Lulu cool guy ife Lulu amatisangalatsa ndipo kunyoza Lulu mkulakwa , ndipo nyimbo za chikalezo Ife tasangala ndi ma music splash ndi Mr splashon , ndipo Lulu sa shilimka nyamata odziwa kuvina , keep it up Lulu,
Lulu ndi shasha kaya namadingo atani koma lulu ndimphudziwako wako namadingo kaya unyoze bwanji koma lulu ndi dolo komanso lulu ndiwapa easy that's why he will have legacy
Ine ndi fan wa onsewa koma Doc matukutuka amawapweteka, Lulu is far much ahead of all musicians in Malawi. Lulu can do a lot in music that Namatist can not. Lulu production of many years back is still enjoying airplay and still making sense than our brother's songs.

I love Lulu ❤ anamadingo kuzikweza too much
Namadingo kuzikonda, lulu ndi cool guy
Lulu ndinumber one .Nama dingo amazimva kwambiri atachepetsa kuzikuza pang'ono anthu ambiri azamukonda
Namadingo amapanga zinthu mwa nzeru
I like Doc kumbali ya yakanizidwe pa business
It just shows kuti anthuwo akuziwana, vuto ndnu you want to bring negativity
Namadingo kulizaka 10 kutsogoloko kuti akafike pa Lulu.
Lulu ndi shasha kaya namadingo atani koma lulu ndimphudziwako wako namadingo kaya unyoze bwanji koma lulu ndi dolo komanso lulu ndiwapa easy that's why he will have legacy
i like Lulu is a cool guy
Namadingo ndi kaswili
Namadingo ankaloweza nyimbo za Lulu kkkkk
Awa ndiye mau ,I know lulu ndi Khalidwe lake lomwr
Lulu is my guy 👦 I like this guy so much Lulu god bless you 🙏 ❤️ 💖 💗 ulemu wanu Lulu Namadingo matama too much go away small boy 👦
I love lulu cool guy continue to honest
Kd muzingoziika poyela zazanu zolakwika osamafukula zokhuza ambuye
Mavita ndiwe amene ukufuna kudanitsa anthuwa
Namadingo nimwana walulu ngati yomaps nimwana wa mack 2 azigwilizana
Vuto la namadingo smachitika nanga sanyera matama akewo
Lulu ndi dolo kuyambila khale namadingo angokula mtima
Lulu ndi dolo anamadingo kaya mutani sungazafike pa lulu size yanuu namadingo ndi shama vocs
Namadingo akuyenera kumapeleka ulemu kwa Lulu. Lulu nd dolo guys
Iwe namadingo mwanowo udziona anthu owapangira koma Lulu yekha umusiye , ndipo Lulu Ali patsogolo pako , wayamba liti iweyo kuimba , ? Ife amatisangalatsa wava ! Mnyamata odziwa kuvina
Lulu ndi one❤
Namadingo ndi zoba , kape
Big man ndi lulu
Namadingo ndi okula ntima
Lulu is best Artist
AMalawi nthawi zina kumawona express views Namadingo marketing amatha heavy plus sound alibho
Lulu ndi dolo heavy
Iwe ndi mbuzi nde wakanbapo chani apa
Lulu ndi big mani
Uyu mapwala aafuna kudanisa anthu
Namadingo mbambande
Namadingo ndi dolo iwe mavita ndiwe kape
Pa Lulu ife tinathera
Eeh Koma namadingo alibe ulemu
Namadingo wangosiya kuyimba kwaya pompano sangafanane ndi lulu
Namadingo saakutha kuyimba
Namadingo nd paja nd wachifundo
Nice one ❤🎉 lulu
Iulu🎉
iwe vuto lako ndi chani,, what do you know about music. iwe nde wodanitsa. mbuzi
Lulu akatundu mboba
Khwisa good reply
Lulu cool guy
❤
❤❤❤❤❤❤
Ine ndi fan wa onsewa koma Doc matukutuka amawapweteka, Lulu is far much ahead of all musicians in Malawi. Lulu can do a lot in music that Namatist can not. Lulu production of many years back is still enjoying airplay and still making sense than our brother's songs.
Lulu
I love Lulu
Anthu inu jealous kwambiri. Musiyeni Namadingo alone