- 3
- 20 643
Dali-Anna
เข้าร่วมเมื่อ 18 ส.ค. 2024
Upcoming artist from Malawi. Venturing into Malawian pop music with dance and visuals.
daliannaofficial@gmail.com
daliannaofficial@gmail.com
Dali-Anna - Ndatopa (feat. Eshent) Official Visualizer [An Andrew Chilonga Film]
Please like, share and subscribe, would really help boost the channel, please and thank you for watching 💖
***LYRICS***
Verse 1 (Dali-Anna)
Wati, take it easy
Ukudziwa ndimakhala busy
Owo? Daily Kodi?
Olo, kundiyimbila phone
Koma ndati nditsimikize
Poti nthawi ya ine ulibe
No hope oh my love
Ndikuyike pa hold right now
Kumwera, kumpoto, pakati ndinasankha mtima wako'we
Tamvera oh
Pang'ono, pa chinthawi ndadikila, ntopa nazo
Pre chorus
Ndatopa, zongokhala ndekha
Ndatopa, zokusowa ndekha
Hook
Nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga , mtima mwanga, mtima mwanga
Chorus
(Ndatopa, zandifowola, ine ndalema, nazo, nazo nazo)
Verse 2 (Eshent)
We have put affairs in order
Ndimakukonda and you know that darling
Sindikuyenda njomba
Si ine njoka mu udzu
Si ine cobra
Nde ukandiona kuti sindikukuona
Pa phone ku khola daily
Ukamagona
It don't mean that I don't love you
Ndimaganizira iwe daily
Nde ndingopusha hustle baby
Ndikupatse zokhumba zako baby
So wine it and slow that thing for me
Mami sekelela, sekelela, sekelela
Nde baby usadande
Attention ndikupatse plenty
Everything you need
Everything you need darling
Pre chorus
Ndatopa, zongokhala ndekha
Ndatopa, zokusowa ndekha
Hook
Nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, mtima mwanga, mtima mwanga.
Chorus
(Ndatopa, zandifowola, ine ndalema, nazo, nazo nazo)
***CREDITS***
Performed by : Dali-Anna, Eshent and Viddix Fyah
Written by: Dali-Anna, Eshent and Viddix Fyah
Shot by: Andrew Chilonga
Music Production: Viddix Fyah and Ghostly Sounds
Special thanks: Repro, Johnnie Kunkhanda, Florence Kunkhanda, Yamikani Kunkhanda, Xemima, Abigail Kululanga, Tapempha Nkhoma.
***LYRICS***
Verse 1 (Dali-Anna)
Wati, take it easy
Ukudziwa ndimakhala busy
Owo? Daily Kodi?
Olo, kundiyimbila phone
Koma ndati nditsimikize
Poti nthawi ya ine ulibe
No hope oh my love
Ndikuyike pa hold right now
Kumwera, kumpoto, pakati ndinasankha mtima wako'we
Tamvera oh
Pang'ono, pa chinthawi ndadikila, ntopa nazo
Pre chorus
Ndatopa, zongokhala ndekha
Ndatopa, zokusowa ndekha
Hook
Nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga , mtima mwanga, mtima mwanga
Chorus
(Ndatopa, zandifowola, ine ndalema, nazo, nazo nazo)
Verse 2 (Eshent)
We have put affairs in order
Ndimakukonda and you know that darling
Sindikuyenda njomba
Si ine njoka mu udzu
Si ine cobra
Nde ukandiona kuti sindikukuona
Pa phone ku khola daily
Ukamagona
It don't mean that I don't love you
Ndimaganizira iwe daily
Nde ndingopusha hustle baby
Ndikupatse zokhumba zako baby
So wine it and slow that thing for me
Mami sekelela, sekelela, sekelela
Nde baby usadande
Attention ndikupatse plenty
Everything you need
Everything you need darling
Pre chorus
Ndatopa, zongokhala ndekha
Ndatopa, zokusowa ndekha
Hook
Nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, nde ndekha mu mtima mwanga, mtima mwanga, mtima mwanga.
Chorus
(Ndatopa, zandifowola, ine ndalema, nazo, nazo nazo)
***CREDITS***
Performed by : Dali-Anna, Eshent and Viddix Fyah
Written by: Dali-Anna, Eshent and Viddix Fyah
Shot by: Andrew Chilonga
Music Production: Viddix Fyah and Ghostly Sounds
Special thanks: Repro, Johnnie Kunkhanda, Florence Kunkhanda, Yamikani Kunkhanda, Xemima, Abigail Kululanga, Tapempha Nkhoma.
มุมมอง: 19 304
วีดีโอ
Dali-Anna ft Eshent - Ndatopa/Ndekha (Official Audio)
มุมมอง 7312 หลายเดือนก่อน
Song title: Ndatopa By: Dali-Anna ft Eshent Verse 1 (Dali-Anna) Wati, take it easy Ukudziwa ndimakhala busy Owo? Daily Kodi? Olo, kundiyimbila phone Koma ndati nditsimikize Poti nthawi ya ine ulibe No hope oh my love Ndikuyike pa hold right now Kumwera, kumpoto, pakati ndinasankha mtima wako'we Tamvera oh Pang'ono, pa chinthawi ndadikila, ntopa nazo Pre chorus Ndatopa, zongokhala ndekha Ndatopa...
🔥🔥🔥
This is fire.. On repeat Was like there's bucci on it too?
Oh Malawi 🇲🇼
Artist ❤️😘🤸♂️🏃🔥🕺kuswa
A collab would be nice😔🔥
@@hi_im_xi just checked your channel 🔥. You can email me
Ndatopa basi
@@EnitaChulu 😂 basitu
Nice tune
Nice tune... And your my crush eheeheh💞😍
Ulibwino
Eshent ndi pangolin 😮😮😮😮😮😮 komano ndkumuva ngti Saint penapake
@@JudahChiyembekezo-c6e Ndi dolo kwambiri.
❤wooow love it
❤❤❤iwe dali tufuna ina ife iyi yatisangalasa🔥🔥
@@Reginahtito in due time, sorting it out 🙏🏾
@@Dali-AnnaOfficial okay mamie please esesa iyi tumaonela dairy🔥🔥
@@Reginahtito I appreciate your support 🩷🩷🩷🩷🩷😭
Nice song 🔥🔥🔥
🔥🔥🔥
Eh mbambande
Wabwela🔥
@@Xavier_Mw been a minute 🩷
@@Dali-AnnaOfficial why isn't eshent in the video
@@Xavier_Mw he was sick that week unfortunately.
Ili bho kwambili nyimboi
dope
Keep it up, ulindi voice yabhoo heavy🔥
@@m-sensevisuals3132 thank you so much 🩷
Wapha
@@captainsisitomalawi1548 zikomo 💗
Eshent on it, good vibes, good energies.
Akometsi recognise this talent please ❤
Sound ili bho heve
🔥🔥🔥
@@vjice_ 🩷 thank you so much 🥳
@@Dali-AnnaOfficial its a great song, vocals on point and the video clean. Keep up the good work coming. This is talent to showcase international, Malawi got talent 🔥🔥🔥💯
@@vjice_ aye aye captain
Zandisangalasa Odi ndipage subscribe 🌹🌹
@@BanksNdugu 🤭 welcome to the club
LET'S GOOOOOOO! NEXT UP
@@narutofox361 🥳
Nice tune
I don't understand what you are saying koma mofaya iyiyi yandiwaza, watching from Russia 😊
@@brightseyani6617 😂 ok
Nice
Beautiful music 🔥🔥
❤❤❤❤
Am your new fan❤
@@chanceaymw-gq1hr welcome to the club
Nfanayu alibho
This is a great masterpiece... I like it 💯💯💯
Nice tune
nice track
Nyimbo iyi chipangireni download ilipa repeat 🔁 nyimbo ili hard 🔥🔥🇲🇼🇲🇼 continue waiting for another banger🔥 we are here to support you ❤
@@MacDonaldMwanje and I appreciate that so much ☺️. Ina pompano.
😍
Zimbabwe approves
@@djk9395 😍 yesss
This song pop up on my feed 🙌 wow NYC song, push it hard 🔥🔥🙌
@@Wikise1992 I'm amazed to see you here!!! Thank you so much 🩷🩷🩷
feature her on a song title Mukazatisiya ena Anditola Mea
What language is this? I like the song
@@subikasam4911 Chichewa 🩷
Dalieee❤❤❤❤
Iwe wekha uchuke First ticket of your show ndizangula
Oooh wow!! This is increadible voice, keep it up💪
Soooooo proud of you❤🎉
@@ShingiraiMkamanga thank you 💕
I'm in love with this song ❤. Ka daily dosage😂
Nice vocals🔥🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Here from Tanzania I like ur vibes🔥🔥
@@KULADINI thank you so much, maybe I can collaborate with one of your artists soon and show off my Swahili. 😜