Nyimbo zanu zimandidalitsa pitilizani kumuyimbira ambuye nyimbo iyi imandisendeza chifupi ndi mulungu ndimamayimvera ngati isathe continue mama God bless your talent
Noone can replace you sure, your the best, Indeed God is using u , you born to do this changing people's lives , mmmmm l can spend a day without listening your song , God bless you mama . Mumandidalitsa .
Mama I love you ❤❤❤❤singalowe pa you tube without praying your songs🤗🤗🤗🤗umboni wako and mundibwezeretse hits zikhale my testimony this year in Jesus Christ name Amen 🙏🙏🙏🙏
Nyimboyi yabwera munthawi yake chifukwa mtima wanga ukufuna mawu a Mlungu koposa china chili chonse zikomo pomvesera Mzimu Oyera kuvumbulutso limeneli. Love your songs mum 🔥🔥
Za mphavu kwambiri pa moyo wanga this song and powerful kwa mulungu nyimbo imeneyi ndimene imandilimbitsa mtima panyengo zanga ndikamavera ndimankhala wodzilimbitsa kwa mulungu wanga
Mau anu Ambuye sadzapita pachabe zoonadi....mau anu adzakhala mpaka muyaya....Amen mayi busa suya....Mulungu akuuze malile anu ...mumatilimbikitsa mu nyimbo zanu zonse.....ulaliki wamphamvu
Thoko Suya my favorite, I love this woman, God uses you mum, may you live longer and proclaim the greatness and goodness of God . I love you so much mum i wish one day ndizakumane nanu and tap your blessings
Mai Busa mumandidalitsa kwambiri mumasutha nyengo zanga ndi kamamvera nyimbo zanu God bless you and akuze malire anu Amen
🙏🙏🙏
Nyimbo zanu zimandidalitsa pitilizani kumuyimbira ambuye nyimbo iyi imandisendeza chifupi ndi mulungu ndimamayimvera ngati isathe continue mama God bless your talent
Nyimbo iyi sinditopa kuimvera ndipo imandibweretsa chifupi ndi Mulungu ndikamafuna kupemphera. Ambuye apitirize kukudalitsani ndikukupatsani uthenga wambiri woti mudzitidalitsa , kutiphunzitsa komanso kutisisimusa
Amen 🙏
Noone can replace you sure, your the best, Indeed God is using u , you born to do this changing people's lives , mmmmm l can spend a day without listening your song , God bless you mama . Mumandidalitsa .
My favourite artist ,,,,,will never stop to like your song's..........your song's is always transformation .....
Amayi nyimbo zanu zimandisuntha kwambiri nkamamvera ndimamva amen olo nyengo zanga ndimaziona kusintha
Ambuye alemekezeke
Ine nyimbo iyiyi imandisutha chifupi ndi ambuye mayi busa suya mulungu azikudalitsan kwambiri mumandidalitsa
Mama I love you ❤❤❤❤singalowe pa you tube without praying your songs🤗🤗🤗🤗umboni wako and mundibwezeretse hits zikhale my testimony this year in Jesus Christ name Amen 🙏🙏🙏🙏
Nyimboyi yabwera munthawi yake chifukwa mtima wanga ukufuna mawu a Mlungu koposa china chili chonse zikomo pomvesera Mzimu Oyera kuvumbulutso limeneli. Love your songs mum 🔥🔥
Mai mbusa nyimbo zanu zimandilimbikisa kwambiri Mlungu apitilize kuchita za mphavu pa moyo wanu
I love your songs so much that playlist yanga kuli thoko suya only
God continue using you ❤
Powerful song may good Lord continue bless you and give you more wisdom to continue bless us with these beautiful songs
Mau anu sadzapita pachabe,,, adzakwanilitsa cholinga chanu.. 🙏🙏my daily prayer... Amen
🙏
Thoko suya may God keep on blessing you so that you should also keep on being a blessing to many ❤❤❤
Powerful message, mayi busa you are truly a blessing to many souls, and am one of them...I enjoy and feel high in spirit listening to your songs
Za mphavu kwambiri pa moyo wanga this song and powerful kwa mulungu nyimbo imeneyi ndimene imandilimbitsa mtima panyengo zanga ndikamavera ndimankhala wodzilimbitsa kwa mulungu wanga
This woman is highly favored by the Creator. The production is excellent
Amen
Truth❤❤❤
Ur right
Mau anu Ambuye sadzapita pachabe zoonadi....mau anu adzakhala mpaka muyaya....Amen mayi busa suya....Mulungu akuuze malile anu ...mumatilimbikitsa mu nyimbo zanu zonse.....ulaliki wamphamvu
Love ur songs
Powerful song. There is power in God's Word.🔥🔥
Amen
Lankhulani nane
I listen to this song everyday
Powerful song ndikamavera ndimasuthika ambuye apitilize kukudalitsani
Amen & amen be
Sending u love from Zambia . Nyimbo zanu zimandidalitsa .
Powerful song and it revives my soul
Powerful song
Chimbo iyi imandifikitsa chifupi ndimulungu
This song is powerful
Powerful song, indeed the is power in the word of God....I'm blessed 🙏
Powerful song imandisuntha moyo wanga sindikhalaso chimodzimodzi
Nyimbo zanu zimanditonthoza ndikundisendeza chifupi ndi ambuye
Nyimbo zolimbikitsa pitilizani
Yehova olenga zonse aptilize kuikiza luso lokomali pa inu mai
mom you're so AMAZING mom ❤Almighty GOD please countinue bless our mom Mrs Thoko suya🙏
Beautiful 😍
Ndupempha ambuye apitilize kukusogolelani sister kt mupitilize kufalisa uthenga
Am blessed everyday with this song
Powerful song 🔥🔥🔥🔥 your a blessing to many souls ❤❤❤
Ndipo nyimbu muli unthenga ndipo wandisitha utengau
Mai busa ndinu dalitso pa wathu
Lankhulani nane mbuye😭
Your songs gives me hope n joy
Powerful
Powers song
Powerful am blessed 🙏
In love with this song ♥️🔥
I needed this kind may the Lord bless you sisy
Respect to you mama❤
🙏🙏
Powerful Song 🔥🔥🔥
🙏
Nyimbo zanu ndi pephero pa lokha
This song always comfort my soul
Powerful 💯
The power of word
Wow mama you are amazing
You're a blessing to me mai busa❤️❤️
❤❤❤❤
❤
Mau anu ambuye amen mai busa
Thoko Suya my favorite, I love this woman, God uses you mum, may you live longer and proclaim the greatness and goodness of God . I love you so much mum i wish one day ndizakumane nanu and tap your blessings
Very powerful
Mau amulungu samapita pachabe.🎉
Love ur songs
Powerful song
Powerful
Powerful song