MALAWI TODAY
MALAWI TODAY
  • 16
  • 368 528

วีดีโอ

ZOMWE WANKHULA MICHAEL USI KU KHWIMBI LA OTSATIRA UTM KU MZUZU
มุมมอง 3219 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ZOMWE WANKHULA MICHAEL USI KU KHWIMBI LA OTSATIRA UTM KU MZUZU
NORMAN CHISALE Wachenjeza komanso kupeleka chiophyezo kwa anyamata a MCP
มุมมอง 2.8K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
NORMAN CHISALE Wachenjeza komanso kupeleka chiophyezo kwa anyamata a MCP
A Kaliati Ayankhulatu
มุมมอง 10K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
A Kaliati Ayankhulatu
PROPHET BUSHIRI Vs PROPHET MBORO
มุมมอง 24519 ชั่วโมงที่ผ่านมา
PROPHET BUSHIRI Vs PROPHET MBORO
Prophet Habakukk Chikondi Chakhodzokera😁
มุมมอง 106วันที่ผ่านมา
Prophet Habakukk Chikondi Chakhodzokera😁
ACHAKWERA SANAGONE KUCHIPANI KOMA AKUGONA KU BOMA
มุมมอง 149วันที่ผ่านมา
ACHAKWERA SANAGONE KUCHIPANI KOMA AKUGONA KU BOMA
KULANKHULA KWA JOICE BANDA (11 Aug 2024)
มุมมอง 122วันที่ผ่านมา
KULANKHULA KWA JOICE BANDA (11 Aug 2024)
MCP Kuwonetsa Utsogoleri Wabwino
มุมมอง 1.2Kวันที่ผ่านมา
MCP Kuwonetsa Utsogoleri Wabwino
HOT CURRENT SUMMARY 21 July 2024
มุมมอง 627หลายเดือนก่อน
HOT CURRENT SUMMARY 21 July 2024
VITUMBIKO MUMBA KUYAMBAPO KUTIMBWATIKA
มุมมอง 879หลายเดือนก่อน
VITUMBIKO MUMBA KUYAMBAPO KUTIMBWATIKA
JOSHUA VARELA KUDZUDZULA MKHALIDWE OIPA OKHUDZA IMFA YA SAULOS CHILIMA
มุมมอง 83Kหลายเดือนก่อน
JOSHUA VARELA KUDZUDZULA MKHALIDWE OIPA OKHUDZA IMFA YA SAULOS CHILIMA
MDIPITI WODABWITSA WA MAGALIMOTO😳 PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA
มุมมอง 7Kหลายเดือนก่อน
Intensified security convoy of the president of Malawi
Zoona A President Tizikhalira Kukukuwani? Wonder Akutero. 8 Oct 2023
มุมมอง 12K10 หลายเดือนก่อน
Zoona A President Tizikhalira Kukukuwani? Wonder Akutero. 8 Oct 2023
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2
มุมมอง 50K10 หลายเดือนก่อน
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
มุมมอง 192K10 หลายเดือนก่อน
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1

ความคิดเห็น

  • @CharlesEliya-d3e
    @CharlesEliya-d3e วันที่ผ่านมา

    Big up Mr kapito And God bless you

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s วันที่ผ่านมา

    Malawi its 4 malawians not 4 mr chikangawa tru speaking mr kapito A.P.M our vote

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s วันที่ผ่านมา

    Thats true sakudziwa za boma ,palibe akudziwa za u presdent thts why wangosanduka chigawenga

  • @thokozanichikafa6602
    @thokozanichikafa6602 2 วันที่ผ่านมา

    God bless you mwamasuka kuuza a malawi

  • @DanielMaruwo
    @DanielMaruwo 2 วันที่ผ่านมา

    That's number one Mr kapito speaking as a man of integrity

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i 2 วันที่ผ่านมา

    My vote

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 2 วันที่ผ่านมา

    Zoona,zoona A.P.M wawina kale olo mr chikangawa olo adzabele sizizanukha kanthu adzipita gwape amenei D.P.P oyee!

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 2 วันที่ผ่านมา

    Ife tikufuna tidzidya msima kuyambila mamawa,masana,madzulo, usiku imeneo nde D.P.P

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 3 วันที่ผ่านมา

    🔥🔥🔥

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v 3 วันที่ผ่านมา

    Bodza ili, mavuto adalipo kuchokera nthawi ya kamuzu, Komaso inuwo a Dpp. Nthawi imene mudali boma bwanji wosathetsa mavutowo.

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z 3 วันที่ผ่านมา

    Professor afa peter muthalika😂

  • @AbudulKamodzi
    @AbudulKamodzi 3 วันที่ผ่านมา

    Mcp ndimbola achuluka ndi anthu ufuna kusilemereza okha osanganizira mavuto awena

  • @RAJABSTYLESTYLE-yi1el
    @RAJABSTYLESTYLE-yi1el 3 วันที่ผ่านมา

    kugulidwa kotai koditu zamavuto alipano sikuti munthu ungsmunsmize

  • @spargomw
    @spargomw 3 วันที่ผ่านมา

    Mr Chisale more fire❤❤❤❤❤❤ Ndasangalala kwambiri kut mwawina❤❤❤ Tikufuna chitetezo cha mphamvu zeeeeeedi kwa Adad❤

  • @PiliraniDanielDaniel
    @PiliraniDanielDaniel 3 วันที่ผ่านมา

    Ife timuvoteraso Chakwera! Dowa yake iti inu munamepo apa! Anthu atatu oti angogulidwa ndiye kumati Dowa ingavotele nkhalamba yosankha mitunduyo

    • @AbudulKamodzi
      @AbudulKamodzi 3 วันที่ผ่านมา

      Achewa inu ndi agalu chifukwa mavuto alipanopa sakuwona kuti uyu anavotela mcp tonse tikulila limozi

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 3 วันที่ผ่านมา

      Tsankho silingapose zomwe aluchita Chakwera ni nyau zinzake. Tsano anthu ali ni ufulu osankhula uyo alufuna. Dziko sila Chakwera ili ayi.

    • @MaritaBanda-p4z
      @MaritaBanda-p4z 2 วันที่ผ่านมา

      iwe ndichisiru osaganiza ndi chikangawa wakoy akupas zingat kut uzilakhula zoduka mutu galu ukuvutikaso chitsiru iwe ubwin wake tonse tikugula zodula limoz

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 2 วันที่ผ่านมา

      Inuso inu nde opanda nzerudi Kutengela kuti ndi ochewa onzanu Muluvutika or panado muzipatala Tsankho lipose asùweni akowo opatsa udindo okhaokha khalabe usasunthe uwone 2025 Poti mudzabela mpake mukukula matako

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 2 วันที่ผ่านมา

      Iweso uli wekha don't be stupid

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 3 วันที่ผ่านมา

    Muto ndi la kupha chilima

  • @GeorgePatels-go7wj
    @GeorgePatels-go7wj 3 วันที่ผ่านมา

    DPP Moto Kuti buuuu

  • @JohnPetro-vv3er
    @JohnPetro-vv3er 3 วันที่ผ่านมา

    Amalawi ozindikila kwambiri

  • @tasmania527
    @tasmania527 3 วันที่ผ่านมา

    Si Dowa ya genuine iyi. DPP siingaphule kanthu ku Dowa. Ochita kugulidwa awa kuti abebetse DPP. Phuma chipani cha DPP, kuwina sikulongolola-owina 2025 ali phee. You can tell kuti anthu awa nga phuma through their leader's speech. A Mutharika kuyankhula mbwelera yokhayokha ngati kuti ma voters onse ali mmanja mwawo."Dikira madzi apite ndipo uziti ndadala".

    • @FrancisMazamba
      @FrancisMazamba 3 วันที่ผ่านมา

      Mot lwe sukuwona mavutowo lne kwanthu ndikasungu Koma sininganene Za chikangawa Kut wapanga chitukuko

    • @tasmania527
      @tasmania527 3 วันที่ผ่านมา

      @@FrancisMazamba Waboza iwe ukungopanga disguise. Chakwera ndi dolo osati zinazi.

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 3 วันที่ผ่านมา

      ​@@tasmania527 udolo wake pakupha chilima ndi ena aja ndi uchigawenga mzomwe akukwanisa plus kugwesa kwacha daily, mkuthwa mkamwa kma pa ground ndi 0/10

    • @ThokoLungu-tq6pw
      @ThokoLungu-tq6pw 3 วันที่ผ่านมา

      Ndi brother wanga uyu from dowa Ndithu Sanagulidwensoi unama zed mmmmm

    • @tasmania527
      @tasmania527 3 วันที่ผ่านมา

      @MzadziWanga Don't forget kuti munatiphela anthu 20 ku mzuzu, munapha ma Albino, munapha Njaunju, munapha Chasowa. Imfa ya Chilima yinali ngozi chifukwa ndege yinali yakutha ndipo mulibe umboni woti anaphedwa, nde shut up.Nkhanza zanu ndi kuyipa kwanu mumachita kunyada nako ndipo zinali pa mbalambanda.

  • @CustomMphandauyo-oe3jq
    @CustomMphandauyo-oe3jq 3 วันที่ผ่านมา

    Anzawo akugaula nursery pano... Anthu awulesi awa

    • @MaritaBanda-p4z
      @MaritaBanda-p4z 2 วันที่ผ่านมา

      koma zomwe akuyakhulaz ukuzimveses bwino lomwe chikangawa iwe

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 2 วันที่ผ่านมา

      Ulesi ndiwe osati Zagwilizana pati Mudamuphelanji chilima asatana inu

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 3 วันที่ผ่านมา

    achewatu amenewo chilungamo kuyenda ngati manzi

  • @OssmanAbubaker-k3q
    @OssmanAbubaker-k3q 3 วันที่ผ่านมา

    Chilungamotu chimenechi osaopatu osafooka osatopa kkkk

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 4 วันที่ผ่านมา

    Awa tikakumana Ku conversion

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx 4 วันที่ผ่านมา

    koma chisale amandipats mantha kut uyuyu kupeze kut wawina koma mwati dzikoli izayenda bwanji

  • @LoudonChauluka
    @LoudonChauluka 6 วันที่ผ่านมา

    Uremuwani mama

  • @DanChirwa
    @DanChirwa 6 วันที่ผ่านมา

    Mumakwana akweni

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 6 วันที่ผ่านมา

    Ndipo a Kweni ayankha mwa ulemu a aka khala Brian banda eeee tinakaonatu zinthu nda kweni

  • @SoftwareSolutioz
    @SoftwareSolutioz 6 วันที่ผ่านมา

    Kweni woyeee

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 6 วันที่ผ่านมา

    A Kaliati poti apa akukuitanirani ku DPP kumeneko mukakhala nobody zonse mukukamba apazi zizatheka muzidzangolira kuti wa PA CARRIER SAIMBA BELU

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 6 วันที่ผ่านมา

    Akweni munangokhala mzimai koma ndinu katundu

  • @ChiyembekezoCharles
    @ChiyembekezoCharles 6 วันที่ผ่านมา

    nkweni umakwana

  • @MayamikoYMsusa
    @MayamikoYMsusa 6 วันที่ผ่านมา

    Zoona mama,,yankhulani

  • @user-ez8uk7py8n
    @user-ez8uk7py8n 6 วันที่ผ่านมา

    Good speach welcome aKweni❤

  • @user-ez8uk7py8n
    @user-ez8uk7py8n 6 วันที่ผ่านมา

    Good speach welcome aKweni❤

  • @MayamikoYMsusa
    @MayamikoYMsusa 6 วันที่ผ่านมา

    Mumakhwana kwene

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 6 วันที่ผ่านมา

    Munthu oyipa anagulitsa chipani

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 10 วันที่ผ่านมา

    Achunga why has he failed Malawi, time has told. He owns the good and the bad.

  • @user-bl2ee4zk4n
    @user-bl2ee4zk4n 11 วันที่ผ่านมา

    Zosangalasa kwambiri kuti woluza akuvomeleza ndikulonjeza kupita chisogolo kugwira ntchito ndi omwe apambana,izi zasonyeza kuti MCP Ndichipani cha mtendere komanso chokondana wina ndi mzake ngati banja limodzi.MCP 2025 ndiyo wina kale,yayika foundation ya bwino kwambiri kuyambila pa convention kukasilizila kuma region ndima district.what a beautiful picture displayed by MCP Party.This sends a clear signal of strategic and mature leadership of president Dr Lazarus maccarthy chakwera.❤❤❤❤❤❤❤

  • @MacDonaldJiyan
    @MacDonaldJiyan 16 วันที่ผ่านมา

    Kapito , you say infact so God bless you plus

  • @JohnBanda-bh5gz
    @JohnBanda-bh5gz 18 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi nkhaniyo ndiyowona

  • @user-qu5ks3kk6v
    @user-qu5ks3kk6v 26 วันที่ผ่านมา

    Kapito is a genius

  • @MercyJohnsonkanchure
    @MercyJohnsonkanchure 26 วันที่ผ่านมา

    😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 27 วันที่ผ่านมา

    Mr.Kapito your now talking. Kodi Aboma Samamvela mfundo ngati zimenezi bwanji kuti Dziko lathu nkutukukako.Ambuye akudalitseni nonse ogwiritsa ntchito mau amenewa

  • @stevenbanda6665
    @stevenbanda6665 27 วันที่ผ่านมา

    Very clear

  • @user-hx6jd4yy4u
    @user-hx6jd4yy4u 28 วันที่ผ่านมา

    Hi

  • @GloriaChikwawe
    @GloriaChikwawe 28 วันที่ผ่านมา

    Mtima udakawawabe ine 😢😢😢😢

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu 29 วันที่ผ่านมา

    Yes indeed

  • @MatemangaMoyo
    @MatemangaMoyo หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 palibe, mkapune

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน

    Mbava ngati iwe angakuvotere ndani waba iba ndi nick cakwera lero ufuna upitilidze kuba

  • @jacquechisale6809
    @jacquechisale6809 หลายเดือนก่อน

    Komano akubanja mwaiwala kutiko chilima anali ndani ... anthutu sasiya kupitako kumandako coz muthu uja anthu amamukonda