ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ngat amatida ifeso melanin 🤴
Trapppa🐐Koma ma dance a one leg up nde atisoo🤣🤣🤣
Sungandivetse 😂
uli ndi luso koma vuto u off and on in music industry🔥🔥🔥🔥🔥
School inampanikiza boi
EEEHH UYUU NDI DHOLO HEAVY GEE✔️✔️🎵🎵🎵
Nyimboyi ndachonga💯✅🔥
14 November, who's here for this Banger 🔥💪Dirty Flo ndi shasha kanayi, 🔥
Underated dawg . My favorite trap artist 🇲🇼
Hiphop ndyomwe madolo amanvera iyi hit dirt Flo ndichidolo
Iwe ndi shasha 💥🔥🔥
dirty ndi dolo kwambiri🔥🔥🔥
Ndwe dolo kwambil nd chifukwa Achina Gatta Ase amakupasa ulemu ndwe dolo wa trapp ku Malawi konsekuno, ✊
Dolo kwambiri uyu
New graduate in Town 🥰🥰🥰luso sosasungunura
The jump move kumapetoko 🔥✅📍✌🏿😂
Koma ka dance akoko 😂🙌
@@griffinskaonga5116 imeneyo tingoti dirty sunga dance move 😂😂📍
Bwana dirty, this is a vibe on point. Keep up
Wakwapula 🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇧🇴
Best Malawian hiphop song 2024
Ngati amatida nafeso melanin 🐐🔥🔥,dolo Ka 200
Uduro wako sitingawuvese🔥👏🙌
Dirty is back shasha kangapo Ngati umandida ifenso Melanin 🤫Trapp ,the tune is dope
Its about reciprocating the energy- the holla at you, you do the same. Kukufaka panja, nawe the same.. Osamakakamiza stuff. Cheteee.. This is dope man the only problem ndiyoti kakutha fast😢
dirty ndiwe gangster kawiri🔥🔥🔥🇲🇼💯 chi nyimbo Cha hard ichiii
💥💯Nyimbo koma iyi
Dirty-flow umatha.....koma wasowatu mphwanga🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ineso ndakuchonga🔥💪🔥🔥
Ngini ya sharp🔥
Abale okutha kuimba💯
Dolo kwambir ngat iyeyu palibe trap ili kwa abale🔥🔥🔥🔥🔥🔥
King of trap 🔥🔥 ngat amatida ife melanin
Singakwanise kupembeza fano 🔥🔥🔥 mwapha madala
Iwuyusotu ushasha wake unanyanya🔥
Madala ma bars okhao eeee
Amatha awa inu🔥🔥🔥🔥
My Breda dette.. umakwana 💥💯💥
Zima flow za Dirty 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Ndachonga kuikaso Good
Chinyimbo🔥🔥🔥
Leto ndikutembelera aliyense omutchula pop young Kut ndi up coming artist ''shabalakata'' walakkata 🔥🔥
Dette iwe🔥🔥🔥
Aise iyiyi ndiye ili pa repeat 🔥🔥
Dirty Flo deserve an award guys mmmmh🙌🏻🙌🏻🙌🏻top music
Alas mumakwana 🔥🔥🔥🔥🔥
mwana waluso uyu🔥
🔥🙌 malawi trap
Define Trap? This sounds like Kwaito of summin
@@panopa9694i was wondering too
Homeboi to de world...🔥Ife za P Diddy ai🙌⚠️
Ngati umatida ifeso melanin 🔥🔥🔥
Eeeh🔥🔥 Ku dancehall watimvesa kukoma 💥
Dirty tumudziwa ife nduyu. Big up.
1st time kunvela doloyi.. eeeh RESPECT ase umatha
bar after bar, Dirty osandizunguza ngt analog💯💥❤🔥🤟
Wapatsa kale// ndipatsaso ///❤️
💥💥💥💥💥💥Eeeeeee km adha
Afana awawa amathaa ndpo nyimbo zake.zosachititsa manyaz kumver kudziko laweni❤🔥
Ngamo 🔥🔥🔥👌💯
Mmmmm fana uyu ndiwoopya
Achimwene iyi mwaiswa 🔥
Uyu nde dirty tumuziwayo
Dolo Kwambiri...im here kachikenaso kachikenaso kachikenaso
big up bro #(dirty flo) mumaitiyimilira pa nkhani ya hiphop, more 🔥🔥🔥🔥
Uyu ndi dolo❤
Fire flames fuego! 🔥💯💪
I swear this song came in handy now this is music 🎉big up my gee
Dolo wamadolo 🔥
Sitikuchitaso kunyumwa kugawa bundle❤nyimbo aise
Izi ndi nyimbo abale 🔥 man
Wapatsa kale ndi mpatsans💯....
Pure Malawian talent 🇲🇼🔥
😢😢😢 kod Ada amatha chochi bwanji 🔥🙏🔥🔥
Pali chani apa? Dude is underrated uyuyu ndiwoposa kuthako 😂😂😂
dolo kwambr🔥🔥🔥🔥
Big up brother man 🔥🔥
Katakwe kwambiri 🫠🥳
Umatha iwe
Shasha wanga wabwelanso💪😀🔥🔥
Eeee dirty ndi machine mmh 🔥
Dolo kwambili ❤🔥
Ngati amatida ifeso Melanin bars 🔥
Dirty flow umatha anse big up bruh Malawian traper nde ndiweyo bruh
Mwabwera kuzakhala boys
Dollo fro🇲🇼🔥
Ase iweyo nd dolo 🔥 🔥
Ngt umatida ifeso Melanin🔥🚨
th-cam.com/video/B1Jr0rXWik8/w-d-xo.htmlsi=Msl5MWsd1IPgGKZK
Iweyo umatha adha 💪
Wakunga hit Dolo kwambri
Man mumatha kuimba❤
Ngat wandihalla ndikuhalla🔥🔥🐐
Ameneyo wamupha chifukwa sangabwenze
Mn mulipo 😊🎉
Ndaku hala 😁🔊🔊🎧🎧
Man fire mwapha Iyiy🔥🔥
Wandikumbutsa revolver tu❤
Our Dirty Flow coz we can’t compare 🔥🔥🔥🔥🔥
Wati sukudya tikumananso💥💯
Dirty uli mkati. 🔥🔥
Madala 🎉🔥🔥🔥
Ameneyo ndy wamupha bas
Koma ichiii💥💥💥💥
Shasha heavy🔥🔥
Nyc song eeeh 🔥🔥 lil GOAT continue my bruh
Mr Hit maker munabwela inuyo❤
ma punchline mbwe 🔥🔥
Music ndiyiyi🔥🔥🔥
Ngat ndaku mwesa Ndikumwesa
Ngat amatida ifeso melanin 🤴
Trapppa🐐Koma ma dance a one leg up nde atisoo🤣🤣🤣
Sungandivetse 😂
uli ndi luso koma vuto u off and on in music industry🔥🔥🔥🔥🔥
School inampanikiza boi
EEEHH UYUU NDI DHOLO HEAVY GEE✔️✔️🎵🎵🎵
Nyimboyi ndachonga💯✅🔥
14 November, who's here for this Banger 🔥💪Dirty Flo ndi shasha kanayi, 🔥
Underated dawg . My favorite trap artist 🇲🇼
Hiphop ndyomwe madolo amanvera iyi hit dirt Flo ndichidolo
Iwe ndi shasha 💥🔥🔥
dirty ndi dolo kwambiri🔥🔥🔥
Ndwe dolo kwambil nd chifukwa Achina Gatta Ase amakupasa ulemu ndwe dolo wa trapp ku Malawi konsekuno, ✊
Dolo kwambiri uyu
New graduate in Town 🥰🥰🥰luso sosasungunura
The jump move kumapetoko 🔥✅📍✌🏿😂
Koma ka dance akoko 😂🙌
@@griffinskaonga5116 imeneyo tingoti dirty sunga dance move 😂😂📍
Bwana dirty, this is a vibe on point. Keep up
Wakwapula 🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇧🇴
Best Malawian hiphop song 2024
Ngati amatida nafeso melanin 🐐🔥🔥,dolo Ka 200
Uduro wako sitingawuvese🔥👏🙌
Dirty is back shasha kangapo
Ngati umandida ifenso Melanin 🤫
Trapp ,the tune is dope
Its about reciprocating the energy- the holla at you, you do the same. Kukufaka panja, nawe the same.. Osamakakamiza stuff. Cheteee.. This is dope man the only problem ndiyoti kakutha fast😢
dirty ndiwe gangster kawiri🔥🔥🔥🇲🇼💯 chi nyimbo Cha hard ichiii
💥💯Nyimbo koma iyi
Dirty-flow umatha.....koma wasowatu mphwanga🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ineso ndakuchonga🔥💪🔥🔥
Ngini ya sharp🔥
Abale okutha kuimba💯
Dolo kwambir ngat iyeyu palibe trap ili kwa abale🔥🔥🔥🔥🔥🔥
King of trap 🔥🔥 ngat amatida ife melanin
Singakwanise kupembeza fano 🔥🔥🔥 mwapha madala
Iwuyusotu ushasha wake unanyanya🔥
Madala ma bars okhao eeee
Amatha awa inu🔥🔥🔥🔥
My Breda dette.. umakwana 💥💯💥
Zima flow za Dirty 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Ndachonga kuikaso Good
Chinyimbo🔥🔥🔥
Leto ndikutembelera aliyense omutchula pop young Kut ndi up coming artist ''shabalakata'' walakkata 🔥🔥
Dette iwe🔥🔥🔥
Aise iyiyi ndiye ili pa repeat 🔥🔥
Dirty Flo deserve an award guys mmmmh🙌🏻🙌🏻🙌🏻top music
Alas mumakwana 🔥🔥🔥🔥🔥
mwana waluso uyu🔥
🔥🙌 malawi trap
Define Trap? This sounds like Kwaito of summin
@@panopa9694i was wondering too
Homeboi to de world...🔥
Ife za P Diddy ai🙌⚠️
Ngati umatida ifeso melanin 🔥🔥🔥
Eeeh🔥🔥 Ku dancehall watimvesa kukoma 💥
Dirty tumudziwa ife nduyu. Big up.
1st time kunvela doloyi.. eeeh RESPECT ase umatha
bar after bar, Dirty osandizunguza ngt analog💯💥❤🔥🤟
Wapatsa kale// ndipatsaso ///
❤️