You condemned the Lilongwe fracas against opposition and today you are celebrating the fracas against government, as an activist you could have condemned this as well, an activist should be in the side of honest regardless of political side otherwise you are positioning yourself as an opposition activist.......self destruction.........
Kkkkkkk koma Bon aaaa you're a real DC
Osatukwana apaa zisawawe,,,, nkhonya yobwezela kuwawa ,,,,,,ili tiligawanapo ndithuuu ndilande woyeeee
Ndilande woyeeee...tikumdikilira Chakwera yo azanya manyi kuno asazaelekeze kubwerai
Ziliboh 😂😂😂😂😂😂
Congratulations anyamata andilande 😊
Koma ine ichii😂😂😂
😂😂😂😂😂 Artist koma Winiko
Congrats ndilande boys
Ewe ndiye ndichisililu umaumba anthu kukhala opusa ulibe ma evitesi tingothokoza uchisilu wakowo
VN iyi inafunika ya live tione momwe akalindo akondwelera😂😂
😂😂😂😂😂Koma polani moto akulu
Awiniko mwayamba kuonetsa mawanga anu poyera tsopano kuti ndinu a DPP…..umanenadi zoona kuti 2024 tiona zinthu 😅
Booooooooooon kalindoooooooooooo the DCCCCCCCC CCC Wawa kwathu ku ndirande
Kungosonyezelat kut Bon kalindo ndichitsilu chamunthu zomwezo zikachitika ku Lilongwe mukumadzudzula koma zikachitika ku BT mukumachemelela chimwemwe tsaya inuyotu ingokhalan pheeee muwone zimene zichitike kulilongwe
Asachemelere bwanji, ku Lilongwe zachitika kangati zimenez?? Anamangidwap ndani n boma linapangap chani??? Anthu atopa mavuto mmene alilimu anthu kuchezera pamzere wamafuta nde iwo azitumbwa mkumayendayenda olo akanangomupheratu amalankhula motumbwa ameneuja
@@MzadziWangaowooh inu amenewo zoyankhula zokuyenerani ndithu zimenezi??
Ndilande si ghetto wamba😂😂🙌
Ati umayankhulira amalawi, amalawi ake ati,vuto losaphunzira school inakukanika mpake ulupanga zaukape, anzako onse sukuwawona koma basi, mbalame yamunthu musamatinamize
Inu tapitan kae ku school mkaphunzire kulemba chichewa choveka zandale mzakuluakulu tazisiyen
Uphuzilanu ND mul pat pano kkkkk
Akunkuyu achotcha 😂😂😂😂😂
Ndayamba tsiku ndikuseka the Dc
kuno sitifuna zopusa za MCP
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kholo linayambisa ana atengera....
🤡🤡🤡
Boma ligulasot oyimba a Bon Kalindo 😂😂😂😂😂😂
Boni kalindo ndi chisilu kwabasi uku ndiye timati kuchemelela zoyipa chisilu chamunthu
Ndichitsirutu uyuyu sianthu amenyera ufulu anthu awa never, kod kundilande kulibe anthu a MCP? So y akusekerera zopusa like this
Kukabewa mukulu wa mec nrb wadowado amewa aone uyo uyo kuphatokiza ndi mutsogoleri wawo
Koma chakwera ofunika a were ku ndirande azachoka opanda panti😂😂😂
Ndinadziwa 😂😂
Zili bwino kwambiri
Kkkkkkk
The DC mwasangalalatu kkkkkk
Koma uyu
😂😂😂😂😂😂
Zonsezi athu anakwiya ndizimene anapanga ku Lilongwe anakhapa athu kunotso sitikusekelera
😂😂😂😂😂😂😂
More fire Bon kalindo
You condemned the Lilongwe fracas against opposition and today you are celebrating the fracas against government, as an activist you could have condemned this as well, an activist should be in the side of honest regardless of political side otherwise you are positioning yourself as an opposition activist.......self destruction.........
It does make no sense
Linayambitsa ndi Kholo nde ana anatengere.....😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 we also have government activist so u can just ask Ben longwe n munlo to condemn
Choka iwe
Chizungu cha ziiiiiiiiiiiiiiiiiii
Uziwayankhulila agogo ako
Ndani angawamvele chisoni okubawo akanaphedwa kumene
😂😂😂😂😂 zikwanje zija zinalibwino? Kagwele ukooo
Born karindo machende ako wamva
Iwenso akowo
@CharlesChakwiya yakunyung'unyatu mbatata iwe kkkkkk unya uchi kamba iwe
@@PrinceTMzundamumva naye kuwawa uyu ndipo simunati
@MauriceMukona paribeee ndi mwana karindo wakoyo kutari muuzane kumeneko, pamtumbo panu nonse ndi iyeyo
@@PrinceTMzunda zako zimenezo zidyani zitezezo
😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂