Episode 12 my clean crush l Kwacha devaluation, who cheats more in a relationship?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 61

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 11 หลายเดือนก่อน +3

    This conversation is good komano mada and Linda musamachite makani kwambiri,try kudekha nzanu alankhule amalize kaye,kenako muziyankha

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmh azimai masiku ano aopsa azimai akufuna ndlama kwambiri dzibwenzi 4muntju mmodzi ndiye akuti kuli ma MG2🙌🏻 ayi Zikomo

  • @PeterChilombo-ou2cd
    @PeterChilombo-ou2cd 5 หลายเดือนก่อน +2

    ndizoona mahule okwatiwa otiali ndiazimuna ao alipo inuyo simunazione kkk

  • @daudmasikam
    @daudmasikam 11 หลายเดือนก่อน

    I love you my 2 sisters mada and linda big 👆

  • @LodrickJamitoni
    @LodrickJamitoni 5 หลายเดือนก่อน

    I can say that now there is a lot of cheating but I agree with him, Milliyam Azimai is the most vulnerable.❤

  • @BlessingsMpezenji
    @BlessingsMpezenji 9 หลายเดือนก่อน +1

    Linda ndi Mada, amuna odziletsa alipo ndithu ambili, amene amakhutitsidwa ndi mkazi mmodzu

  • @AlinafepiliraniMbale-md8en
    @AlinafepiliraniMbale-md8en 11 หลายเดือนก่อน

    Mada and Linda Bwerani Mbali zakuno nzakuonetseni wangayu satchita nawo.

  • @andrewchiyembekezadimba7173
    @andrewchiyembekezadimba7173 2 หลายเดือนก่อน

    Ndakumva nawo chisoni atsikanawa promoting abortion. I did not expect them saying this if indeed are the cathedral saints.... Zomvetsa chisoni ndithu

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 5 หลายเดือนก่อน

    Ndipo azimbo abwino alio example ndi wanga❤❤❤

  • @MemoryLester
    @MemoryLester 5 หลายเดือนก่อน

    Am with u sisters it's better to be single kusiyana ndikumasamala munthu moti sasamala zaiwe

  • @giftngombeyakuyera8703
    @giftngombeyakuyera8703 16 วันที่ผ่านมา

    But somebody criticizing women on plenary wapalamula.

  • @AsimenyeMweneungu
    @AsimenyeMweneungu 3 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂 eee koma guy's mumatha

  • @IbrahimShaibu-p4o
    @IbrahimShaibu-p4o 5 หลายเดือนก่อน

    Mada and linda try to calm down when someone is talking
    And palibe chimodzi chomwe mumadziwa chukhuza banja akunena zoona malliam kuti mukwatile koma chimene ndingakuuze its not all man are shirting and nkazi ndimunthu oyipa one tou will reglet what malliam was light

  • @ModesterCheckcheck
    @ModesterCheckcheck 2 หลายเดือนก่อน

    Millium anemu mesa❤

  • @jackiendlovu9564
    @jackiendlovu9564 4 หลายเดือนก่อน

    Atsikana inu chomwe munhadziwe ndizakuti nkazi ndiopolila komanso amavomeleza momwe mwamuna wake alili , ndipo amakhazikika pamenepo ndipo amapanga ntchiti akamuone mwamunayo zomwe akupanga komanso nzomai samapanga ntchiti the time amamuonetsetsa kaye akatopa nzimai ndipamene amapangano ntchiti nzomai good day

  • @LuciaJames-xh3ms
    @LuciaJames-xh3ms 2 หลายเดือนก่อน

    Aunt maliamu inuyo ndi wachiyawo mutumwanu mayenda zamuna ndiye mukuwona ngati zimai aliyese anabadwa ziwanda zokonda anunazo ai sitose

  • @LameckManuel-h7e
    @LameckManuel-h7e 11 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂 ine ndilipo ndili ndi mkaz modz

    • @MadaLindacomedy
      @MadaLindacomedy  11 หลายเดือนก่อน

      Zopanda umboni zimenezo

  • @yohanekipandula5197
    @yohanekipandula5197 หลายเดือนก่อน

    Mada mwakula kwatiwani

  • @LuciaJames-xh3ms
    @LuciaJames-xh3ms 2 หลายเดือนก่อน

    Omwe akuwonjeza ndi azibambo amaliamu sakhara ndimahule

  • @JamesMalango
    @JamesMalango 11 หลายเดือนก่อน +1

    To be honest Mariam akunena zoona

  • @ConeriasPhiri
    @ConeriasPhiri 6 หลายเดือนก่อน +1

    Kulibe mamuna amene Ali okhulupilika

    • @hardworkkayuza6353
      @hardworkkayuza6353 5 หลายเดือนก่อน

      Ndpo kwambili,,azimai akakwatila anakhutisidwa😘😘

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa 11 หลายเดือนก่อน +1

    Kutaya mimba ndikupha dziwani kuti umoyo wachinthu umayamba pamene wadzindikila kuti uli ndi mimba tsono mumapha munthu yemwe wayamba ulendo. wamoyo.

  • @StanleyStanley-x5p
    @StanleyStanley-x5p 11 หลายเดือนก่อน

    Tianato sitidziwa kanthu😅😅😅😅

  • @LeviMalanda
    @LeviMalanda 3 หลายเดือนก่อน

    Koma azibambo ali pa top kunama😂

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 11 หลายเดือนก่อน

    Tili munyengo yasakhulupirirana😂😂

    • @MadaLindacomedy
      @MadaLindacomedy  11 หลายเดือนก่อน

      Umukhulupilire mwana wa ndani? 😂😂

  • @GiftMwaleGreaSaidi-i4q
    @GiftMwaleGreaSaidi-i4q 7 หลายเดือนก่อน

    Kkkk mumakwana

  • @StanleyStanley-x5p
    @StanleyStanley-x5p 11 หลายเดือนก่อน

    Nkhaniyo si sayizi yawo😮😮😮😮

  • @PillassDaula
    @PillassDaula 11 หลายเดือนก่อน

    Akazi amapanga shirt mowonjeza

  • @marygoza1205
    @marygoza1205 11 หลายเดือนก่อน

    Ine amuna anga sapanga cheat ndati ndisutse zoti palibe amuna osapanga cheat 😂😂

    • @MadaLindacomedy
      @MadaLindacomedy  11 หลายเดือนก่อน

      Mulibe umboni iyaa 😂😂😂

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 11 หลายเดือนก่อน

    Mada umakwana🎉🎉

  • @yamikanimkanthama4354
    @yamikanimkanthama4354 5 หลายเดือนก่อน

    Azmay or mwalusa koma mwachepa

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 11 หลายเดือนก่อน

    Mada, mada ndi Linda mukunena zoona

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 หลายเดือนก่อน

    Mmmmm 1:03

  • @SangwaniNkosi
    @SangwaniNkosi 2 หลายเดือนก่อน

    Azibambo ndi amene Ali pa top

  • @WilsonMwale-yu4js
    @WilsonMwale-yu4js 10 หลายเดือนก่อน

    Inu ndiaboza Gati popo akugonana ndi Amina azake posana pawo

  • @FatimaKananji-kz6yx
    @FatimaKananji-kz6yx 5 หลายเดือนก่อน

    aliyese pauwili wawo wose alipabanja akuzembela nkazi wake musamanene kt akazi uwule akupanga nkasi nimamuna eyetu

  • @MussahHassan-pj7il
    @MussahHassan-pj7il 5 หลายเดือนก่อน

    Umeneo nde uhule kulimbikisa kutamimba anthu

  • @bornface4786
    @bornface4786 5 หลายเดือนก่อน

    Alipo azibambo okhulupirika ndithu and ine ndi m,modzi wa iwo

  • @louisgolden
    @louisgolden 11 หลายเดือนก่อน

    Azibambo samapanga zinyengo Ngati nkazi akukanika mnyumba

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa 11 หลายเดือนก่อน

    Mukunamizana azibambo alipo okhulupilika

    • @MadaLindacomedy
      @MadaLindacomedy  11 หลายเดือนก่อน

      Mubweleseni poyera timuwone

  • @FatimaKananji-kz6yx
    @FatimaKananji-kz6yx 5 หลายเดือนก่อน

    amarriam uwule nditima muone

  • @matembanevermind-po3me
    @matembanevermind-po3me 11 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 5 หลายเดือนก่อน

    Pa nyini panu nonse

  • @louisgolden
    @louisgolden 11 หลายเดือนก่อน

    Azi bambo tilipo ambiri wokhulupilika

  • @robertsitifano9021
    @robertsitifano9021 4 หลายเดือนก่อน

    Winayo sapato zili kuti?

  • @LloydMkandawile-c9p
    @LloydMkandawile-c9p 11 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa 11 หลายเดือนก่อน

    Inu mukukambilana. 17:09 zimene muli mubanja?