ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Keep it up big manlakula ndi dyera kufuna kudzudza a Malawi Mulungu awakankhe
Wakumva wamva bwana ulemuwanu ndipopitilixani ndikutiunikila ndinzeluxanuzabwinozi Mulunguoziwakudalisa ndikupelekanzelu akhalenanunthawixonse ameen
Munalimalo mmisewu kumakajila pamene munali kulamula
Palibepo mfundo apa
Kuyankhula mwamphamvu young man.
Mcp paulendo 2025
Oro mungagule anthu bwanji a MCP koma voti ndiwe wekha mudzakhamudwa 2025 mudzalira.
Ulila zenizeni usanati ndipo unyenyeka
More 🔥
Komatu akulakuluwa akutionongera dziko ife tikuona.Heatherwik Mtaba ndi anthu akuluakulu ndipo ambiriwa akuyenera kusiya ndale.
Mulungu atipulumutsa ndithu mulungu si Lazaro
Amwene tikuuzeni Kuti anthu akuthawwko chani Ku DPP mwina simukudziwa chisankho chimene anapanga adpp anthu ambiri sanakondwe nazo masankhidwe Ake Moti pofika July 2025 aaaaa ambiri achokako zimenezi muziziwa
wabodza iwe
Mawumawu mvivi zina zanyasidwa nanu bravo bravo
Muthu sungamu pangile zochita mbuzi chibazi wadya chimene cjikulakhulitse ukunama palibe zakuvuta angakuvele zimene akulakhuzo
Pliz Nyau iwe, upite ku school ya Kwacha. Kukanika kulemba chichewa zoona?
Kambani ndinu ndege unagwetsa ndiwe basi umbuli ngati DPP alibe nzeru ngati iwe
Chonena Chagwera Nkati
Wakumva wamva, munthu wanzeru zake sangadzayerekeze kuvotera boma ili nthawi yachisankho chaka Cha m'mawa!!!
Mwasowa chonena ali yese ali ufuli wolowa chipani chimene wachikonda
Ndiye mwati ankukha chiani 😮😮😮😮
Mawu
Mwalankhula bwino bwana anthuwa tawatopela chofunikila ndichakuti aliziwe ziko atasala okha abale awo akazi awo ana awo ataphedwa inenso ndagwilizananazo zimenezi ndipo ife tikhoza kubwela kumeneko ndipo tikhoza kupanga zimenezi chifukwa m c p anyamata awo alli ndi chibwana
Musanamize athu amuluzi anamangidwa ndichipani cha dpp ndipo mtsoleli wawo adatani kumumasula
Anthu Akuda kumuvotela munthu kumuika paulemelelo inu ndikumadya chitedze. Ma MP Nyumba zomwe akumanga komanso magalimoto akugula ndi vote yako,
Mau amphamvu kwambili
zako iwe ushasha ndi umene ukukuvutawo ungatani kodi iwe pola moto ulila ndipo sunati wa dpp iwe kampeze muloyo umudziwe ukamuyabe dala akuswe
😂😂😂😂 eti osasonkha msonkha, msonkho ndi force bwanawe
Zomvetsa chisoni kwambiri
Dzuwa salozelana APM anachita kududuluza kumukwezeka pasanja nthawi yamsonkhano wawo uja aliyese anaona zimene zija Kuti akuluwa Atha ndiye pano muziti anthu akugulidwa aaaaa manyazi bwanji
azatsitsa zinthu ndindani iwe tanenako presdent anatsitsako zinthu malawi muno? munaononga kale zinthu dziko muno ndamene munapangisa kuti anthu tizizuka inu osangotseka kukamwako bwanji
Ndizó ndalezo mbale
Zoonadi bwana mphepo amalawi tiyeni tizuke tsopano nthawi yakwana tsopano.
Kuganiza mopepera bola kulankhula pati ndiye munthu
Ayimba chani uyo ndi wa satanic chimoto
Fusani phungu wanuyo osati mudane ndianthu ena vuto ndi maphungu anuwo ife pheeeee wathu akutithandiza kwambiri
Moti apa mwadya kale kwasala kawili Kuti mudye
Eeee koma mwalusatu kkkkk 😂😂😂😂 muli pamavuto amwene
Ali zochita zawo awa koma kumvela chisoni abale ako ndi anga
Masamaiwale kuti malawi ndiziko lanthu ndipo kulibe komwe tingakakhale moyo wathu onse kuposa kumalawi nde anthuwa akamatiunikila zimakhala zithu zabwino kwambili
@@AliajoeAliajoe-vv1wo aaa kuunikira kumakhala konyoza chonchi kokhala ndimbali?
Eeeeee koma utenga wabwino
Mulungu wathu kumwambako fungatirani anthu wonse a chipani cha dpp musalore satana apambane tichitireni chifundo
Boma ndi lomweli sitikusintha
😅😅kkkkk zopusa
Chakwera woyee MCP 2030 and above
Ngati likukukanika banks lako ndiye usitha bwanji maganizo azako
Mcp chaka cha mawa kulibeko dpp boma
Uli pamavuto m'bale😂😂😂😂
Kkkkkkkkk uli bizzy kulankhula za ziii kagwireni job
Boma ndilomweli
fotsek
Mbuzi
😂😂😂 boma ndilimene, a richard mungovutika ingokhalani pansi 😂😂😂😂 I think zomwe mukuyankhulatu zikusonyeza kut inuso mumapha anthutu 😅😅
Keep it up big man
lakula ndi dyera kufuna kudzudza a Malawi Mulungu awakankhe
Wakumva wamva bwana ulemuwanu ndipopitilixani ndikutiunikila ndinzeluxanuzabwinozi Mulunguoziwakudalisa ndikupelekanzelu akhalenanunthawixonse ameen
Munalimalo mmisewu kumakajila pamene munali kulamula
Palibepo mfundo apa
Kuyankhula mwamphamvu young man.
Mcp paulendo 2025
Oro mungagule anthu bwanji a MCP koma voti ndiwe wekha mudzakhamudwa 2025 mudzalira.
Ulila zenizeni usanati ndipo unyenyeka
More 🔥
Komatu akulakuluwa akutionongera dziko ife tikuona.Heatherwik Mtaba ndi anthu akuluakulu ndipo ambiriwa akuyenera kusiya ndale.
Mulungu atipulumutsa ndithu mulungu si Lazaro
Amwene tikuuzeni Kuti anthu akuthawwko chani Ku DPP mwina simukudziwa chisankho chimene anapanga adpp anthu ambiri sanakondwe nazo masankhidwe Ake Moti pofika July 2025 aaaaa ambiri achokako zimenezi muziziwa
wabodza iwe
Mawumawu mvivi zina zanyasidwa nanu bravo bravo
Muthu sungamu pangile zochita mbuzi chibazi wadya chimene cjikulakhulitse ukunama palibe zakuvuta angakuvele zimene akulakhuzo
Pliz Nyau iwe, upite ku school ya Kwacha. Kukanika kulemba chichewa zoona?
Kambani ndinu ndege unagwetsa ndiwe basi umbuli ngati DPP alibe nzeru ngati iwe
Chonena Chagwera Nkati
Wakumva wamva, munthu wanzeru zake sangadzayerekeze kuvotera boma ili nthawi yachisankho chaka Cha m'mawa!!!
Mwasowa chonena ali yese ali ufuli wolowa chipani chimene wachikonda
Ndiye mwati ankukha chiani 😮😮😮😮
Mawu
Mwalankhula bwino bwana anthuwa tawatopela chofunikila ndichakuti aliziwe ziko atasala okha abale awo akazi awo ana awo ataphedwa inenso ndagwilizananazo zimenezi ndipo ife tikhoza kubwela kumeneko ndipo tikhoza kupanga zimenezi chifukwa m c p anyamata awo alli ndi chibwana
Musanamize athu amuluzi anamangidwa ndichipani cha dpp ndipo mtsoleli wawo adatani kumumasula
Anthu Akuda kumuvotela munthu kumuika paulemelelo inu ndikumadya chitedze.
Ma MP Nyumba zomwe akumanga komanso magalimoto akugula ndi vote yako,