*Noni Noni Lyrics by Phyzix, Martse and Dan Lu* *Verse 1: Martse* Pano achina martse amafilidwa ndi ma diva ngakhale ndi azimayi a mvano/ Pano sindikuchoka chifukwa ndaona Ka noni noni noni noni Pano / Pano after nditayimba mwano akazi kundizungulila ngati ndikukamba nthano /Pano/ Akuti azandiphaka ine akuti azandiphaka mani ngati phwando/ Ndawauza kuti eh ndibwele mawa/ Ndizitolele Kaye ndigule bawa/ After zokhala single sizindikhala/ Nde titha kukhala limodzi mpaka mawa/ Sikafuna cash man koma time man/ She has no friends kandiuza alibe size man/Ndakafusa wagwaan yoh its my time /And she knows that I still keep it fresh man. *Chorus: Dan Lu* Apa apa ndidabwepo apa Munthu wamkulu angozungulira khonde Ndati ndati ndidabwepo apa Mose wayambira munthuyu sakuchoka Kumukoka/ sakusuntha Kumukankha/ sakugwa I think wamva Noni Noni I think wamva Noni Noni *Verse 2: Phyzix* Kodi Jomeni uyuyu/ mission yake mu hood mwathu ndi mkazi uyuyu? Ndikudabwa naye uyu/ akumapezeka kuli konse kuli mkaziyu! Ma chick a ku BIU/ Polytechnic, CHANCO, MZUNI Bhawa uyu Ku Medicine ndi ku Exploits ku LUANAR mufunanso Bhawayu? Chimenyeleni chi verse mu Bayuum Thiii Mabebi akumadzapempha udukulitsi Chaka chino ndi cha Captain Bae/ Man Phyzo/ ngati uli woimba ulimbe Ndimayankhula ngati munthu wa ndale Ngati mphasha ZANI angandi CHALLE Ukangomva Very Good! Very Good! UmangodziwilaTU verse si mphaleTU *Chorus: Dan Lu* Apa apa ndidabwepo apa Munthu wamkulu angozungulira khonde Ndati ndati ndidabwepo apa Mose wayambira munthuyu sakuchoka Kumukoka/ sakusuntha Kumukankha/ sakugwa I think wamva Noni Noni I think wamva Noni Noni *Verse 3: Dan Lu* Mkaziyu angoti male/ dolo ndi ameneyu andi marry/ marry He has cash don't worry/ political affairs she just party/ party Coz you know/ mafilu Sangayende pansi/ kukwera bus Coz akudya money Wamva Noni Noni Noni Noni Noni Noni Too Ghetto Too Gutter Wamva Noni Noni yaka yakayo Wamva Noni Noni yaka yakayo Very Good Very Good Coz you know/ mafilu Sangayende pansi/ kukwera bus Coz akudya money *Chorus: Dan Lu* Apa apa ndidabwepo apa Munthu wamkulu angozungulira khonde Ndati ndati ndidabwepo apa Mose wayambira munthuyu sakuchoka Kumukoka/ sakusuntha Kumukankha/ sakugwa I think wamva Noni Noni I think wamva Noni Noni It's Only Entertainment (#IOE) *Outro: Phyzix* Chilungamo ndakuuzani mushale Ma chick a mu hood mwathu thick/ Zani Challe Thick/ Zani Challe Thick/ Zani Challe Thick/ Zani Challe Thick/ Zani Challe
*Noni Noni Lyrics by Phyzix, Martse and Dan Lu*
*Verse 1: Martse*
Pano achina martse amafilidwa ndi ma diva ngakhale ndi azimayi a mvano/
Pano sindikuchoka chifukwa ndaona Ka noni noni noni noni Pano /
Pano after nditayimba mwano akazi kundizungulila ngati ndikukamba nthano /Pano/ Akuti azandiphaka ine akuti azandiphaka mani ngati phwando/
Ndawauza kuti eh ndibwele mawa/
Ndizitolele Kaye ndigule bawa/
After zokhala single sizindikhala/
Nde titha kukhala limodzi mpaka mawa/
Sikafuna cash man koma time man/
She has no friends kandiuza alibe size man/Ndakafusa wagwaan yoh its my time /And she knows that I still keep it fresh man.
*Chorus: Dan Lu*
Apa apa ndidabwepo apa
Munthu wamkulu angozungulira khonde
Ndati ndati ndidabwepo apa
Mose wayambira munthuyu sakuchoka
Kumukoka/ sakusuntha
Kumukankha/ sakugwa
I think wamva Noni Noni
I think wamva Noni Noni
*Verse 2: Phyzix*
Kodi Jomeni uyuyu/ mission yake mu hood mwathu ndi mkazi uyuyu?
Ndikudabwa naye uyu/ akumapezeka kuli konse kuli mkaziyu!
Ma chick a ku BIU/ Polytechnic, CHANCO, MZUNI Bhawa uyu
Ku Medicine ndi ku Exploits ku LUANAR mufunanso Bhawayu?
Chimenyeleni chi verse mu Bayuum Thiii
Mabebi akumadzapempha udukulitsi
Chaka chino ndi cha Captain Bae/ Man Phyzo/ ngati uli woimba ulimbe
Ndimayankhula ngati munthu wa ndale
Ngati mphasha ZANI angandi CHALLE
Ukangomva Very Good! Very Good!
UmangodziwilaTU verse si mphaleTU
*Chorus: Dan Lu*
Apa apa ndidabwepo apa
Munthu wamkulu angozungulira khonde
Ndati ndati ndidabwepo apa
Mose wayambira munthuyu sakuchoka
Kumukoka/ sakusuntha
Kumukankha/ sakugwa
I think wamva Noni Noni
I think wamva Noni Noni
*Verse 3: Dan Lu*
Mkaziyu angoti male/ dolo ndi ameneyu andi marry/ marry
He has cash don't worry/ political affairs she just party/ party
Coz you know/ mafilu
Sangayende pansi/ kukwera bus
Coz akudya money
Wamva Noni Noni Noni Noni Noni Noni
Too Ghetto Too Gutter
Wamva Noni Noni yaka yakayo
Wamva Noni Noni yaka yakayo
Very Good Very Good
Coz you know/ mafilu
Sangayende pansi/ kukwera bus
Coz akudya money
*Chorus: Dan Lu*
Apa apa ndidabwepo apa
Munthu wamkulu angozungulira khonde
Ndati ndati ndidabwepo apa
Mose wayambira munthuyu sakuchoka
Kumukoka/ sakusuntha
Kumukankha/ sakugwa
I think wamva Noni Noni
I think wamva Noni Noni
It's Only Entertainment (#IOE)
*Outro: Phyzix*
Chilungamo ndakuuzani mushale
Ma chick a mu hood mwathu thick/ Zani Challe
Thick/ Zani Challe
Thick/ Zani Challe
Thick/ Zani Challe
Thick/ Zani Challe
Nyimbo imene nnaziwa kuti inuyo aphiyzo mwabwera nnaziwira that song eeh munakutha man
Who is here in 2024🔥
Martse was a machine
Akatundu. RIP Martse
@@kamzy6158 legend never die
It's 2022 and I can't still get enough of it, simply a masterpiece 🔥🔥🔥🔥😍😍🇲🇼
End of year 2023 but still is the best song❤
Bom video,boa musica.
shout out to malawian hiphop 🤟💥
sanqakwere bus akudya Money.. umayitha captain Bea level ...
U rock guys man phyzo
Greetings from Finland #A brothers mumaitha achikulile 👌❤✌#NONI NONI
Thank you M-DOUBLE! Much appreciated
Nyimbo iyiyi ndi akatundu 🔥
Rip to Martse
captain bae waipha... love it
Thank you. Much appreciated. #CaptainBae
This a big bang homies...💯
Kod Domini uyu uyu mission yake mu hood mu ndimkazi uyuyu 🤣🤣🤣🤣🤣hahhahahah koma adah inuyo VERY GÒOD VERY GOOD VERY GOOD
2024🙏
Martse😭
Ngati bodzatu 😭😭😭😭
Rip mr man martin
#captainbae Issa hit !!
Thank you Emily!
Nyimbo iyiyi osayitora
❤
hits i like it mwaitha fellaz
Thank you Romeo
noni noni osanama ndakafila hvy Kali bho
Yes panopa yaymba kundisangalasa
Very good very good
💯💯💯💯💯🔥🔥🔥🔥🔥
nice 1
To those who said Malawi is poor they all shirt,,this people are enjoying kuva noni noni,,which I'm thr🤡🌹
Good..
nyc 1
achina marste ndi madolo pa mbwerera production maguyz
Mmmmm captan bae ndi one
Ndanva noni noni
muli boo
Thank you
Ndanva noninoni..lol..nice
Thank you Amanda!
ndimanva ukoma
Ndikudabwa naye uyu hahahaha kom cholapitsa umakwana
Thank you. Umaitha
Nice one
Thank you Nick!
Who still enjoying it 2019(jupsy Jupapa)
We r here
#Noninoni
noni noni osanama ndakafila hvy Kali bho