Wow this song ndangoinvera lero but it deserves a million views and this guys deserves to be a star... ndanvera nyimboyi ndikudusana ndi tiana tikunvera pa Bluetooth speaker mpaka ndatipasa 1000 kuti ayibwereze nyimboyi😢 its really a good song with a good message...nditha kulumikizana naye bwanji munthuyi?
Here in October 2024 … iyiyi munapha 🔥🔥🔥🔥
iiiii nyimbo inayimbidwa iyi🙏🙏
I like voice
Amen
Anyone here in 2024😢❤
Nyimboyi ikundifikitsa Ku Malo kwakuya😂
Kutiko 😂😂😂
Watching from Mozambique Tete
Ndinaimvera koyamba minibus eee ulendo unakoma lelo ndati ndiisake mpaka ndaipeza 😂😂😂
Have known this song last week😢 ndudandaula ndaiziwa mochedwa eishiii.... U killed it Bro❤
Nyimboyi ndiyabwino kwabasi 🙌 kuimva koyamba a few minutes ago, koma nde ndaisaka mpaka ndaipezatu 🔥🔥
a Diness 😅
mbambande tune
On repeat everyday. I don't y I am hearing this in 2024 . 2022 really?
Bless up bro nice tune❤
Anyone with me September 2024
Uyu tiyeni timunthandize guyz
Aise iweyo umatha nyimbo unayikunga bwino Ndayionera ka 4
excellent mboba
Ngat nepman😢
Ndaisaka km nyimboyi eee much love
Anyone 2024??
All along I thought its a zambian song
This is dope tune eeeeehhh
I heard the song yesterday day a abar then i didn't hesitate but to ask the title of the song ,now on my repeat Playlist
Ndipo reapet sichoka nyimbo iyi izandithawitsa nyumb😂
Fada awa ndi dolo
Imakhala pa repeat dàily ,, beautiful song
Man nyimbo iyi munapha it deserves a million views kma vuto amalawi simupanganika
Message yonse kumachita kuimva bwinobwino 🔥🔥🔥🔥
This song is dope🔥👏
❤❤❤❤❤🎉
Tizakumane tizakakalamba man awa amatha. Nyimbo yanji yosaguga
I love this song
nice and promising tune
Wise song
Umumu muli message❤
Mbambande ine ngat sindiimvera Mmm ndimasausika coz imandipitisa patali ambuye akusogolen bos
mkului ndi dolo koma nyimboi ndaivetsa lel shaa😂😂
voices yokha eee❤❤❤❤
Goo broski💪 🔥 🔥 🔥 🔥 you nailed it🎉
Nyimbo munaganiza ulem wanu
0:41 this part is fire !!!!!!! This guy deserves to go viral
munthu wamkulu nyimboi waimba koma tingalumikizane naye bwanji munthui ndimalira nayo nyimboi ndithu moyou siopanganika ai koma kudekha basi
Kma hit iyi ndi fire
Wow this song ndangoinvera lero but it deserves a million views and this guys deserves to be a star... ndanvera nyimboyi ndikudusana ndi tiana tikunvera pa Bluetooth speaker mpaka ndatipasa 1000 kuti ayibwereze nyimboyi😢 its really a good song with a good message...nditha kulumikizana naye bwanji munthuyi?
use the number in the decription section
Nyimbo iyiyi munadekha zed,,message yabwino
Nyimbo iyiyi ndsaname ili bwino kwambiri
🎉🎉🎉 my favorite song
🎉🎉🎉 my favorite songs
This song imandipangitsa moyo wanga kusuntha guyz