![The Boom Mic](/img/default-banner.jpg)
- 12
- 24 288
The Boom Mic
South Africa
เข้าร่วมเมื่อ 3 ธ.ค. 2023
Arts and entertainment🎤🎬
วีดีโอ
The boom mic interview with DJ Clen #malawi #zambia
มุมมอง 1012 หลายเดือนก่อน
The boom mic interview with DJ Clen #malawi #zambia
The boom mic interview with Laynex Luther
มุมมอง 1365 หลายเดือนก่อน
The boom mic interview with Laynex Luther
The boom mic interview with kay Lux (MR X)
มุมมอง 7716 หลายเดือนก่อน
The boom mic interview with kay Lux (MR X)
The boom mic interview ep 4 with Lay b salima
มุมมอง 19K6 หลายเดือนก่อน
The boom mic interview ep 4 with Lay b salima
The boom mic interview ep 4 with mazzo openga
มุมมอง 3.2K6 หลายเดือนก่อน
The boom mic interview ep 4 with mazzo openga
The Boom mic interview with Edmond khwisa(Nyumwisa)
มุมมอง 1867 หลายเดือนก่อน
The Boom mic interview with Edmond khwisa(Nyumwisa)
The Boom Mic Ep1 interview with Luckcious
มุมมอง 1387 หลายเดือนก่อน
The Boom Mic Ep1 interview with Luckcious
kunayakatu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Koma kuli nkhondo 🔥🔥
Fully🔥🔥🔥
Kuyakhula chilungamo ndi mkaz wanga nice
Umakwana bro
Ndiwe shasha openga
❤❤ hello
mfanayu amatha koma sogolo ndilowa ase
Za ziiiih
Ndipo nkaziyo ndiopoila zachani akupangazo
Thando ❤
Khala serious aise moti mabilinganya empire sumaiziwa iweyo
Mtola nkhani yo atochitatu manyazi abale madamu waso hiya aaa 😂😂
Ninga konde wamenyako ndi wax
😂😂😂
Wow🎉❤
🔥🔥🔥🔥
Zoona a nchuzi🎉
Za nice 🥰
Yooo nice
Madala
Nduchita manyazi ndine 😂😂😂😂
😀😀😀
everything has its on time tu happen i think lay b yamukwanila km ku mbali yangaa mmm akanapusha kae muzic kt akhale ndi dolla
Dolo kwambr lay b and congratulations for the family ife timkaonatu ngat stunt lol but anyway zobeba kobas
Akatundu 🔥🔥🔥
Machine
Eee nkulu ameneyu amatha guys🙌💥💥💥
Taona naotaona siliko ziliko
Kkkkkkkkkk kom banja ili lidzathela mapenete
Adonawo😂
km wafulumiza kukwatila unakapusha kae zingin
Ex azimva kuwawa
Madam are serious kwambiri eeeee
Wish all the best to those Guys
2024 more music 🔥🔥🔥🔥
BIG UP
Ndiwe kape lay b
Zosililika km kd achimwenewa ali ndi zaka zingat ??? Mwina nafenso tizilimbikitsika kut olo uli mfana utha kukwatira ndithu
Dolo kwambiri💪🏾
Umakwana now he's deserving as a model of other pipo so osamaphweketsa, vep ilibh due to his age,he supposed to pull up his socks
Keep on
Keep burning Lay B
Mmmh ulendo wa career ukupita kokufa
😂😂😂komatu nde eee amadamo pango.no pisakukharira pamyendo 😂😂
Lay b amatha kuimba
Big up lay b iweyo umatha Nice couple❤❤
Komatu akaziwo eeeeee🙌
Not impressed
Alibho heavy
Zilikotu ziliko conex Banda Kodi alikuti mwina taonani taonani ntsika wachikondi nanga mayi poleka Inu mkazi wamkulu taonani taonani😂
Nice couple ❤
Apa lay b akupanga Kaye zachikondi, sound tidikile Kaye.