

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 17 วันที่ผ่านมา

    achibuku amalimbikira kupeleka machine chifukwa chibuku ukalezera machine saona,koma ndibwino apitilire kugwira ntchito

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 17 วันที่ผ่านมา

    Inu osusa musayesere nawo

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 17 วันที่ผ่านมา

    achibuku amalimbikira kupeleka machine chifukwa chibuku ukalezera machine saona

  • @user-pf4iw1kw7x
    @user-pf4iw1kw7x 17 วันที่ผ่านมา

    Koma malo ena monga Malo a ku Misuku :Mwenitulo,Muchona,Mwangulukulu1,2,3Jonas,Tayali Mwambatata,Ngandana,Ngana,Makeye.,Mbande,Muwisi kophanda network.Ndekalembera akachita bea?

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 17 วันที่ผ่านมา +2

    Most ignorants citizen dint know that candle lighting is a very powerful ritual.....only few pple knows whats going on

    • @sweeneykamwendo6251
      @sweeneykamwendo6251 17 วันที่ผ่านมา

      Candle lighting is very powerful ngakhale mfiti sangamake

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 15 วันที่ผ่านมา

      Exactly. These politicians know what they’re doing. I’m talking of the oppositions and the ones who are in power

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 17 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkk degreeless, 😂

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 17 วันที่ผ่านมา

    Ife amene timakonda utm ndidatuluka mugwidzano mcp idapanga convention adavotela Chakwera nanga bwanji akukakamisa utm kuti alinawo limodzi chifukwa chani poti iwo adapha mtsogoleli wa utm chilima amaganidza zoti mwina angachiwine chipani cha utm chikhale chawo wauphonda inu mcp pitilidzani chipani chanu musiye utm yokha tsimudapange dzabwino amcp pomupha chilima midapanga big mistake anthu adadzindikila pano dziko lidachangamuka anthu umaganidza ngati malawi wakamudzu ndipo mudanena kuti achewa ndinu ochuluka kwambili bwanji ukukakamila chipani changoni chisiyeni chipani chagoni tiwone ngati achewa odzindikira angakuvotereni manyi anu mukuphangawa dziko zithu kudula njala ndimeneyi chimanga chikudula chifukwa chani fetereza kudula inu ukuganidza mtengo wafetereza or abambo anu chakwera angakweninze kugula PA tango umene ndalama ikuvuta maphedzedwe ntchito kulibe ukungoba ndalama dzaboma tidakuvotela ndi ife km mwalemba mwana wanu kukhala oyang'anila ku immigration kd adalikuti 2019 pamene chilima kalimbikila campaign lero mwayamba kulemba ntchito anthu akubanja kwanu musidya limodzi uziba limodzi

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 17 วันที่ผ่านมา

    Mumatha makolo. Koma chawezi Banda mutichotsere ku Mibawako. Akutisokonezera wailesi yathu. Ngati iye ali m'meneri wa Chipani bwanji sanakapikitsane nawo ku convention kuja?

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere 16 วันที่ผ่านมา

      Akufunika apite Ku MBC ameneuja anzake a MCP alikumeneko

  • @AndreaBotoman
    @AndreaBotoman 17 วันที่ผ่านมา

    Inu mmakwana 😂😂

  • @AmosTembo-d9j
    @AmosTembo-d9j 17 วันที่ผ่านมา +1

    Bokosi 😂😂😂😂😂😂

  • @user-zo5zx2pu5n
    @user-zo5zx2pu5n 16 วันที่ผ่านมา

    Shame in you People of amalawi.kodi mukathandizira kuberako mukukhala mukupuza ndani?
    Kodi nanga mavutowa inuyo sakukukukuzani ?or chisoni mulibe kodi?
    Mulungu alinako kuthekera kwakupanga chirichknse chosakhala bwino kubwera poyera .
    Musamailetu kuti padziko pano sikwathu ndikungoothera dzuwaaa. Musakomendwe kopitilira.zikomo

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 16 วันที่ผ่านมา

    Mmmm Steve musapusise anthu