Limpopo moto weni weni wafika mu program ina zili umu ndi Mr Don’t Trust

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 63

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 2 หลายเดือนก่อน +3

    Koma manganya wakhumudwitsa athu sakuchita bwino ndipo ndimkamukonda ndimkaona ngati masewelo anha ndiwadzelu kani ndiwachabe Chomcho mm wampeleka nzake koma mmm ndiolotse ndikakutafune Ambuye atithandize ndithu

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 2 หลายเดือนก่อน +3

    Manganya ndi wa MCP umbon lowani ku FB kuli movie ya manganya act same like kamudzu banda this is a true

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 หลายเดือนก่อน +12

    manganya akuwona ngati angapusise anthu akunama imfa ya achilima manganya akuziwapo kathu chakwera ndi chigawenga

  • @JefreyMtambo
    @JefreyMtambo 2 หลายเดือนก่อน +4

    A Miko usi zomwe zimakukhalani ndi ma drama osati ndale mwalowa mbali yolakwika muyaluka😂😂😂😂

  • @moseschokani157
    @moseschokani157 2 หลายเดือนก่อน +3

    Zomwe zikuchikazi, ndikupanda Mzimu waumunthu komanso Kusowa chochita.. Kodi zinthuzi anganamizidwe ndindani ngati a Malawi sitikudziwa ayi ayi ,auponda Mr DJ don't trust.

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 หลายเดือนก่อน +5

    Manganya atumikila MCP APITILA limodzi ndi MCP yakoyo 2025

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 หลายเดือนก่อน

    Zimvere mumtolo manga we proud of you Limpopo guys

  • @ChristopherChakometsa
    @ChristopherChakometsa 2 หลายเดือนก่อน +2

    Misonkho yathu yomwe lero kumatikongoza mwauponda anthu adya zimenezo koma osabweza😂😂

  • @austenbushiri-cx1kh
    @austenbushiri-cx1kh 2 หลายเดือนก่อน +1

    Asiyeni nthawi yawo atipeza pompano nthawi nkachisilu

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน +7

    Komaso olo apileke ngongole panopa zaka zonsezi anali kutiko ndiye akuwona ngati angatipusinse ife mapwala ake manganya chisiru

  • @LamieTiger
    @LamieTiger 2 หลายเดือนก่อน +8

    Ndalama aba iba athu oipa asatana manganya naye aferazayen

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 2 หลายเดือนก่อน +2

    Bweresani ngongoreyo tikagulire chakudya njala bwana kuno

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 2 หลายเดือนก่อน +6

    Manganya ndi bambo a sikono tisaiwale pamepo. Ndipo ndi mthila kuwili kapena chidule chadzina nale ndi chikakha manyi chomatuluka thukuta koma chikukakha zonukha ndiye ndi manganya

    • @Shelifibraheem
      @Shelifibraheem 2 หลายเดือนก่อน +2

      Kungotengela khalidwe lake olo patakhala pasewelo emwa ama ima pa zaphindu ndi winiko. Kusonyeza awawa kaumuthu alibe koma kupusitsa ena basi.

  • @JosterNgalawa
    @JosterNgalawa 2 หลายเดือนก่อน +5

    Manganya ndi yemwe amamupereka chilima, koma mulungu simuthu mawa mawali ndi iweyo

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 หลายเดือนก่อน +4

    Manganya ndamene apeleka Chilima komaso ndi wa MCP.

  • @DickinsonLikhoma
    @DickinsonLikhoma 2 หลายเดือนก่อน +5

    Manganya ndi wa mcp kuyambila kale kale ndipo za chilima waphesa ndi iyeyi

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 หลายเดือนก่อน +1

    Awulutse maviyen anthu awuze okuphawo

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 หลายเดือนก่อน +3

    Ndi waku Zimbabwe ameneyu si mmalawi

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 หลายเดือนก่อน +7

    MCP you mast ❤

  • @WestonGawaza
    @WestonGawaza 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mwana akalakwa timamukwapula manganya ndi mwana ayenera kukwabulidwa ngati mwana

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya manganya manganya.Amalawi ochuluka akutuluka.akungokunamiza amenewo

    • @RManyau
      @RManyau 2 หลายเดือนก่อน

      manganya muthu oyipa ngati mutchimbuzi

  • @JosephMzumala
    @JosephMzumala 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya akuchita kuyamikila poyela ATI chakwela anampasa y VP manganya ndiwa MCP koma choti aziwe nduchakut kuli achina zikhale ng'omaa Abid Mia ambili mbiku akuufuna u vice president umenewo
    Atamuonese show ndi achina zikhale imwewo osat chakwela

  • @AlexHenere-r6l
    @AlexHenere-r6l 2 หลายเดือนก่อน +1

    Anthu9 ose anaphedwa osalakwa kuchikangawa ndipo amene amakaulaura zisisi zachilima ndiyemweyu Kwa chakwera izi ndi imfa zimene sizizaiwalika komaso Ife ovota sitingaiwale.komaso adziwe Kuti palibe wamyaya padzikolino nawoso alipaulendo adzafa Chuma ngakhale achikonde bwanji Koma Azachisiya

  • @rashidmtembo6045
    @rashidmtembo6045 2 หลายเดือนก่อน +1

    Limpopo ndimakusatani koma whatsapp line ndilibe, nane ndiziponyako maganizo anga plz.

  • @HolyNickMbewe
    @HolyNickMbewe 2 หลายเดือนก่อน

    Nsonda anabadwa Ali otuwa akukula Ali otuwa azafanso Ali otuwa ndimulomo wake wautali ngati sakhwi.

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน +3

    Koma manganya akuwona ngati angatinamize ife akunama iyeyo ndifiti yake ckwalelayo

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 2 หลายเดือนก่อน +6

    Manganya ndi wa Mcp! Koma sangatiuze china chilichose

    • @MilikaKilion-tn1bn
      @MilikaKilion-tn1bn 2 หลายเดือนก่อน

      Akeni sonda I think amwa mankhwala thawi yaitali ndiye mutu unasiya kugwila ntchito

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 2 หลายเดือนก่อน +1

      😂😂😂😂😅😅😅 akufunika akamusinthile mankwala 😅😅😅😅😅​@@MilikaKilion-tn1bn

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya ,,,why ? Sakuvala makaka a UTM fotseke ameneyo achoke muchipani cha UTM ,,, Kodi zomwe akupanga manganya sika mpeni bwanji asonda akudana ndi fedokisi Kuti asiye makendulo ,,zitsilu zawanthu Za MCP. ,,,manganya akabwela tawuni yakwanthu tidzangenda ayelekeze

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba 2 หลายเดือนก่อน +6

    Zoona zake

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 หลายเดือนก่อน +1

    Amanganya anthu akukuwelengani pang'opang'ono koma anthu akukusatirani kamba ka UTM mubwere poyera kuti ndi WA MCP muone zomwe tichite PA nchombo wako

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 หลายเดือนก่อน +1

    Za Ken Msonda whether wakula kaya watani akungofunika kulanga ndi makofi simple

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 2 หลายเดือนก่อน

      Zakukulako ziri apo athibulidwe basi ndi opisa

  • @HolyNickMbewe
    @HolyNickMbewe 2 หลายเดือนก่อน

    Bambo a Nick ndi Bambo a Sikono magazi a chirima ayamba kuwapengesa misala. Ayamba kusavuka .

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya angoyenda mwantendele ku mcp akamuphele konko

  • @HolyNickMbewe
    @HolyNickMbewe 2 หลายเดือนก่อน

    Bamboake a sikono ndi khwangwala ozola Ufa oyera kuti afanane ndi akakowa oyera kobadwanako . Koma powoloka pamazi azaziwika kuti bambo sikono ndi khwangwala.

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 2 หลายเดือนก่อน

    Limpopo umakwana

  • @NedGft
    @NedGft 2 หลายเดือนก่อน

    Manga akupanga kampen watumidwa zonse zomwe achita yankho ilipo 2025 ndipamene aziwe kut malawi walero siwathawi ya kamudzu tiwakhazika pansi 2025
    Mavotedwe aliyense akuyenela avote kugwirisa pepala iliyonse yochoka kwa amfumu

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 2 หลายเดือนก่อน +2

    Hello Don't trust. Big up

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 หลายเดือนก่อน +1

    Akupanga zachamba manganya

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Asapusitse amalawi kawiri akakupatsani ngongoleyo idyani ndalamayo ndipo musabweze chifukwa ndi misonkho yanu

  • @JefulyPesulo
    @JefulyPesulo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya alibe zelu

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน

    Manganya ndi galu wamuthu anachenjeletsa mopusa ine ndipo amandinyasa kwambili ndipo sitingavitele zitsilu zimenezi

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 2 หลายเดือนก่อน

    Manganganya ndiwa MCP patalike pafupike uyaluka manganya 2025 athu akumpha inu

  • @JamesDaud-jz7uq
    @JamesDaud-jz7uq 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya ndi joker,anachenjera mopusa akuona Ngati amalawi ndi opusa kuti atsatira maganizo ake, ndalama anthu apatseni komanso olo osabwenza palibe milandu potion AMAT wadya zake alibe milandu ndi ndalama zathu zija

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 2 หลายเดือนก่อน +1

    Program yowophya ku chipani cha chakwera osayisiya avesese

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 หลายเดือนก่อน

    Tikhoza kukamba kuti amakaoda akapeleke ku mwela akagawe kwa mtundu wa Malawi

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 หลายเดือนก่อน +2

    Manganya u mast go

  • @ChavukaGumbo
    @ChavukaGumbo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma ndiye galu osaka weniweni

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 2 หลายเดือนก่อน

    Ndi 1

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera wakugwirisa ntchito manganya
    Vuto chilima sanaziwe kuti manganya ndi udasi manganya si wa utm asatinamize manganya zeru walibe akuyendera zipatala koma mankhwala mulibe koma akugawa mhongole kwa anthu oti ali bwino alibe vuto koma kuzipatala kulibe mankhwala anthu akumwalira pali zeru panenepo. Ine ndikanakhala manganya ndikanamuwuza Chakwera kuti asiye kukongoza ndalama ndalama zo akagule mankhwala

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 2 หลายเดือนก่อน +3

    Usi Ndi munthu oipa kwambili

  • @FelixMwenifumbo-u8l
    @FelixMwenifumbo-u8l หลายเดือนก่อน

    .

  • @PatumaNgomwa
    @PatumaNgomwa 2 หลายเดือนก่อน

    Ndalamazo zidyedwe koma vote Ili mumtima

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p 2 หลายเดือนก่อน

    Athu oipa awa nasatana awamako mwandi

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 2 หลายเดือนก่อน +1

    Manganya manganya manganya.Amalawi ochuluka akutuluka.akungokunamiza amenewo