KWATULUKA NKHANI YACHISISI YOMWE ILI MU KALATA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 31

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w 5 หลายเดือนก่อน +5

    Ndeno ndalamazo zipita kt afuna kuthila mthumba mwake chakwerayo

  • @IbraheemclassickmahmoodIbrahee
    @IbraheemclassickmahmoodIbrahee 5 หลายเดือนก่อน +1

    Kuchosa ndalama zimenezo potengera ndi mmene dziko lilili,palibe vuto chifukwa chonena kuti ma MP amalandila ndalama zochuluka ndi kale, zomwe zikuoneka kuti akulandila ndalama pa ntchito zomwe akugwira

  • @user-qe2lz7mx7u
    @user-qe2lz7mx7u 5 หลายเดือนก่อน +1

    Ndichifukwa amangotukwanako akafika ku parliament osaganizilanso za wanthu chikhalilenicho akudziwa kuti ndilandilapo kawiri bingu ananena kale izi maphungu ambili Ali ndi ulesi mudera lawo chifukwa cha maalawasiwo Kodi iwowa angadwale bwanji pomwe Ali ndi ma self doctor fotseki

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w 5 หลายเดือนก่อน +2

    Very good chilima ❤

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 5 หลายเดือนก่อน

    komatu akuluakulu inu andale musamaeonengati dzikoli ndiyanu nokha ayi panopa tikufunano adzunguno abwelele adzatilamulile mwina dziyenda aguinu tatopananu kwabasi kumalawi ko ife tatopa ndalama mudzingonya nokha koma kumamidzi mumayenda ana amayi amangokhala ngati amitsala ganidzani bwina akulua akulu

  • @user-qv4ko6ps4j
    @user-qv4ko6ps4j 5 หลายเดือนก่อน +3

    Nkhaniyo ndiyonadi ndipo zitheke kuti ndalama zizigwila ntchito zoyenela mchitukuko cha dziko,,,,,
    Mp akukatsegulila bridge ku dela lake ndie asainile allowance ndipo mwexi ukatha alandilenso salary.
    Kodi ntchito ya MP ndi yanji?
    Ngati ntchitoyo akukagwilila ku dziko lina apo mpomvekadi kusainila allowance koma osati adzilandila allowance chonsecho MP akugwila ntchito mdziko lake lomwe iye adasangalatsidwa kutumikila mnzika zake ndie please cancel allowance for MPs

    • @abdulrafiquekalembo469
      @abdulrafiquekalembo469 5 หลายเดือนก่อน

      Nanunso inuu.kodi munabadwira mwa munthu koma.Kodi ndalama yo akayambe kuchita save pano aMCP atabaiba ndalama yochuluka??? Ndiye pano azikaoneka ngati ndi anzeru po saver ndalama podula ndalama ya aphungu.It will never change kuti dziko alikonze awa awononga kwakukulu

    • @user-qv4ko6ps4j
      @user-qv4ko6ps4j 5 หลายเดือนก่อน

      @abdulrafiquekalembo469 walankhula maganizo ako ndipo ndizoonadi potengela ndi mmene MCP yaonongela chuma cha dziko koma phunxilaso kulemekeza maganizo anxako osati za mwano zakozo ! Ukati mnabadwila kwa munthu kodi? Ndi njila inaso yotani yomwe munthu adaenela kubadwila kupatula kunyeredwa ndi ku nyini?

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili หลายเดือนก่อน +2

    Kkkk

  • @user-jo3nz3gn6m
    @user-jo3nz3gn6m 5 หลายเดือนก่อน +1

    Wawa thawi izakwan

    • @user-jo3nz3gn6m
      @user-jo3nz3gn6m 5 หลายเดือนก่อน

      yasala pang'ono aona

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 5 หลายเดือนก่อน

    Ndichifukwa amadana naye chilima ndiopoira kwambiri .

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy 5 หลายเดือนก่อน

    Zimenezi akufuna kulanga otsutsa oonse ,poti akudziwa kuti omwe alim'bomawo adzidziwa mowapasila mwake allowances awo .
    Komanso zimenezi zachita link mwadala ndi cholinga choti nkhani ya passport tiyiwale kae

  • @IbraheemclassickmahmoodIbrahee
    @IbraheemclassickmahmoodIbrahee 5 หลายเดือนก่อน

    Company imatha kupungula ndalama kumene kwa ogwira ntchito awo if things are not oky,

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 5 หลายเดือนก่อน

    Kuchema

  • @lenzophiri
    @lenzophiri 5 หลายเดือนก่อน

    Akadwala munthu amapita ku chitala ndipo ndi ulere osati kugula aspirin

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkkkk

  • @KambewaKenikeni-bz2se
    @KambewaKenikeni-bz2se 5 หลายเดือนก่อน

    Watulusa report ndi chakwera ndi mcp kufuna kuipisa chilima

  • @user-og1nx7en7j
    @user-og1nx7en7j 5 หลายเดือนก่อน

    Following

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of หลายเดือนก่อน

    Abale khani izi ndizakalekale kodi khani zasowa?

  • @EvelynL.Chisale-co8zz
    @EvelynL.Chisale-co8zz 4 หลายเดือนก่อน

    Tilipano kukumvetselani tiona 2025

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z 5 หลายเดือนก่อน

    Ndalama olo zitatelo mesa mcp idzingodzitapabe. Zopoyiyila

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ru 5 หลายเดือนก่อน

    Nkhani yabwino imeneyo

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z 5 หลายเดือนก่อน

    Paja Ali target a mcp

  • @lusungumsiska2293
    @lusungumsiska2293 5 หลายเดือนก่อน

    Timva zambiri

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 5 หลายเดือนก่อน

    Iyaaaa zopeka chabe ndikuona choncho

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 5 หลายเดือนก่อน

    Achita bwino

  • @user-er7gm1ez3t
    @user-er7gm1ez3t 5 หลายเดือนก่อน

    mulibho ahot 265

  • @user-mq3nw3mb1d
    @user-mq3nw3mb1d 5 หลายเดือนก่อน

    Malawi yhaaa😂

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda หลายเดือนก่อน

    No mutu

  • @sibubrightcmasulanphiri3652
    @sibubrightcmasulanphiri3652 5 หลายเดือนก่อน

    Koma yaaaa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣