congratulations to the young talented Aidfest And Kineo, mumatha "Big thanks for to Jaakev mukukwaniritsa basi support yonse pa industry". I'm from Mozambique
Iweyo kuphwekesa nyimbo iyiyi nde umafuna nyimbo iyimbidwe bwino motani?🎉 🔥 hit .....am not a fan of Malawi Music that much but this is the music you call play whole night........Big up flames 🔥 zuwa salozerana aliyese amaliona ....hit fire 🔥 🎶 🎵
Koma nyimboyi mwati ndiyaku Malawi kuno. Too good to be true. 🎉
Itiyo
Kwathu amabwera yekha ndi matenda ake pheee💃💃💥💥
🤣🤣🤣🤣 kumulandila ndi nkokomo
@@innocentchikapa9404 zinthu zake amwene😂😂
Kkkkkk
Kuwagawana
😂😂
Amene titha pa repeat let's gather here 🔥🔥🔥🔥
Nyimbo yolimbikitsa uhule. The vibe is just too fire koma
Anthu ndipo akulimbikiratu kuposa kugwira nthchito kkkkkk
Guys lyi yokha yifike 1million view jealous down anawa akuyimba bwino ❤❤❤ love u kineo and aidfest 😊
You can say that again 🎉
nyimbo ndi Hit iyiyi ... Kaya muti mkaziyi ndiwagulu koma kwathu amabwera yekha
Eeee weekend yuchedwa tivine ma bar mu
@@cloy28eyemark😂😂😂😂😂😂Km ndiye
Iwe umati
4@@ChimwemweIdanaMasiye
Our very own Blaq diamonds ❤😂 nyc one iyiyi ili pa repeat tuu ati uyuyu ndiwanga wanga basii eeeh pamenepo
😂😂 literally what I thought
For sure like blaq diamond ❤️❤️🥳🥳🥳
Zolaulatu a kineo mwaiyamba verse and mwaika hook Track is lit
Ndipoooo
Chi heat
I think ambilinu Kineo samatsata alind solo songs pomwe Aidfest sinamvepo olo imoz
Mmmm man mostly amaoneka ko kut akupanga zambili ndi aidfirst yo..... Koma iyiyi kineo wapha
@@SophaiTadeyo komadi
jerous down nyimbo zanu zimamveka bho ndipo am one of your fans🎉🎉🎉🎉🎉
Ndipo live
True 🎉🎉
Ok Malawi gut vibes. Zambia 🇿🇲 and Malawi means kuchalo. I gut our support from Zambia 🇿🇲
Kineo, I'm impressed now that umatha. I'm ur big fan. Yekha 🎵 🎶 tachezera nayo dzulo
Thank you guys for feeding the nation with pulchritudinous amapiano songs
Much love from here 🇿🇼 these guys they're representing Malawi
Another Hit 1 mwatipanikizat oimba aku MW More! Fire works!!!! 💥💥💥💥💥💥💥
Everytime someone likes my comment ndilipano to watch it again 🔥
Bwela mphwanga uzawoneleso🤣
Eyo💥
Come again 😂
😊😊
Musatinyengepo apa aaaah😂😂😂
congratulations to the young talented Aidfest And Kineo, mumatha "Big thanks for to Jaakev mukukwaniritsa basi support yonse pa industry". I'm from Mozambique
This is good music ❤team on repeat/ibwerezenso let's gather here🎉
Koma nyimbo iyi..these guys killed it🔥🔥🔥🔥...ndipo nde sinditopa kuimvera😂❤
Hoooo God, this song is amazing ❤❤❤❤ from Mozambique
U are right ,but u should search vula Malaya,zeze kingston
Anawa khaliz ndi kev mwawachuna bho ali nyatwa more fire madnes😊😊
Amabwera yekha ...day ina adzabwera ndi HIV 🤣🤣...... Hit 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
😅😅😅
Boys mumatha eeeeeeh, this lit, smashing the boarder 🔥🔥🔥🔥🔥
BadBoy Aid 🔥🔥🔥🔥🔥
Hit after Hit🔥🔥🔥well done guys
You're leading the music industry...i like your joint🇲🇼💣💥
Mafanawa ndi madolo eee 🔥🔥
Ma guy's anga inuyo mmatha the hit is very powerful. Amabweladi ekha basi keep it up genties 🎉🎉🎉
Who have watched more than 4 times lets gather here❤❤❤❤❤
I've jxt watched it once
Can't believe that it's first time to listen to this nice truck.being my home land music.By God grace we r improving. Keep it up bro.
Seanyfilms 🔥🔥
Yoba 🔥
Aidfest + Kineo🔥🔥🔥🔥
This was powerful aaahhh😩😩😩🔥🔥🔥💯🙌
Kaya muziti mamunay nd wagulu amabwera yekha ❤🎉🎉
yes
Yeah 💓💓yes iwe Yenkha on fire💥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Amene tayenda chothamanga from mikoz page like my comment 🤩🤩
In the name of father son and the holy spirit, i bless you guys!. This sound i recommend it above all the past songs🔥🔥🔥🔥🔥
Thank you guys, I'm from Mozambique
U are welcome
Okay zipangani makani mufa ndi Etchavi💔🙌 Dzuloso anali ndi chi mdala china chake oho
inuyo ndimadolo guys mumatha🔥
koma nyimbo za ng'oma mkati ine nde zimandifikapo eish 😂❤zimakusintha mood osat masewera 💥👊🔥🔥
Ngt unali nkhawa balala😅
Guys please share the video ,,, let’s make this sound blow up 🙏🙏
🎉🎉
🔥 inu ndi madolo eeeh muli fire boiz🔥 nice work
kwatonse amene titenge matenda chifukwa cha nyimbo iyiyi,..lets gather here 🙃
Lol boss be serious😂
Kodi mukuti chani 😅
😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 komatu 🙌🏾
Ndati Mumva M'bebe...amabwera yekha ndipo ndimapita ndekha. ❤
Patiently waiting😌♥️🔥
Iyi yokha mwaswa ma blazz eeh 😂😂🙌🙌 much respect
I will not get tired to watch it again once you hit 🎯 a Like to me... Let's make it 100K first
This song is fire 🔥 from Zambia 🇿🇲
I will do 20 push-ups for every like
😂😂
Anawah amatha kuimba! Saying honestly muli talent yokhanzikika!
I will do 1 push up for every like that this comment gets ❤ this is hit
😂
You must be a bouncer now 😂
@@mayakadango3195 😄
😂😂😂😂😂
Iweyo kuphwekesa nyimbo iyiyi nde umafuna nyimbo iyimbidwe bwino motani?🎉 🔥 hit .....am not a fan of Malawi Music that much but this is the music you call play whole night........Big up flames 🔥 zuwa salozerana aliyese amaliona ....hit fire 🔥 🎶 🎵
Soon 1 million fewz 💪💪💪💪 Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥
Kineo killed this one tisanamizanepo🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼
Nkani ndiyokuti amabwera yekha basi ❤❤😂kaya tilipo gulu kaya bola kwathu amabwera yekha
Let me say a word international🔥🔥🔥🔥beat nde mwaikwera
Izizi ndi zanyinbo zimatha kwambiri ❤❤❤ muzangosowa guys 🙌🙌
Thank you Mikozi page yikanatidutsa 😂😂😂😂😂😂🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Madness Entertainment 🇲🇼🔥 ma guys team yanu ikutipasa Content Yabwino Keep up Guys❤❤❤
Mafana Ali ndi luso awa 🔥
Tiyeni tapase anawa 1k ....I'm watching ka number 6
Amabwera ekha on repeat keep it up mwana wa kulu anga
Its now at 1M views guys woow 🎉🎉congratulations boys🎉🎉🎉🎉
My baby is there gooo Ntaba ❤😊
Ngat ali wagulu ndine admin wagululo😏🌹❤️big up boiz
Anawa samapalayi 💥✊ ichi ndichi hit mesa 🎉
Fantastic!! Keep the fire burning boy!!!!!
Best collaboration ever, yekha yekha 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Hit song big up hustle sugona ikan giya osapang zibwanans 🔥🔥
I like the idea of getting tima model ta size yanu😅, baddest tune big up
Nkhani ikhale yoti amabwera yekha basitu❤️❤️❤️❤️
Jetu kikkkkk naneso ndiyamba uhule.....ndaseka
Palibe chilichose ndikuona apa
Choipa very good guys
Nice song❤❤❤❤ keep on working hard our Young stars
Eeehh Kodi etii 😂😂
Mwafera maonekedwe etii... tiphanaa 🙌🙌
Ya ready know uja amafunikiranso 😅😅😅😅 iyi nd hit ✌️🔥🔥🔥🔥🔥🔥
nyimbo iyi ikumakhala on repeat ngat ndilindi chibwenzi😂😂😂💔🙌🏻
😂😂😂😂 ma guy, 😂😂😂
Mmwandiwaza heavy.
Let me leave this one here first. 😂😂😂
I like the tune.
Amabwela awir kale, koma anasiya titolaso best friend wak😇😉😉😉😉
Hit song
Chaka chino mumva m'bebe😂😂😂🎉🎉🎉🎉nice songg❤❤
uyu ndi wanga wanga wanga basi ndasayina ndasayina basi ❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥❤🔥
It's the wagulu and chimulu part❤️🔥
💃💃💃ndpo
Mmakwana ma guys best duo group chaka chino mukutenga
The Malawi music industry is developing indeed. I like you guys. Keep it up
Wow that's great Song kept up mumatha inuyo guys 🔥
Mwakwana mafana my favorite song now ❤
Nice hit 🔥 🔥 🔥 🔥 osati zachina JB kufuna kuchosesa malawi pa map😅😂😅 kuyamba lelo JB siwakumalawi
Inuyo ngt mmukufuna mmuzibwera nayee ngt Ari waguru km kwanthu akimabwera ekha iiiiiiih hit after hit
I see you my model duh Tiya ntaba ❤🎉
I was at Dedza last week with Zeze kma fans inkafuna mafanawa Nd Jetu of course kunali Mablacks ndie tinava kukoma kma
Love this song 💝😍💝💝😍 . Eli you are the best
Fantastic song week end ndalama zitha basi
Malawi to the earth 🎉🎉🎉
Zoona onena azinena koma akama bwera kwathu anabwera yekha❤❤❤😂😂😂 🎶🎶🎶🎶
Big up guys
This song Hits different🔥🔥🔥🔥
This song deserves more than the support it's receiving
Can't get enough🔥. In love with what madness is doing to these two
Kodi ka dara kovura mayarako bwanji ❤😂🎉🎉🎉
Nyimbo ili bwino kwambiri keep it up guys🔥
Mafana awa music industry ili mwanja mwawo 🔥
Amuperekeza ndi Ena koma akamafika amafika yekha osati mpaka kubwera yekha eeeeee kunaipatu 😅😅😅😅😅henewe sounds pretty gud
Zolimbikisa uhule basi.....nice koma🔥