Assalaam A'laykum warahmatullaahi wabarakaatuh Tati tikudziwitseni tikhala tisakuoneka kwa miyezi iwiri kapena mwezi umodz In Shaa Allah Tizakhala tikupitiriza pomwe tasiyirapa Allah akatifewesera Tipempha Allah atifewesere ndikutisunga ndimoyo wathanzi kuti tizakhale tikukumbutsananso uthenga wa Allah In shaa Allah
Masha Allah you are doing great job
Assalaam A'laykum warahmatullaahi wabarakaatuh
Tati tikudziwitseni tikhala tisakuoneka kwa miyezi iwiri kapena mwezi umodz In Shaa Allah
Tizakhala tikupitiriza pomwe tasiyirapa Allah akatifewesera
Tipempha Allah atifewesere ndikutisunga ndimoyo wathanzi kuti tizakhale tikukumbutsananso uthenga wa Allah In shaa Allah