Kodi ine ndimati ndifuse nawo Bingu anapanga chani choposa Dr Bakili muluzi ine ndakulira ku malawi ku Lilo gwe mpaka pano sinditha kuona chitukuko chomwe anapanga Bingu wamunthalika kupatula Parliament building,kukozaso Manda a Kamuzu ndi Bic ndi presidential villa komaso zosezi zinali maso mphenya a muluzi ndi UDF xinachitikaso mu 5 yrs yomwe iyeyu anathawitsa kupita nalo ku DPP koma muzaka zake za 5 yrs term yomwe anasakhidwa ngati wa dpp palibepo or chimodzi chomwe anapanga apart from kuzuza a Malawi kupha opanga ma demo okwana 21 komaso kumanga aliyese otsutsana Naye kuzima Kwa magetsi dairy,kusowa Kwa mafuta tinadziwira Kwa iyeyo sugar kumafola pa mzere makani matama kufikilira kudana ndi Mozambique Zambia Tanzania kumauza masapota azitimenya tikalakhula,osamayelekeza Dr muluzi or Dr Kamuzu Banda even Joice Banda was good mu 2yrs anamanga Bingu stadium kumangira Anthu manyumba osaika Dr Banda or anali wa nkhaza zonse zabwinobwinozi anapanga ndi iyeyo chilichose cholimba anapanga ndi Kamuzu Banda
Chilungamo ndichofunika pachikondi i like this song Kell umaitha keep it up
I feel this is one of the best collaborations in Malawi
kodi nyimbo iyi ndimaonela ndekha.... this deserves 1m views
team we here
Kell kay my favourite artist, you never disappoint
❤❤
❤❤❤❤ I love this song
This is the best of kell kay
I love this song
Nyimbo iyi Munagwetsa maguy
My favorite of all time ❤
❤❤❤❤❤🇬🇧
Beautiful song
n one here
❤❤❤ good ssog
Umatha big up song
❤
Zilibwino