TIMES EXCLUSIVE WITH MIKE CHITENJE - 27 JULY 2019

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 4 ต.ค. 2024
  • In Times Exclusive this week, Brian Banda engages Mike Chitenje, a boxing promoter and business man on what his day-to-day activities include.

ความคิดเห็น • 32

  • @manzykawika8988
    @manzykawika8988 4 ปีที่แล้ว +1

    Mesa ndamva zoti Ngati adpp Sakupasa ndarama uwulula yomwe anapha njaunju bwanji ukubisa

  • @mrsbkamwendo1021
    @mrsbkamwendo1021 5 ปีที่แล้ว +1

    Keep up Brian ukamafunsa munthu suopa umafuna tidziwe chilungamo

  • @hajiwayison8748
    @hajiwayison8748 3 ปีที่แล้ว

    Mafuso abwino komaso ndithokoze bambo mike chitete n'mene akuyankhira mafuso komaso ndithokoze wires ya times pomatigawila nkhani zosiyana siyana GOD bless you brian banda with mike chitete good bye👍

    • @hajiwayison8748
      @hajiwayison8748 3 ปีที่แล้ว +1

      Because munthu akakhala ochuka zambiri zimakhala.zikumugwera kwayine ndikubalaka T/A kalembo koma ndasangalasidwa ndimene mafuso mwafusila komaso ndimene mike wayankhira🕋👍

  • @dezmondmanjolo9558
    @dezmondmanjolo9558 2 ปีที่แล้ว

    This interview was a bang

  • @frackisonlogah4165
    @frackisonlogah4165 5 ปีที่แล้ว +3

    Mr mbanda mukumanenso ndi black Moses

  • @williamsbanda9225
    @williamsbanda9225 5 ปีที่แล้ว +1

    Keep on Brian,ameneyu ndi wachiwebu wankulu ,king of Cardes,one day shall come,koma Ku Nsonkhano was DPP amakafuna chiyani

    • @greysonjake9998
      @greysonjake9998 3 ปีที่แล้ว

      You all probably dont care but does anybody know a trick to get back into an Instagram account..?
      I somehow lost the password. I love any tricks you can offer me

    • @elizion6748
      @elizion6748 3 ปีที่แล้ว

      @Greyson Jake instablaster =)

    • @greysonjake9998
      @greysonjake9998 3 ปีที่แล้ว

      @Eli Zion i really appreciate your reply. I found the site through google and Im waiting for the hacking stuff now.
      Takes quite some time so I will reply here later when my account password hopefully is recovered.

    • @greysonjake9998
      @greysonjake9998 3 ปีที่แล้ว

      @Eli Zion It worked and I finally got access to my account again. I'm so happy!
      Thanks so much you really help me out :D

    • @elizion6748
      @elizion6748 3 ปีที่แล้ว

      @Greyson Jake you are welcome :)

  • @frackisonlogah4165
    @frackisonlogah4165 5 ปีที่แล้ว +1

    Mr Briana musalimbane ndi uyu ndi cadet wa dpp kuti muve Zambili za imfa ya Robart mufunse black Moses akuuzani chulungamo

  • @denniskhalamba9655
    @denniskhalamba9655 5 ปีที่แล้ว +3

    King wa ma cadet uyu.

  • @vincentlamanmathebulamwana5697
    @vincentlamanmathebulamwana5697 5 ปีที่แล้ว

    Mr Brian ntayeni uyu koma mau amodzi kwa nkuluyu ndi awa kukula nthupi,kunyamula zitsulo sikuthandauza kuti ndinu odziwa kupha, mupite pa mirror mukaziyang'ane bhobho kuti mwina kukula nthupiko mwina mulinso ndi manso kumbuyo, koma ngati mulibe muzikhala ndi mantha coz minga ndi munthu tikachitenga chachikulu ndiye ndi munthuyo komatu minga imabaya munthu

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 4 ปีที่แล้ว

    Brian, interview iyi sinali level yako, kuyankhula ndi mphwepwa, ife timadziwa kuti Brian amayankhula ndi anthu oganiza, odziwa chimene akunena osati izi za ziiii.

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 2 ปีที่แล้ว

    He's cool man

  • @rossferg1987
    @rossferg1987 5 ปีที่แล้ว +1

    Wa cadet ameneyo

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 5 ปีที่แล้ว +1

    But do you really have peace mind ?????

  • @elliotdzekedzeke4130
    @elliotdzekedzeke4130 5 ปีที่แล้ว +1

    Wakuba samavomera kuti amaba olo atamenyedwa sanga ulula.... #Mkulakwa kunena choncho. @ Brian Banda. 🤣 🤣 🤣

  • @AlihIbrahim-w6n
    @AlihIbrahim-w6n 4 หลายเดือนก่อน

    Palibe anganvomele choyipa, koma chabwino aliyese amachithamangila,,,

  • @marynkhada3870
    @marynkhada3870 5 ปีที่แล้ว

    Mulungu akuona kumwambako ndipo angodikila nyengo,kunali Nachipant ali kuti,kunali Osama biniladen alikuti,inuso nthawi yatsala Pang'ono,Mulungu simunthu,Mukakhala muzidziwa kuti kumwambaku Mulungu akuona

  • @stevemwakisimba5986
    @stevemwakisimba5986 5 ปีที่แล้ว

    Maik mpwanga iwe ndi achitsiru mwanva?kuyanka kwa Sirius? Kkkkk mwakulatu!

  • @mrwh.mwalimumrwh.mwalimu4397
    @mrwh.mwalimumrwh.mwalimu4397 5 ปีที่แล้ว

    Brian ndi yemweyo ndi jomo wakwatopwa. amaziwona ngati madolo malawi muno koma Thawi izawafika

  • @angellahmunthali733
    @angellahmunthali733 5 ปีที่แล้ว +1

    Cadet uyu

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 5 ปีที่แล้ว +1

    But do you really have peace of mind ?????

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 5 ปีที่แล้ว

    Kkkkkkk inetu ndikumvatu kwa inuyo.🤣🤣🤣🤣🤣

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 3 ปีที่แล้ว

    Funso lililonse akuti ndikumva kwainu he is so wicked,40 day will come soon

  • @francismadeya1232
    @francismadeya1232 4 ปีที่แล้ว

    Hahahaha koma Brian kkkkkkkkk

  • @freedommvula1184
    @freedommvula1184 5 ปีที่แล้ว

    I are supper man of God