Samson Phiri
Samson Phiri
  • 21
  • 109 376
MALAWI INNOVATORS & ACHIEVERS BEN KANKHULUNGO
This brilliant young mind is able to amplify power using his home made machine.
มุมมอง: 58

วีดีโอ

MAWINDO BROTHERS 2
มุมมอง 659 หลายเดือนก่อน
Gawo la Chiwiri la Program yoonetsa anyamata ochokera ku Phalombe omwe akuchita zodabwitsa pa ntchito za Techinology.
CHINAMWALI CHA ZOMA
มุมมอง 539 หลายเดือนก่อน
Kumudzikutu kumachitika Zinamwali,ndipo zambiri zimakambidwa za Chinamwalizi. Kodi Munaonerapo mwambo wotulutsa Chinamwali? Uku Mku Mulanje ndipo sindinafune kuti ndione ndekha.
GAS COOKING- MAWINDO TECH BROTHERS
มุมมอง 3510 หลายเดือนก่อน
Anyamata awiri awa ochokera ku Phalombe akupanga zinthu zambiri. Mwa zina apanga Gas kuchokera ku Petrol..
SAMUEL NDALEMA-Tehila Metal art
มุมมอง 2510 หลายเดือนก่อน
Mkulu uyu wochoka ku Sigelege mu Mzinda wa Blantyre ali ndi luso lopereka Chidwi.Iyeyu amaotchelera zitsulo zakale mkuwumba zinthu ngati Galu,Njobvu ndi zina zotero. Iyeyu wakhala akugwira nchitoyi kwa dzaka zambiri ndipo ndiwodziwika bwino.
GEORGE KALICHERO-Kalichangu e bikes
มุมมอง 5710 หลายเดือนก่อน
George Kalichero Mnyamata waku Mulanje anapanga Njinga yotchaja ,Windmill komanso Stove yamakono.
Sanga Kanthema - Qubix Robotics
มุมมอง 2810 หลายเดือนก่อน
Sanga Kanthema is a brilliant Malawian award winning Innovator who has invented a lot of things. Some of the things proved to be Life serving during the Corona Virus era. This program was aired on MBC inside Innovators and Achievers TV program. Be inspired.
MALE-WIKISE-INNOVATORS AND ACHIEVERS MIRACLE AND FAITH
มุมมอง 4.9Kปีที่แล้ว
Mafana akubangwe omwe anapangapo nyimbo ya Namadingo M'buyomu apanganso Video ina ya Wikise yotchedwa Male. Koma moyo wawo ndi wotani? Program yi inatuluka pa MBC
UPHUNZITSI WA SIGN LANGUAGE
มุมมอง 74ปีที่แล้ว
Malawi ali ndi Sukulu za Sign Language. Koma kodi zimatheka bwanji kumuphunzitsa mwana wosamva Sign Language?
SIGN LANGUAGE
มุมมอง 52ปีที่แล้ว
Munaganizapo kuti mutakumana ndi munthu wosyankhula emwe akufuna thandizo kwa inu kuti Mungatani? Tsiku lina ndinachita mwayi wocheza ndi Munthu mmodzi emwe ndi wosamva komanso kuyankhula. Komatu nde tinaseka..... Uku Kunali ku Embangweni School for the Deaf Mboma la Mzimba.
INNOVATORS & ACHIEVERS THOKO CHIZINGA
มุมมอง 103ปีที่แล้ว
Mnyamata uyu anapanga makina omwe azigaya Chinangwa kukhala ufa wa Kondowole. Zipangizo zomwe anagwiritsa ntchito ndizochita kutoleratolera. The Program was aired on MBC. Enjoy.
FIRST DRIEMO TV INTERVIEW
มุมมอง 67Kปีที่แล้ว
Malawis Afro Pop star Driemo had his first ever TV Interview with MBC. Sam Phiri followed him at his base in Ntchisi where he had also an interview with his Producers Tak Tic and Nyanda. Enjoy
ZION MALINGAKA featuring Sindigwedezeka
มุมมอง 9Kปีที่แล้ว
Mpingo wa Zion umamveka ndi mkhani zosiyana siyana. Kupatulapo kuti amalesa anthu awo kumwa mankhwala Ena akuti amalumpha moto. Kodi iwowa ndi ndani? Taonani
LIKILIKI
มุมมอง 263ปีที่แล้ว
Some women from Area 25 in Lilongwe gained overnight fame with their Song Mbuye Ali Likikili. We Could not resist the temptation of bringing them to the public. Ngakhale muli likiliki komabe 10 minutes yokha mutha kuonera akaka....It was aired on MBC and still remains their Property.
A Chart with Malawi Lesbians #LGBTIQ#
มุมมอง 924ปีที่แล้ว
Malawi has people who enjoy indulging in Same-Sex relationships. Some of them are leaving in hiding but the brave ones are able to come out. In this 10-minute clip, I managed to ask some Girls from Malawi who told me why they feel so attracted to people of the same Gender. I will not disclose the city and names for fear of Homophobic attacks that could follow. The clip was aired on MBCs Good Mo...
Kumudziwa Rasta part 2
มุมมอง 325ปีที่แล้ว
Kumudziwa Rasta part 2
KUMUDZIWA RASTA Part 1
มุมมอง 723ปีที่แล้ว
KUMUDZIWA RASTA Part 1
Ku Khulubvi Part 2
มุมมอง 514ปีที่แล้ว
Ku Khulubvi Part 2
A Chart with ACHALUME hit maker-Wally Chris
มุมมอง 25Kปีที่แล้ว
A Chart with ACHALUME hit maker-Wally Chris
The Musical Lawi
มุมมอง 115ปีที่แล้ว
The Musical Lawi
KU Khulubvi part 1
มุมมอง 192ปีที่แล้ว
KU Khulubvi part 1

ความคิดเห็น