😂😂😂😂😂😂 Wachiyao wangalusa The real GOAT chemandota n am feeling good with you....may the Allah still keep your safe n long live🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️
Kkkkkkk,,,,zoti amakupanga record iwe pamenepo iwe sukuona???🤣🤣🤣🤣 You're the best,,,inetu ndimapanga like video iliyonse even ndisanayionere ndimayamba kaye kuseka🤣🤣🤣
Che mandota is a abig deal, umatiyimilira continue entertaining us with your good comedies.
Me l want to know more about innobuld
I can't wait next week, bwanji mungotuluza m'mawa. bro mandota.
Eee Che mandota on fireeee 🔥🔥🔥🔥best comedian for sure
Kankhani finally azauzidwa zonse 🤣🤣 apapa akita akufa bas part 2
Koma Dr suspension si ya bho
But still keep it up...
Kkkkkk mandota kkkk 😋😋 paka kupephelela Mr your very best bro🤪🤪
Mumatiimilila inuyo eee I can't wait for part 2
Your my best che mandota
Mkazi wakakhani sikuti alola ayi koma foni anakatenga ija akupanga likodi kuti aveselese amuna ake kuti amuna ake azivele okha chifukwa kuti angolankhula Mr kankhani savomeneza akufuna azivele okha ndiye apangeno chiganizo ose
😃😄😄🙌🙌Mandota lweyo eee
Kom iyiyokha nde mwaswatu
Mwayesesa Mr mandota
Amachipanga record Icho chili busy kutsitsa mfundo 😂😂😂😆
Mandox 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mumakwana
Chemandota kom gys wayamba ukuluku Kom mamaili azanyanyale kadzi wa khankhan akukanani apa mix nchitho kuthe 👆🤣🤣🤣🤣🤣🤣🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Eee mandota iwe ukufuna kuthandiza mwa ulere kkkk machine iwe nkhope yakoyo ungasiye kulondola mwana
Hahaha koma ndaseka
che kankhani nde auswatu ulusi 🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂 Wachiyao wangalusa
The real GOAT chemandota n am feeling good with you....may the Allah still keep your safe n long live🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️
Big up mandoxy.....
buladi fulu shupiti shupiti amwene wayo chitaphwasi kwene😂😂😂😂😂 can't wait to see you the next chapter,ankana katondo kuntawa musanda kutila
Kkkkkkk,,,,zoti amakupanga record iwe pamenepo iwe sukuona???🤣🤣🤣🤣
You're the best,,,inetu ndimapanga like video iliyonse even ndisanayionere ndimayamba kaye kuseka🤣🤣🤣
Ndipo sungalephel kuseka che mandota kodi
xtra ordinary wabwera ngat coming
A kuti mafuto sudikira kuti munthu akuuze Koma umawona wekha..😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ……
inu number one in Malawi
Mandota umandiwaza hvy💥💥🐐
Fire 🔥 📛 👩🚒 umakwanila Doxcy.....
🤣🤣🤣🤣🤣pelekani basi solution chemandota fisi kkkkkkkk
Mandota ati sakufuma mawe oh Boyz never give up 🙌😜🤣
You're the best of comedian chemandota eishiiiii next week ikutalika ngat chaka
Koma asamale zomwe walankhula zili mu foni
Mandota iweyo fundo zako mmmm zachabe kkkkk confidence mwala amwala
😀😀😀😀😀kkkkkkkk I can't wait
Kkkkkk
Umumu nde mulidi Vuto
Mweeeeee
Uchapidwatu Koma mandotaaa kkkkk
Awesome 😎
Khaziyo big sayakhai amakutepani NDI foniyo
My favourite person Chemandota
Brilliant Mandota 😂😂😂😂😂.
I can't wait to the next video
Akunenela Kwa abwana ako amena
Push ndamene amuthandize chemandota ndithuu 🤣🤣🤣
Kkkkkkk koma ndaseka kkkkkk
Koma kankhani akangonva zot ukufuna umulasle mkaz wakeyo akufinya julata uwona😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
My favorite comedy in Malawi 🔥 am watching from Comoros
Kudikila week yamawa mpaka pano aaaaa inu mwatani kodi
You're the best Che Mandota 🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣
waiting for next episode.....koma I guess Alola zothanzizidwazo😃😃
Nice comedy ,mandota on 🔥
Mukuveka aChe Mandota kuno ku Mozambiqui ,mukutiseketsa ..muli boo
Kkkkkkkkkkk ati kunena mwamphamvu osadziwa kuti phone ili pambalipo Kkkkkkkkkkk koma chemandota I can't wait for next week
Ukufna idye madam bigy
Bhuuuuuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Che Mandota mumatimvetsa kukoma😂 pitilizani
😂😂😂😂😂🤷♂️ komatu uwu ndiye wakwana hahahahahah .... banja limalimba akakhala vuto bambo 🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌🙌 you're the best . Can't wait for part 2 😂😂
Mandota mwayanba kufusira eeee
Koma mandota
Sindinabese libandulo langa
Umatha.
Koma akupanga recording chemandoda
inu ndindolo mandotha😂😂😂
Kkkkkk 🤣😂mumakwanira bg
Azakumenyani coz akukupangani voice recoder cheh kk
I think actor akufa week yamawa chifukwa mkaz wabwanayo wapanga record zose zimene wayankhula che mandota kkkkkkk
Komatu Pana Santana akati akunyenge eeeee. Kkkkkkk
Mmatha boss #Ndotaaa
Apapa Mandota is definitely being recorded & he gonna be in a hot soup when his boss is back 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Lol ndiye mwati che mandota osati bwana mandota😇
Wayi kwapula bho
Chimene atayakhe ndichakuti amakupangani record a mandota piliz😂😂😂🤣🤣I can't went part 2
🤣🤣🤣tikuwona kudwa km iweyo ndi dolo 🤣🤣🤣
Kkkkkk km chemandota umakwan iweo😅😅😅😅
mandota iweyo ndi one mmmmm kkkkkkkkk
Osaiwala coment
Che mandota nkaziyotu wakukanani pamenepo ndiposo adzauza abwana anu
Mmakwana inuyo ndi Captain
Km che mandot adakoza kkkkkkkkk ukufun kuikam wanu mwana ai zikom
Akushatapulani man mwinaso amakupangan record aziziwa a Kankhani muli mmadzi mn kkkkkk
Ukamapanga download ma comedies a che mandota sikuti ndikubesa ai mmmmh!!! Amatha ndithu
Mandota iwe ndi 👍👍👍👍👍
Yomweyo galu iwe
Mphwanga, zikuvuta
Inu nda king
Kkkkk chemandota umatha koma days Ina uzapangeko ndi ma askono.
Inutu basi wa kumudzi wakwana🤣🤣🤣🤣🤣
Komatu apapa ndie zaipa kwabasi
Chokatengera fone mkukhala chani?
Game mbola apa usanyadire kwambiri.
😂😂😂😂😂actor afa next video. Umakwana Ndoxy
Akulu inu mufa ulere paja nde siumalapa kkkkkkkk
I Ikathera kuwaya iyi
🤣🤣🤣🤣🤣iwed ndi mandota ase
Koma chemandota kkkk ndinu patali, ulemu kwa chemandota crews, mumaitha guys
Palibe zoyakha koma ukukamangisidwa
Iweyo ndi dolo ase😂✊🔥
Amapangidwa record ameneo akita azava basi kkk
Uyutu anakupanga record ixe zithera misozi iyi
Kkkkkkk iwe ndichitsilu kobasi
Koma mandota usanditseketse 😂😂😂😂koma mkazi ameneyo akupwetekesa kwa abwana
Maili ali ngat Sikono sitizamuona mpaka mpaka
Umatha kucheza usazafe
shudren mayili alikut 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ukwana
This guy eeeeshi 🙌🙌😂😂😂❤️❤️♥️♥️
Chemandota mmakwana kkkk 😂😂😂
Kkkkkk mandota nd more ....
😂😂😂 Amandota zikuvutani
This guy is so funny 😅😅😅😅
Piliz pilzi ndoxy sholusholu yakeeeeee🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😍😍😍
Nice
😂😂😂 mbambande che mandota
litunu likusogodwa kkkkkk
😂😂😂😂😂 chi mandot amatha kufuna kudya amkz abwino
Mandota on biii🔥🔥
#Kankhani ndi dolo 🔥