- 28
- 138 704
Enock Bwanali
South Africa
เข้าร่วมเมื่อ 11 ธ.ค. 2013
MANGOCHI TELEVISION
วีดีโอ
TIZINGOPUSHA music video by Mangochi Boys
มุมมอง 32ปีที่แล้ว
TIZINGOPUSHA music video by Mangochi Boys
MH tv Atohn Manje live in Cape Town part 2
มุมมอง 18ปีที่แล้ว
MH tv Atohn Manje live in Cape Town part 2
DR Thomas Nyirenda -TN Stars football club Malawi
มุมมอง 1113 ปีที่แล้ว
DR Thomas Nyirenda -TN Stars football club Malawi
Idrissah Nkomana ndi Eliza Kamwendo wedding
มุมมอง 2367 ปีที่แล้ว
Idrissah Nkomana ndi Eliza Kamwendo wedding
N CHALO -ST ANDREWS CHIYANJANO CHOIR-AULENDO MUNKAKUTI
มุมมอง 1.5K8 ปีที่แล้ว
N CHALO -ST ANDREWS CHIYANJANO CHOIR-AULENDO MUNKAKUTI
Koma asilamu mpaka kuopseza khoti. Malamulo ake akunena iwowa
Mangochi si boma la asilamu okha ngakhale ali ambiri. Aliyense ali ndi ufulu kupanga business iliyonse. Tisamaopseze anzathu. Democracy patsogolo.
Ngati Kuli anthu omwe atakakyambe kulowa kumwamba nde ndasilamu
Thanks for daily brede
Mashaallah zoona
Ku mangochi kulibe aids
Zazi imeneyo sikhani iwowo asilamuwo amadyenga akazi azawo kukwatila kwatila paka muthu mozi akazi 10 sihalamu imeneyo kuberekera ana asikana zupusa mwasowa khani
Tsopano munataya nyama anthu kuthamangira kukatora tinene kuti pamenepa kumangochi kulibe okudya nkhumba , Nanga mowa ndi haramuso koma umwamwedwa mwambiri mpaka kampani ya chibuku ill ndi branch , anakukamizani kudya ? Vuto apa ndi Umbuli ndi kusalemekeza ufulu wa ena
MANGOCHI OSAMULOLA CHAKWELA NDI MANGANYA KUBWERA KUMENEKO
Izinso nde ziti. Kumeneko si ku malawi?
Za ziiiiii
Mowa m'mene ukumwedwera ku Mangochi nawonso ndi haram mwaiona inu ndi nkhumba yokha komanso sanakukamizeni kudya kapena kukudyetsani musakudziwa ndiye wakulakwirani bwanji , Liwonde & Ntaja zikutheka ndiye ku Mangochi kulibeko okudya nkhumba ? KUDzikonda bwanji ku Rumphi ambiri ndi akhristu mizikiti mukumanga bwinobwiino , muli mvuto ndithu.
Simunalakwese asilam lizipezeka dera limodzi loyera 😂😂😂😂😂😂
Zili bwino ❤
I blame government
Ndine khristu koma nkhumba kumpingo kwathu amaletsa kudya detronomo 14 vs 8
Ndine khristu koma nkhumba sindidya ndiyoletsedwa Bible detronomo 14 vs 8
Thats why akukuphwanyani ku gaza kuja asilamu anthu oipa kwambiri inu
Zisilu za anthu khumbayo mumadya kuno ku joni,, mbuli, chimidzi kwambili tayendani muwone agalu
Iweso manyi ako
Ignorance has no defence
Yakula nd musanje
Asilam ndinu olakwa Kodi musikayambili tsamagulitsa nyama yakhumba metsa Muthu umasiya kugula mwaganidza bwanji Kodi mumene dzithu dzavutilamu kumalawi mubwedzeleni ndalama yakhe komatso kumangochiko kulibe ankhilititu?
Part of ignorance. Amaona ND anthu akeso
Sizoona kuletsana kupanga business Malawi ndi dziko la aliyense not asilamu okha be serious guys
Mowa ukugulitsidwa kumangochi si Haram? Nanga bwanji nkhumba ikuvuta alipo anakakamizidwa wa chisilamu kudyetsedwa ,Umbuli ndiye vuto APA.
Ndiye akut walakwa kugulitsa nkhumba? Wolakwitsa ndi otayawo chifukwa ogulitsayo sadawakakamize ,kodi kumaboma ena asilimu kulibe nanga nkhumba imadibwa bwanji?_Nanga amene amadya sakuwaphera ufulu? Vuto ndi umbuli by the way Malawi is a secular state kod Mangochi ndi state payokha
Bulumuv
Mabubho
Allah wakubalu Means mwala waukulu
Asilamu si anthu antenderetu ndichonwe mudziwe
Mungosatila chipembedzo choti simukuziwa kuti kodi mukupita kuti 😂😂😂😂eish anthu amisuli inu
Nkhumba ndi ntchimo koma chigololo ayi mmmm koma chipembezo ichi ndiye kaya Muhammad mwini wakeyo ankadya nkhumba
Ase manyi ako
Dziko ndi la aliyense ili palibe ulamuliro wa ntundu umozi
😂😂😂😂😂 mademo a mijomba anakaziwa kuti muli madyo mu ngumba
Musiyenso zoyimba ng'oma and muziswali
akuyakhula ndi athu ena awa sakuyakhulana chifukwa zikusephana
Nkhani zopanda mutu izi
Manyaka 🤣🤣🤣
Ngakhale kuno Ku south Africa mashop ndiyambili ofuna amagula ngati sumadya umasiya koma zopusa zanuzo aaaaa chamba kwambiri
Ndiye Kuti Mulungu analakwa kulenga nkhumba bvuto umbuli umene ukupangisa...akulimbana ndi namalenga chifukwa ndiamene analenga zonse zamoyo
Kuweluza ndikwa mwini mulungu asilamu ngat simudya nkhumba chisakhale chiphyinjo kwa Ife timadya ndipo mumimba ndimwathu pakamwaso sitibwereka Panu podyela nkhumbapo zopusa bas Bible mumawerenga koma uhule mumapangaso mukuwona ngat kulakwa ndikudya nkhumba kokhako zazii
Mburi za anthu odya nkhumbawo amadyera pakamwa panu
Iweyo ungangulise nyama yolesedwa malo ayo
Mumachita machimo ambirimbiri kunyenga akazi a eni kupha azanu kusetera mmanja kumwa mowa nde mukamulange nzanu chifukwa chankhumba muphuzire kupita kusukulu
Manga amagulitsira kunyumba kwako? Uchimo onse mumachita asilamu inj:1Nyanga,ufiti,dziwelewele,ndiye munenapo chani apa.
Mukuti nkhumba harram nanga mitala imene mumakwatira si harram eti agalu
Eyo mind ur mouth dude pls let's respect each other's bro
Ine singasiye mkhumba kudya ku mangochi kutitso
Vuto ndi umbuli ayawo kumangochi ndiye aliyese ndi musilamo basi Zausiru
Iweso chisilu
Ine ndimakhala ku Newlands (JURBERG)pamalopo pali chisilamu wokha wokha koma za uchisuru zokhazokha achehe kumasintha azimayi anzizawo ankandifusa why you r eating pork? naneso ndimafusa bwanji iwe kumasintha azimayi komaso umanyenga akhazi a ena ache ? Abale zose akziwa mulungu no judgement pa dziko lapasi mu christu or musilamu tose ndife ana amulungu
Umbuli kodi asilamu mumalanda akazi a enaache kwa mulungu sinchimo kumapha anthu sinchimo dziko lapasi nkhondo zimachitika ndi asilamu kukangana ndi a christu mbuli zeni zeni Muhammad si mulungu kodi analenga nkhumba ndi mulungu not Muhammad
Mashaalah
Kodi inu mukuyelekedwa, inu ndinu asilamu?????????? Mumangomva za chisilamu eti????????????
Tizingoyakhulani zichewazo mukuwonangati zazizunguzo zikupinduliran