May this song strengthen someone going through hard situations. Be strong and be courageous. I pray that God answers you speedily in Jesus Mighty name ❤❤
Thoko Suya has a way of ministering to my spirit that I can't even put in worlds. May your name be forever grorified dear Lord because of the gift of ministration through music that you gave us through Thoko.
Mumandidalitsa kwambiri mama suya
Koma yesu yekhayo ,ndalama zimalephera koma yesu yekhayo,abwezi amalephera koma yesu yekhayo,kukhala ndi moyoku koma yesu yekhayo
@@tamaramayuni559 amen 🙏
Reminds me of those old times when people went to church to seek the face of Yahweh and not now we go to church seek prosperity
My favorite song i can sing it throughout the day,nothing else only Jesus
Koma yesu yekhayo ndiye njira ndichowoonadi
Nic song ilove you thoko suya nyimbo yanu ndimatsitsimuka kwambili mumandipasa chilimbikitso kut ndisamirebe kwayesu
@@MercyMichael-z8t amen amen 🙏
God be praised
Koma yesu yekhayo Amen❤❤
Koma Yesu yekhayo!!!!Abwenzi amalephera koma Yesu yekhayo 😢
Zikomo Thoko umayimba nyimbo za bwino mulungu adzikusamalila ndi kukuteteza umatilimbikitsa kwambili pazambili zikomo
Amen God remember me
May this song strengthen someone going through hard situations. Be strong and be courageous. I pray that God answers you speedily in Jesus Mighty name ❤❤
Zikomo mama ndimadalitsika Nanu ndi tsiku lililonse ndimamvera nyimbo zanu ndipo ndimalimbikitsika nazo
Ntchito zanga sizikondweletsa inu mulungu wanga 😭😭😭
Koma Yesu ekhayo
Zonse sizikwanazi koma Yesu yekhayo 🙌🙌🙌
100% true
Koma yesu ameneyu
Thoko Suya has a way of ministering to my spirit that I can't even put in worlds. May your name be forever grorified dear Lord because of the gift of ministration through music that you gave us through Thoko.
Koma yesu yekhayo ❤❤
Mtumiki wa Yesu ,opembedzera Yehova namalenga .....ukuku wa Yehova paliponse uonekele ndi kufikila
Zikomo yesu🎉
Happiness chinkwita.may yoh soul continue resting in perfect condition peace 🕊️😢..
Ngati ndafka kale ku paladizo ndkuva kukoma zed pena ngati ndlire eee amen amen
Powerful song❤❤❤❤
Ndibisale momwemo mwa yesuyo
Zonse sikwanayi koma yesu ekhayo amen sisi
Koma yesu yekhayo ameeen
O yes.... Ndibisale mungaka yake
Powerful song
Zonse sizikwanatu Koma Yesu ekhayo❤
Koma Yesu yekhayo ❤
Koma Yesu yekhayo... 🙏🖤
Mai inu Mulungu apitilize kukupatsani mavumbulitso ochuluuka simunapaleko nyimbo zanu
Powerful watching from zambia
Ndi Yesu yekha basi
I love you Mai Busa Suya❤
Bwana Sandram ulemu wanu
@@FlorenceAliciaPrince-eu6yr amen amen
GOD BLESS YOU AND INCREASE YOUR ANOINTING MORE FAVOR AND GRACE IN JESUS NAME
I'm from Moçambique and I love this song❤
My favorite song..I always listen to this song everyday
This song is powerful and full of grace of jesus
Dziko limalephera koma yesu basi powerful
Koma yesu yekhayo from Burundi
Powerful singing pouring out her all .❤❤
Our strength is in God alone. ❤
Yesu yekha♥️
Koma yesu yekhayo Amen
Deus anazimukatu,bravo brother
@@FlorenceAliciaPrince-eu6yr Inde Inde atsogo
This is massive to my heart.
God bless you.❤
It is said that men don't cry, but with this song, I fail to hold my tears😭
I feel blessed so much when listening to u songs and that reminds me walls of Jericho gell down because of singing....wow!
Hahahahaha koma yesu yekhayo
Koma Yesu ameneyi, eeishi!
Ndibisale momwemooo basiii!!!
Yesu salepela
Koma nyimbo ndamvera iyi pansi pamva, mmawa uliwonse nsanatuluke ndimaonetsetsa kut ndiimvere. Mamie inuyo kumwamba kunakulemekezani ndi luso❤
Koma yesu yekhayo🔥🙏🙏
But how did i miss these live shows??
Zonse sizikwanatu koma Yesu ekhayooo🙏
I like the song❤
Ndikafika kwathuko tiwonane ( ndi Yesu) maso ndi maso.... strong message ❤
Ntchito yabwino Mama Buu!
Ndili wodalisidwa pakubvera nyimboyi Ambuye apitilize kujudalisani 🙏🙏🙏
ndibisale momwemo🙏
That's very powerful indeed
What a powerful hymn
Powerful watching from zambia ❤
God bless you and your family 🙏🙏🙏🙏
Praise the Lord.koma yesu yekayo.
Koma Yesu yekhayo basi ndiye chida changa .
Glory to God
I feel heaven when I hear this songs
Thànthwe langa ndo yesu
Ndibisale momwemo Amen
Amen zizikondwelanu I watching from Zambia
This woman amandidalisa🎉
Powerful full of the anointing.Gid bless u mum
Koma yesu ameneyi mama
Amen, God remember me
Amen mama
Nyimbo iyi imanditumikila mochuluka and I can't stop watching it ❤
🎶🎼🎤Zonse sizikwanazi! koma Yesu yekhayo🎸🎙🎶
Koma Yesu yekha Amen
What a powerful song.
Koma yesu ameneyu praise the Lord
Koma yesu yekhayo hallelujah 🙏no weapons formed against us shall prosper 🙏🙏🙏🙏
Koma Yesu yeka bas
Mumatisisimusa ndinyimbo zanu mama, mulungu apitilize kukupasani zisomo zochuluka
Thanks God
Amen Amen
@@kettiemkumbira3973 amen
Koma Yesu yekhayoooo😭🙏
Powerful god bless
On repeat 🔥🔥
May God bless you Emmanuel
Glory be to God 🙏🙏🙏🙏
Am blessed with your songs mum
A song without borders
That's true
Koma yesu yekhayo
Yesu yekha Amen 🙏 🙌 👏 ❤️
My favourite song... Am blessed
Glorious 🔥🔥🔥🔥🔥
It's really just Jesus. Powerful song indeed.
This is a great song
This song will never go
Powerfully song
Koma Yesu Yekhayo
Feeling great and blessed this morning 😫🙏
🙏💪👍